16/09/2023
Malipoti ena akusonyeza kuti katswiri wa mpira wamiyendo Chimwemwe Idana wabwelela ku timu ya Silver Strikers
Idana anachoka ku timuyi mgwirizano wawo (Silver Strikers) wa miyezi isanu ndi umodzi utatha ndi timu ya Mbeya City ya ku Tanzania
Tapeza kuti timu ya Silver Strikers ilengeza zonse bwino lomwe lero lisanathe pa mgwirizano watsopano omwe apanga ndi Gattuso Idana pomwe pali malipoti oti osewerayu wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri ku timuyi
Chimwemwe Idana anasewerako ku timu ya Nyasa big bullets mmbuyomu asanapite ku timu ya Mbeya yomwe anamupititsa pa ngongole ku timu ya Silver
====================================
➖➖ KUCHIMAKE KWA NKHANI ➖➖➖
▫️▫️▫️▫️◼️ 🇲🇼MALAWI◼️▫️▫️▫️▫️
▫️▫️▫️▫️♦️ GOSSIPS ♦️▫️▫️▫️▫️▫️
▫️▫️▫️▫️🟢 ORIGINAL🟢▫️▫️▫️▫️▫️
📌📌📌📌📌📌📌📌📌📌📌📌📌📌
NKHANI ZOSAKONDERA MBALI ILIYONSE
➖🇲🇼🇲🇼➖ ➖🇲🇼🇲🇼➖