Kashoti Vibes

Kashoti Vibes Ubwino wake mwafika. Page sikula yokha ifunika dzanja lanu.

29/03/2024

Mbewu ya cha nkhotakota ilipotu

Kodi Jaa Kev  munamuyankha kuti Eya kapena Ayi?Fukwa ndiye simmene kuliri🤣🔥
23/03/2024

Kodi Jaa Kev munamuyankha kuti Eya kapena Ayi?

Fukwa ndiye simmene kuliri🤣🔥

19/03/2024

Kuno ndakumana ndi mzungu akumvera Crispy Malawi akuchita kusatilizira nyimbo ya Pake Pake Pake Pake Pake nayenso ndi gaku bwake🤣

18/03/2024

Ati ngati inaduka PTC iwo ndi ndani?
🤣

17/03/2024

Mwabwerako koonera game kapena basi m'madana ndi zopusa🤣

17/03/2024

Kodi Zeze uja amati Zokhudumwisa, Zodukhumwisa kapena Zokhumudwisa ndi zambiri...

17/03/2024

Ndiye ati munali ndi ndani dzulo?

16/03/2024

Artist wake ndi uti amakupangisani nokha kuzimamva kuti mmaziwa zinthu zabwino? Mutchuleni azifile yekha🔥🔥🔥

16/03/2024

Nyengo ino osadya nyama eni eni ndi ma Ras omwewa. Enawa mzokayikisa

15/03/2024

Ndiye kuti Airtime ifunikadi?

😂😂💔Mpaka pa kona gagaga,Nkhani ya ku TARGET inayamba chonchi kuti ipheduke Mikoz yangofikira pa Climax.Hedi ndi Mwana ga...
15/03/2024

😂😂💔Mpaka pa kona gagaga,Nkhani ya ku TARGET inayamba chonchi kuti ipheduke Mikoz yangofikira pa Climax.Hedi ndi Mwana gagaga gegege hede💔😂😂😂🙌

Check out TNC MALAWI265's video.

Munthu amafuna ma freestyle 10 chomulesera nd chan🤣🤣😂💔🔥👏👏
14/03/2024

Munthu amafuna ma freestyle 10 chomulesera nd chan🤣🤣😂💔🔥👏👏

35 likes, 4 comments. Check out TNC MALAWI265's video.

06/03/2024

Akuimba nyimbo za bwino ndi ma Upcoming Artist omwewa.

02/03/2024

🔥🔥🔥🔥NYIMBO YA BWINO IYI ATI SINATULUKE.

Zeze wakana Ku Kips wa joina anyamata a Memo 🔥👏such a humble artist,simomwe chikutemera nthongo😂😂😅
25/02/2024

Zeze wakana Ku Kips wa joina anyamata a Memo 🔥👏such a humble artist,simomwe chikutemera nthongo😂😂😅

Check out TNC MALAWI265's video.

Address

Blantyre
312213

Telephone

+265997529501

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kashoti Vibes posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share