Nchalo daily news

  • Home
  • Nchalo daily news

Nchalo daily news Pure and fresh news from nchalo only

Looking for a school to send your child to ? Tumizani ana Anu ku little shining stars ndipo simuza khumudwa Imbani pa nu...
05/01/2025

Looking for a school to send your child to ?
Tumizani ana Anu ku little shining stars ndipo simuza khumudwa
Imbani pa number iyi kuti munve zambiri
0886884504

17/12/2024

It's tomorrow.....ukuku kuzakoma

13/12/2024

CHENJEZO

Unduna wowona za madzi ndi ukhondo kudzera ku nthambi yowona za madzi walengeza kuti mitsinje ina mzigawo zapakati ndi kummwera ikuyembekezeka kusefukira pakati pa Lamulungu likudzali pa 15 December 2024 ndi mpakana Loweruka likudzalo pa 21 December 2024.

Undunawo wati mitsinjeyo ikuyembekezeka kusefukira kaamba ka mvula yochuluka yomwe namondwe wotchedwa Cyclone Chido yemwe akuchokera panyanja ya Indian Ocean akuyembekezeka kubweletsa malingana ndi ulosi wa nthambi yazanyengo.

Mitsinje yomwe ikuyembekezeka kusefukira ndi monga Nkula, Linthipe, Lingadzi, Lipimbi, Lifidzi, Nadziphuru, Livulezi,Nasolo, Mudi, Lilongwe, Diamphwe, Likangala, Thondwe, Namadzi, Phalombe, Namphende, Sombani, Likhubula, Mwanza, Lisungwi, Mkulumadzi, Mkombedzi wa Fodya, Nyachipere, Thangadzi ndi Thuchira.

Mchikalata chomwe watulutsa lero, undunawo walangiza anthu kuti apewe kukhala mmphepete kapena mmbali mwa mitsinje yomwe yatchulidwayi komanso akhale tchelu kuzizindikilo za ngoziyo komanso azitsatira malangizo omwe akupelekedwa.

We are a newly opened school located at Nchalo trading centre next to ESCOM and opposite smallholder..We have Baby class...
06/11/2024

We are a newly opened school located at Nchalo trading centre next to ESCOM and opposite smallholder..

We have
Baby class
Nursery
pre reception and
Reception

We have qualified teachers and English is a must ..

Register your kids today.

For more Information contact our Administration office on
0886884504

Little Shining Stars kindergarten School
We shine like stars in the u universe..
(Phillipians 2 v 15)

23/10/2024

Vacancy
We are looking for a teacher at little shining stars

Requirements
The person should have an MSCE certificate

Good at speaking English

Those with an ECD certificate will have an added advantage

Call this number for more information
0886884504

You can start bringing the application papers today

21/10/2024

CHIDZIWITSO

Sukulu yabwino ndinso yapamwamba yomwe inatsekulidwa pa Nchalo moyandikana ndi escom ikufuna kuthandiza ana awili omwe ndi ochepekedwa..

Anawa akhale ochokela pa Nchalo trading ndipo azaka 3-5.

Anawa Azaphunzila mwaulele pa sukuluyi komanso azagulilidwa zonse zofunika ngati uniform,school shoe,zikwama,makope,zolembela komanso chakudya chapa break ndinso lunch.

Ofuna kumva zambili atha kulembela ku [email protected], Whatsapp pa 0886884504 komanso m***a kuwayankhula ku page ya school Yao Little Shining Stars kindergarten School .

Kodi zabwino zipose apa?

Schools are now in session. Join us at Little  Shining stars Private-schools where the student have loads of fun and exc...
23/09/2024

Schools are now in session. Join us at Little Shining stars Private-schools where the student have loads of fun and exciting activities such as Career Day! Painting , gardening, coloring,🎉 Sports, Drama etc. Enroll your little ones today. Classes available in Baby class, Nursery , Reception and primary standard 1 to 4..Our contact: ⁨0886884504/0999218221

Nchalo next to ESCOM...

22/09/2024

Uthenga kwa makolo
Pa 23 September kuku tsegulidwa primary school yo cheaper ya 10 thousand pamwezi ,
School Ili pafupi ndi Escom kuno kunchalo ....
Imbani number iyi kuti munve zambiri
0990710023

19/09/2024

Little shining stars ndiyo primary school yosa bowola nthumba imenene ikutsegulila pa 23 September Monday lomweli .
Fees 10 thousand pamwezi
Sukuluyi Ili pafupi ndi Escom kuno kunchalo
Mukafuna kunva zambili imbani number iyi 0990710023

Nkhani yake ndiya sukulu yapamwamba koma yotsika mtengo ..Little Shining Stars kindergarten School  Yomwe ikutsekulidwa ...
18/09/2024

Nkhani yake ndiya sukulu yapamwamba koma yotsika mtengo ..
Little Shining Stars kindergarten School
Yomwe ikutsekulidwa lolemba pa 23 September 2024.

Sukuluyi ikupezekela moyandikana ndi ESCOM.

Ndipo ana 5 oyambilila kulembetsa Azaphunzila mwa ulele kwa mwezi umodzi komanso kupasidwa uniform Yao yokongola mwa ulele .

Kuphatikiza apo mwana aliyense azadya breakfast mwa ulele kwa mwezi onse.

Inu sukulu yabwino iposele apa?

Sukuluyi yayambila nursery class kulekezela standard 4.

Call or whatapp the director on 0886884504.

"Exciting News!🥳🥳

We are thrilled to announce the opening of Little Shining Stars kindergarten School a nurturing and engaging learning environment for your little ones!

Our preschool is dedicated to providing a safe, stimulating, and child-centered space that fosters social, emotional, and cognitive growth.

Our classes are baby classnursery class reception class

Standard 1-4

School fees is k10 000 per Month and breakfast is inclusive.
School opens on 23 September 2024

Join us for a fun-filled journey of discovery and exploration!

We are in Nchalo next to ESCOM.

We can't wait to welcome your child to our preschool family!

Little Shining Stars
-we shine like stars in the universe-
(Phillipians 2 v 15)

Tataya mtumiki wa mulungu, Bishop dauya omwe analalikila pa ground pa council pa malilo a malemu Chipililo black .Iwo at...
08/08/2024

Tataya mtumiki wa mulungu, Bishop dauya omwe analalikila pa ground pa council pa malilo a malemu Chipililo black .

Iwo atisiya lelo mammawa pa ngozi yomwe yachitika ku ntcheu pa malo otchedwa
Bawi-Nkhumba.

Iwo pamodzi ndi mkazi wawo komanso anthu Ena awili anamwalilila pamalo angozi omweo, ndipo Ena awili avulala.

Mayina a anthu otisiyawa ndi ; Bishop Eric Dauya ndi akazi awo Mercy, Elizabeth Maonde ndi mwana wawo wa zaka 22 Deborah.

Chidziwitso!!Kukutsekulidwa sukulu yatsopano yotchedwa Little Shining Stars kindergarten School  pano pa Nchalo trading ...
06/08/2024

Chidziwitso!!

Kukutsekulidwa sukulu yatsopano yotchedwa Little Shining Stars kindergarten School pano pa Nchalo trading center...

Sukuluyi ndiya ana oyambila zaka 2.

Fees zao ndi k15 000 pa mwezi ndipo ana 20 oyambililao kulembetsa azadya lunch mwa ulele kwa mwezi umodzi pa sukulupa.

Get your toddlers ready...
Mangani malamba chifukwa sukuluyi ikuyendetsedwa ndi akadaulo osata za maphunzilo ndipo simuzakhumudwa..

Tikhala ndi interview ndi eni sukuluyi masiku akubwelawa.khalani pomwepa..

Zikomo

Tiwoneleko kanyimbo aka pa YouTube, kachikhalidwe chathu chachisena
25/06/2024

Tiwoneleko kanyimbo aka pa YouTube, kachikhalidwe chathu chachisena

18/05/2024

SAD NEWS
We have lost Naira Issa mkazi wa Gafar.

Amene anali mayi ake Ashard yemwenso watisiya mwezi watha omweu.

May Ashard's soul keep resting in peace...

May Naira,s soul rest in peace.
INNALILLAH WAINNA ILAIHI RRAJIUN

16/05/2024

Mongokumbusana....

Today's date is 16th May 2024..

Mwafika kale ku court??

Jetu ukutu..Tiyeni tikaipemelele. panea garden is the place...3pin mmanja..mkati mwenimwemweni.Iwe ndi ndani 😋
14/05/2024

Jetu ukutu..
Tiyeni tikaipemelele. panea garden is the place...3pin mmanja..mkati mwenimwemweni.

Iwe ndi ndani 😋

To our lovely Top fans..Mukupeleweledwa zingati kuti mugule ticket yaku show? Keep commenting mmusimu...Our lucky 5 winn...
12/05/2024

To our lovely Top fans..

Mukupeleweledwa zingati kuti mugule ticket yaku show? Keep commenting mmusimu...

Our lucky 5 winners will be announced p***a....

Thanks for being part of Nchalo daily news ...
Without kuipatsa Moto kwanu, Ife kulibe.

Followers3
Everyone

12/05/2024

Go get your tickets pa Humphrey Photography mwamba pa Nchalo shopping complex komanso kwa MR TMORE

Ife ndiye tili mkati mwenimweni....

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nchalo daily news posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share