Pemjizzy Mw

Pemjizzy Mw This page is about bringing smiles, laughter and also displaying local talent and latest news around Africa and the world together with multimedia. ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ
(1)

06/11/2024
This must be   playing   ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ Tchyaayaaa!!!!
05/11/2024

This must be playing
๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ Tchyaayaaa!!!!

YAOMBATU KHOMA APA๐Ÿ’”๐Ÿ’”Amunanga anatenga phone yanga ndi kudilita number ya Chibwenzi changa Michael ndipo anatenga Number ...
05/11/2024

YAOMBATU KHOMA APA๐Ÿ’”๐Ÿ’”

Amunanga anatenga phone yanga ndi kudilita number ya Chibwenzi changa Michael ndipo anatenga Number yawo ina ndikuseva dzina la Michael monga momwe ndinalembera ineyo...

Tsiku lina Michael ananditumira message k*ti zamuvuta akufuna ndalama yokwana 100 sauzande,,osadziwa kt anthu anawawuza Amunanga kt ndikuwazembera ndipo ine cfk ndimamukonda Mamuna wachibwenziyu ndinanamiza Amunanga k*t andigawireko 100 pin ikufunika kumudzi kwavuta...

Amunanga anandipatsadi ndipo ndinamutumira Michael ku Account yomwe anandipatsa...kenako ndinamuyimbira Michael k*t nditsimikize ngt ndalamayo yafika..

Ndinadabwa kumva mawu a Amunanga akuvomera kt ndalamayoyafika.....ndinathawa pakhomo pa Amunanga ndipo ndikukhala kwa Nzanga pano week yatha tsopano....

Ndasowa mtengo ogwira nditani??,?

Angakhale ndan ku Malawi kuno ameneyi๐Ÿ‘€
05/11/2024

Angakhale ndan ku Malawi kuno ameneyi๐Ÿ‘€

Kumasamalatu kwa anzathu omwe tikupita ku NSANJE kuli SOMBA zoduphila mkamwa ohoo๐Ÿ˜‚
05/11/2024

Kumasamalatu kwa anzathu omwe tikupita ku NSANJE kuli SOMBA zoduphila mkamwa ohoo๐Ÿ˜‚

01/11/2024

๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ
Bad news ๐Ÿ“ฐ
Bambo Mwamadi ku balaka nyamata njala onse kufa, modzi kugwa ndikukumba okha ndi mwanayo k*tisiya momo๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

DEAR AKAZI  IZI NDI NJIRA 6  ZABWINO ZOLANGILA MAMUNA AKAMAPANGA ZIBWEZI1. Mamuna mukamuvera k*ti akupanga chibwezi akuk...
01/11/2024

DEAR AKAZI IZI NDI NJIRA 6 ZABWINO ZOLANGILA MAMUNA AKAMAPANGA ZIBWEZI

1. Mamuna mukamuvera k*ti akupanga chibwezi akukuzembelani musafulumire kukhumudwa. Inuyo ingotini phee musamukwiire olo kumufusa. Akabwela mochedwa mutelekeleni madzi asambe kenako pitani kuchipinda. Gulani ma emergency pill or prep kapena pep mukangomaliza kugonana naye imwani k*ti asakupasileni matenda. Muzimwa asakudziwa ai

2. Muthandizeni mmene mungathele mpaka khalidwe lakelo asiye. Munyengeseni koopsa ndipo mukondeni mpaka azasiya kupanga zibwezi zanserizo.

3. Akasiya mukondeniso kwambiri kenako mwadzidzidzi nyenganani ndi mzake wapamtima ndipo nkhaniyo uzani munthu amene mukuziwa k*ti akamuuza ndipo yesetsani k*ti imupeze. Ikamupezani nkukufusani vomelani k*ti mwanyenganadi ndinzakeyo ndipo zizamuwawa kwambiri akatero azadana.

4. Mupepeseni mochokela pansi pamtima ndipo muzilila daily mpaka mamina uku mukupepesa mpaka akhululuke. Akangokhululuka dekhani ndipo muonetseni k*ti ndinu osinthika ayambeso kukukhulupililani kwambiri.

5. Pamene mwayambilaso kumwava kwambiri ndipo akukudalilani ndi kukukhulupililani nyenganani ndi mngono wake. Zikatero pangani zoti aiziwe nkhaniyo ndipo akakufusani vomelani k*ti zoonadi koma sindimaziwa chomwe ndimachita chonde ndikhululukileni. Pepesani koopsa kuposa koyamba kaja ndipo yesetsani mwamphavu zose k*ti aiwale zakale ndipo pangani zoti amve k*ti mwasinthadi mok*ti ayambeso kukukhulupililani kwambiri ndipo zimvanani naye kwambiri

6. Mukondeni molapitsa nde akangoiwala zakale zija nyengananino ndi bambo ake k*ti akhaleno mwana wanu mukatero pangani zoti nkhaniyo aimve akakufusani vomelani nk*thesa chibwezicho kapena banjalo. Mukatero mamuna mwamutha asamazolowele kudabula.

Zikomo

31/10/2024



Mkulu wa Bungwe la Mera, a Henry Kachaje, wapepesa ku mtundu wa a Malawi ponena k*ti dongosolo la kapezedwe ka mafuta m'dziko muno sikadayende mene amayembekezela.

a Kachaje ati bungweli likuchilimika pofuna kuonesesa k*ti zonse zikuyenda bwino, ndipo ati aMalawi asade nkhawa, popeza zonse zikhala zitalongosoka pofika nyengo ya Khirisimasi

Njala zake zimenezi tizibelanaso๐Ÿ˜
30/10/2024

Njala zake zimenezi tizibelanaso๐Ÿ˜

22/10/2024

Alendo mpaka kugona maliseche!

 #๐Ÿ˜โค๏ธ
22/10/2024

#๐Ÿ˜โค๏ธ

20/10/2024

Ndinali ku National bank kokapanga activate account koma simmene chiseko chija chandimenyera nsana.
Boma ili litipha ndithu๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

10/10/2024

Ndi mkazi yekha emwe amapilira zofooka za mamuna wake, pomwe agalu ambiri amunawa zofooka za mkazi wawo amakauza chibwezi chawo

Address

Zomba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pemjizzy Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Pemjizzy Mw:

Videos

Share