Kulinji? Tidziwe

Kulinji? Tidziwe To gather and disseminate news stories

28/12/2020

Andale, inu mukule ife tichepe

23/12/2020
18/12/2019

Anthu Okwiya Atentha Njinga Zamoto Zokwana Zisanu Ndi Imodzi Zomwe Zimagwiritsidwa Ntchito Ndi Ma Ofisala A Pa Chipatala Cha Bowe Ku Dowa. Anthuwa Ndi Okwiya Ndi Mnamwino Wina Emwe Akuganiziridwa Kuti Sanathandize Mzimayi Oyembekezera Moyenera Zomwe Zinapangitsa Kuti Mzimayiyo Amwalire. Poyamba Anthuwo Anathyola Ndi Kuphwanya Galimoto La Mnamwinoyo. Ngakhale Anthuwa Anakambirana Ndi Akuluakulu A Bungwe La Anamwino Zkusonyeza Kuti Mkumano Wawo Sunaphule Kanthu. Reported By Precious Leonard Mwale

17/12/2019

BREAKING NEWS Pakistan's Former President Pervez Musharaf Has Been Sentenced To Death For Treason.

26/09/2019

French president Jasques Chirac has died.

29/07/2019

Paramount Chief Ngolongoliwa Of Thyolo District Dies.
He Was Admitted On 24 July 2019 At Mwayi Wathu Hospital In Blantyre. He Died On 28 Of July 2019.
Ministry Of Local Government Through Its Public Relation Officer Has Comfirmed The Insdent.

18/03/2019

Form 4 Boy With Albinism Has Gone Missing In Balaka District

14/03/2019

MCP-PP ALLIANCE
Kutangotsala masiku owerengeka kumka ku chisankho cha patatu pa 21 may chaka chino, mtsogoleri wa MCP Dr Lazarus Chakwera akukambirana ndi mtsogoleri wa chipani cha PP Dr Joyce Banda Kuti Agwire Ntchito Limodzi, M'mawu Ake Mneneri Wa MCP Rev. Maurice Munthali Watsimikiza Za Nkhaniyi. Iye Wati Cholinga Chawo Akufuna Kutulutsa Malawi Mu Chipsinjo.

14/03/2019

DPP SITENGA NAWO MBALI PA DEBATE.
Chipani Cholamula Cha Democratic Progressive Chalengeza Kuti Oimira Chipanichi Sakhala Nawo Pa Mtsotso Omwe Uchtikire Ku Comesa Ku Blantyre Lero. Malingana Ndi Chikalata Chomwe Mlembi Wamkulu Wa Dpp A Jeffrey Atulutsa Dzulo, Dpp Izigwiritsa Ntchito Njira Zina Zokopera Anthu Osati Mitsutso Ai.

31/12/2018

Malawi Congress Party President Dr Lazarus Chakwera Said He Will Resign As President After Two Years Of His Ruling Term If He Will Not Accomplish His Predges.

31/10/2018

kusowetsedwa kwa makina a Malawi electoral commission ( MEC) zaphera mphongo komanso kubweretsa poyera kulephera ntchito ya commissioner WA bungweli Mayi jean Ansa.
ichi ndi chifukwa chokwanira kuti commissioneryu asiye pansi udindo wawo mabungwe omwe si aboma kuphatikizaponso zipani zina zotsutsa boma akutero.

21/09/2018

Akuluakulu a boma Ku Lilongwe akukana kulandira petition

Address

Blantyre

Telephone

265885704004

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kulinji? Tidziwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share


Other News & Media Websites in Blantyre

Show All