Sameer Suleman akuti: "A Chikangawa, zomwe mandipangazi, mwandipasa mangolomera."
Wonerani ndi kumvera nokha.
Mkulu wa nyumba ya boma yowulutsa mawu mdziko muno ya MBC, a George Kasakula, akuti palibe mutsogoleri yemwe angapitilize ntchito zachitukuko mdziko muno kupatula a Lazarus Chakwera. Iye wati a Peter Mutharika, a DPP, ndiwokalamba kwambiri, azikangogona ku State House kusiyira anthu ngati Norman Chisale ndi a Getrude Mutharika kuyendetsa dzikoli. Iye watinso a Dalitso Kabambe, a UTM, siwodalirika chifukwa anatenga chipani cha UTM mokuba potero simunthu wokhulupirika.
Wonerani kanemayi:
Highlights from Prophet Shepherd Bushiri's Crossover at AHL in Lilongwe where over 25 000 people, drawn from different parts of the world, gathered and prayed together to end 2024 and begin 2025.
Enjoy.
Anthu mazana mazana akupitiliza kuzaza ku Golden Peacock Complex ku Lilongwe komwe kukufikira alendo ochoka kunja omwe akubwerera kuzakhala nawo pa Crossover ya Prophet Shepherd Bushiri.
Uyu si pangolin?
A Dr Michael Usi akuti alibe ukali ndi mkwiyo ndi a Dr Dalitso Kabambe. Komanso akuti komwe ayitanidwa kukayankha milandu, sapitako chifukwa alibe nthawi.
Wonerani.
A Jeju Air Boeing 737-800 carrying 181 passengers crashed while landing at Muan Airport in South Korea, leaving at least 124 dead. The flight originated in Bangkok, Thailand.
Shocking footage shows the plane veering off the runway, colliding with a wall, and erupting into flames. Early reports suggest poor weather and a possible bird strike as contributing factors, though the cause remains under investigation.
Two survivors, both flight crew members, have been rescued from the wreckage as emergency teams continue recovery efforts. This tragedy has left the nation and aviation industry reeling.
We will keep giving you updates.
#Nyasatimes
Hilton Banda, a renowned businessperson and philanthropist, together with his wife and children, brought smiles and warmth to the elderly residents of Mai Mbambande Care Home in Lilongwe this Christmas. On Friday, December 27, the Banda family, including their two children, Tadala and Tikondane, spent the day celebrating with the elderly, reminding them of their value and importance during the festive season.
The celebration was made even more special with a performance by Jetu, an elderly musician who continues to inspire others by pursuing her passion for music. Banda explained his reason for inviting her, saying, “Jetu is a shining example that age should not stop anyone from achieving greatness. I wanted the residents to see that they too can continue to live fulfilling and meaningful lives.”
The event featured music, food, and moments of shared laughter, creating an atmosphere of joy and community. Deborah Mbale, founder of Mai Mbambande Care Home, expressed her gratitude, calling the event a “wonderful treat” for the elderly. The Bandas’ heartfelt gesture was a powerful reminder of the importance of honoring and cherishing the elderly, especially during the holiday season.
Click the link below to read the full story: https://www.nyasatimes.com/mr-and-mrs-hilton-banda-brings-christmas-joy-to-the-elderly-at-mai-mbambande-care-home-in-lilongwe/
Uyu ndiye akutipula pa ground.
Vice President Dr Michael Usi kuyankhula ndi anthu pa Chileka CDSS ku Lilongwe loweluka.
#nchezo
Akuti yemwe aziti kwacha ku Ndirande azithamangisidwa!
Mtsogoleri wa chipani cha UDF a Atupele Muluzi alimbikitsa a Malawi kuti, ngakhale zinthu zikuvuta mdziko muno, aliyense ayetsetse kulimbikira pa nkhani ya ulimi kuti tikhale ndi chakudya chambiri.
#Nyasatimes
Mmene zikumvekera, akuti Prophet Shepherd Bushiri akubweresa zinthu zoti a Malawi ambiri sanaziwonepo ku Crossover ya chaka chino.
Tikupasirani zambiri.
Mkulu wa NRB a Mphatso Sambo afotokoza motere:
Vidiyo iyi taitenga pa Nation Publications Limited