๐“ฌ๐”ƒ ๐“ฌ๐“ฒ๐“ซ๐“ฎ๐“ผ

  • Home
  • Malawi
  • Blantyre
  • ๐“ฌ๐”ƒ ๐“ฌ๐“ฒ๐“ซ๐“ฎ๐“ผ

๐“ฌ๐”ƒ ๐“ฌ๐“ฒ๐“ซ๐“ฎ๐“ผ ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

12/12/2023

Ma********ng paka dogstyle koma Atumbuka ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

12/12/2023

Ubwino wake chaka chamawa munenacho ndi mwezi wamawawu๐Ÿ˜‚๐Ÿ’”๐Ÿ™Œ๐Ÿƒ

11/12/2023

Mbuye mtima mumatenga my number 1..
๐Ÿค—
Happy birthday Shammah Vocalzz

11/12/2023

Mungawadziwe bwanji atiloge nawo?? ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

11/12/2023

Chibwezi mpaka kupempha ya fertilizer ๐Ÿ˜ฅ

23/11/2023

Dzulo tagura fon kuma demoโ˜บ

08/11/2023

Atamenyedwa limodzi ndi malume awo anvekere ๐Ÿคฃ

20/10/2023

Km yeah anthu mukuyera๐Ÿ˜‚

19/10/2023

Anakuzani k*ti chatha kapena ndi ngozitaya ๐Ÿคฃ

19/10/2023

Nde kwabadwa ma hule ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ

30/09/2023

๐Ÿ˜ wrong number : hello mk*ti mukumeneko kuyimbirako.
๐Ÿฅฑ Me. : Muyimbira kuno kukhutu boss

16/09/2023

Ngat ndisamamva English ndenso heart break ๐Ÿ’” ndichan

13/09/2023

Ikakhalla English ndakhozano six akakhala masamu marks anga asowo

23/08/2023

Morning inu abambo okoza mugututu๐Ÿคฃ

22/08/2023

Dad ndiwe wak*ti okuda chonchi km ungakhale ndi mzimu oyera iwe๐Ÿคฃ

20/08/2023

Ulendo wina muzajambulitsire Kwanu iya ๐Ÿคฃ

19/08/2023

Mwadzuka bwanj pakhomo pamakolopo mwamasukapotu mpaka mwayamba thupi laku banja.

18/08/2023

Vuto ndiloti munaona ngati aliyense amakufunani๐Ÿคฃ

17/08/2023

Joker wanu uja wapeza chibwezi China kuno๐Ÿคฃ

17/08/2023

Zikuoneka k*ti zovala zija zilibe mwini mwini๐Ÿคฃ

16/08/2023

Ngati leader wa mkalasi yathu walephera JCE nde ine ndi ndani k*ti ndimupose anatero mabvuto atamufunsa abale ake๐Ÿฅฑ

16/08/2023

Kupanda bambo anu kukhwima bwezi muli ndani inu tiona sakukalamba๐Ÿคฃ

15/08/2023

Ukagwira Slay_Queen
Umakhala ndi 2years yonjanja
Zinazo zimathera pa mphasa
Kenako zaiwe timafufuta
โœŠ๐Ÿ’ฅโœ…๐Ÿ˜‚

14/08/2023

Kupanda Snapchat bwez ulindani galu iwe๐Ÿคฃ

13/08/2023

Ati avala chowonetsa mchombo km kuona kamimbako Kali biiii ngati mafuwa๐Ÿคฃ

11/08/2023

Adona yosavala mwadoyi nde mutiphanayotu๐Ÿคช

10/08/2023

Azikaseka admarc nde Dstv ndi kachan zachamba๐Ÿคฃ

08/08/2023

Mkazi ozindikila adasiya kale kale kukhumudwa
Chifukwa cha mamuna
Amangodandaula k*ti business sikuyenda
๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ

03/08/2023

Musamba ๐Ÿค”

02/08/2023

Ati matenda kuwatsiya kuno kukawatengera ku jonz iwe ulinduwusilu eti ๐Ÿคฃ

31/07/2023

Mwadzuka bwanj pakhomo pamokolo anupo๐Ÿคญ๐Ÿคญ

30/07/2023

Kumalawi kwavuta mpaka mfumu yamuzi kupita kujoni ๐Ÿ™‰๐Ÿƒ

30/07/2023

Mkazi ๐Ÿ’ƒndi kumbuyo nanga mwamuna๐Ÿ•ด????

29/07/2023

MDF yaku South Africa ak*ti athana ndima foreigners sakuwafunaso kukhala mu dziko la south Africa aliyese azipita kwao

29/07/2023

Nde period iyambe uli mu swimming pool sibas red Sea๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿคฃ

28/07/2023

Ubwin okhala bashala umatha kusendera mbatata Sheva๐Ÿคช

14/07/2023

Timadziwa Ife k*t MBC ikaonetsa mpira timaluza ๐Ÿคช

14/07/2023

Ndiwe wak*ti Dadie๐Ÿ™„okhumbila mamuna nzako? ๐Ÿ’”

02/07/2023

๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ misara iponsele kuvula zovala zonse ndiku vala ๐Ÿ‘‰CHISHANGO๐Ÿ‘ˆ ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ

Address

Blantyre

Telephone

+265982235666

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ๐“ฌ๐”ƒ ๐“ฌ๐“ฒ๐“ซ๐“ฎ๐“ผ posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ๐“ฌ๐”ƒ ๐“ฌ๐“ฒ๐“ซ๐“ฎ๐“ผ:

Share