Malawi Bureau of Standards (MBS) has reopened Chipiku Plus at Wenera following its closure yesterday.
The shop was closed due to poor storage, inadequate pest control, mixing of spoiled and good products, and poor ventilation.
MBS officials have confirmed that the shop owners have addressed the issues that led to the closure.
By Grace Donga
#CFMNews
#Malawi
[Video]
Chichiri Shopping Mall ShopRite in Blantyre has been shut down for selling expired products and failing to maintain proper hygiene standards.
#CFMNews
#Malawi
Madzi osefukira akusautsa anthu mu msika wa Tengani m'boma la Nsanje, kutsatira mvula yochuluka yomwe yagwa m'derali.
Ngakhale kuti boma linamanga msika wamakono m'derali anthu ochita malonda sanasamukirebe kumsika wamakonowu kaamba koti ulibe mzinthu zina zofunika monga magetsi.
Zambiri mu kanema uyu;
Wolemba ndi kujambula: Manford Chirombo
#CFMNews
#Malawi
Nduna ya za ntchito Vitumbiko Mumba wakalipira mayi wina yemwe ndi mkulu owona zolemba anthu ntchito pa kampani ya NT plastics kwa Njewa mumzinda wa Lilongwe kaamba kothandizira kuti nzika za dziko la China zizinyozera malamulo.
Kampaniyi anayitseka dzulo kuti akonze zina ndi zina koma lero ayitsegula, ndipo mayiyu amayankha andunawa zomwe zinawakwiyitsa mpaka auza a ku ofesi yoona zan tchito kuti afufuze maphunziro àwo.
Zambiri mu kanema uyu;
Wolemba ndi Kujambula: Joseph Mazizi
#CFMNews
#Malawi
DAYBREAK MAALWI WITH GRACE DONGA
Daybreak Malawi with Grace Donga. Where are you listening from?
Wildfires menacing Los Angeles have killed at least 10 people and devoured nearly 10,000 structures, with five fires burning into a third night on Thursday, as dry desert winds fanning the flames again gathered strength.
The Palisades Fire between Santa Monica and Malibu on the city's western flank and the Eaton Fire in the east near Pasadena already rank as the most destructive in Los Angeles history, consuming more than 34,000 acres (13,750 hectares) - or some 53 square miles - turning entire neighborhoods to ash.
The Palisades Fire between Santa Monica and Malibu on the city's western flank and the Eaton Fire in the east near Pasadena already ranks as the most destructive in Los Angeles history, consuming more than 34,000 acres (13,750 hectares) - or some 53 square miles - turning entire neighborhoods to ash.
A wildfire ripped through an upscale coastal area of Los Angeles overnight, with Hollywood celebrities among those evacuating by car and on foot.
Details in this video by Reuters
Text by Jorge Garcia and Rollo Ross
Credit: Reuters
#CFMNews
#Malawi
LIVE! DAYBREAK MALAWI WITH JANE KAONGA
LIVE! DAYBREAK MALAWI WITH JANE KAONGA (Where are you listening from?)
Panali chisangalalo panja pa bwalo la milandu ku Lilongwe bwalo la milandu ku Lilongwe nduna yakale ya zachuma Joseph Mwanamvekha ndi ena anayi omwe anamangidwa dzulo, atatulitsidwa pa belo.
Oganiziridwawa awatuluta popanda chikole cha belo kaamba koti nkhaniyi ayitumiza ku bwalo la milandu lalikulu.
Izo zikutathauza kuti ambali ya boma adzachita kulembera ku bwalo lalikulu pa mfundo za belo lomwe awapatsa ( Bail conditions)
Iwo akuwaganizira kuti anapalamula milandu yokwana isanu ndi itatu.
Lolemba apolisi anamanga asanuwa powaganizira kuti akukhudzidwa ndi kusokonezedwa kwa ndalama zoposa K447.5 billion za kampani ya Salima Sugar yomwe inali pansi pa Greenbelt Authority.
Wolemba ndi kujambula: Catherine Banda
#CFMNews
#Malawi
Hundreds of people in a rural part of Ethiopia, 165 kilometres north-east of the capital, Addis Ababa, have been leaving their homes in panic as a nearby volcano has been showing signs of a possible eruption.
A local chief, Sultan Kemil, has told the BBC that the smoke coming from Mount Dofan that began around 17 hours local time on Thursday has a fiery plume that is very high.
In a video posted by the Ethiopian Geological Institute on its page, steam and debris can be seen shooting out from the mountain.
In recent weeks, there have been more than a dozen seismic events around Awash Fentale – an earthquake-prone area of Ethiopia’s Afar region.
Meanwhile, an official evacuation process is under way to prevent harm to residents amid earthquakes that are getting higher and stronger with tremors also being felt far away in Addis Ababa.
#CFMNews
#Malawi
Anthu ochuluka asomkhana pa Masanjala m'boma la Chiradzulu kudikira m'tsogoleri wa chipani cha DPP Peter Mutharika.
Mutharika akuchititsa minsokhano yoimaima m'maboma a Mulanje, Phalombe komanso Chiradzulu ati ndi cholinga choti afotokozere zina mwa mfundo za chitukuko zomwe chipani chake chakonzera aMalawi.
Pa ulendowu, Mutharika akulimbikitsanso anthu kuti azitenga nawo mbali mu zochitikachitika za chisankho.
Wolemba ndi Kujambula: Andrew Salima
#CFMNews
#Malawi
Happy New Year!
Mwachilowera kuti?
#escapeordinaryradio
#keepitcapital