The only hopefully DPP presidential aspirant without any rumors of misconduct, Rt Hon Dr Paul Gadama during the recent DPP press briefing.
Uyu akufunika kumusiyira chipani bร si, mpatseni achikonze moyenerela. Uyu mgwamzeru uyu
Don't miss a chance
No Gadama, no DPP bouncing back into the government come 2025
The first and last life president
The founder of Malawi Republic
May His Soul continues resting in peace
Ngwazi Dr Hastings Kamuzu Banda
Father and founder of Malawi Republic
The first and last life president of Malawi Republic
The founder of Malawi Congress Party
May His Soul continue resting in peace
"Siya"
โSiya"
Akazombo agawa okha fantaa๐
Nkhani ija kuno๐คฃ๐คฃ๐คฃ
Tamia ja anthu amakuputatu
Professor Joe Gwaladi wagula njinga ya moto ndi ndalama zomwe wabwela nazo ku joni komwe amakayimba
More fire mbuyache๐ฅ๐ฅ
Mwanza yayakhula dzulo pamene mighty Malawi Congress Party (MCP) inali ndi msokhano wa chitukuko (development rally)
Uku kunali akuluakulu achipani cha MCP monga Hon Richard Chimwendo MP omwe ali Minister of local government and national unity komanso Youth director, Hon Mia amene ali Minister of water and sanitation ndi akuluakulu ena, kumaloku kunapezekaso Hon Nicolas Dausi omwe ndi mphungu waderali komanso mneneli wa chipani chotsutsa boma cha DPP.
Kupezeka kwa Hon Dausi ku msonkhanoku kwadzutsa manon'gonon'go ku chipani cha DPP kuti Hon Dausi abwelera ku chipani chawo chakale cha MCP.
Kodi kupezeka kwa Hon Nicolas Dausi pa msonkhano wa boma umene umachitikira mu dera lawo mkolakwika?
Perekani ndemanga zanu ku comment box
Ndale ndipa ground ๐ฒ๐ผ
#RoadTo2025
#trending
2. #secondvideo
#GiboPearson kumulangiza professor Joe Gwaladi monga mzake after the first video went viral
Professor sakukumbukira kalikonse, Madam Professor kuyipatsa moto pansipansi๐๐
#Trending
1. #FirstVideo
Professor Joe Gwaladi kusangalara ndi ndalama zomwe wabwera nazo ku Joni.
Collage Herbal๐
Those remembering this, let's gather for comments
M'busa wina wamenyedwa kamba kokakamiza kupepherera munthu wina yemwe amaganiziridwa kuti ali ndi dziwanda.
M'busayu amakuwira munthuyi kuti "fire, fire, fire". Izi ndi zomwe amachita azibusa pamene akupepherera munthu kuti ziwanda zimene zili mwa iye zipse ndi moto wa uzimu.
Tsoka ndi ilo munthuyi anatibula m'busa yu mpaka kugwetsa moto onse kuzimitsa
"Fire, Fire, Fire" ๐ฅ
Osakakamizana kupephera komanso osamenya azitumike a Mulungu๐
Akuluakulu ananena kale kuti Njovu zikamamenyana umavutika ndi udzi
Tiyeni tikhale anthu odekha komanso owugwira mtima pamene tikuliyamba tsikuli pakuti zichitochito zathu zitha kupangitsa ena kuti avutike
Ambuye atidalitse mu tsiku limeneli
Amen๐
Katakwe pa chuma, mwini wa FDH Bank, Thom Mpinganjira kuyakhula mwa nve nve nve
Chinsinsi chokonza mitengo ya chimanga kuti ikhale yofikilika ndi kutsitsa mitengo ya fertilizer..
Ga Ga Ga, Dhe Dhe Dhe ๐
#Malawi_Media_Network joins the first citizen His Excellency Dr Lazarus Mcthany Chakwera in celebrating #Kamuza_Day
As Malawians, we celebrate this day with joy and pride.
The late #Mgwazi_Dr_Hastings_Kamuzu_Banda is the founder of the Malawi Nation
#Happy_Kamuzu_Day
Lero ndi Friday
Loรฑg weekend
Continue Resting in Peace Martse ๐
Rt Hon Dr Paul Gadama, The Only DPP presidential aspirant recognized worldwide
As days are closing by to the great day of DPP convention, a day for the real change, new blood and face for DPP when the most decorated DPP presidential aspirant Rt Hon Dr Paul Gadama will take over the party's presidency from Professor Arthur Peter Mutharika, the international community has finally recognise him as the next DPP president and Malawi as a country..
On Monday this week, the next DPP president, Rt Hon Dr Paul Gadama was on News Central TV talking about his stand for the DPP presidency and Malawi's current situation
Eeeh situweshoni vere kilitiko, zinthu zafikapo ๐๐๐
Mmodzi mwa atsogeleri amene akukapikisana nawo pa mpando wa u president wa chipani cha DPP, #Rt_Hon_Dr_Paul_Gadama
Eeeh komatu kuyakhula ngati anabadwila konkuno๐คฃ๐คฃ๐คฃ๐คฃ
Uyu adzivota๐คฃ