Akungi

Akungi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Akungi, Digital creator, Molhalaletsi, Polokwane.

20/01/2024

Akungi tabwera apapa admin wanu anemenyedwa kuchibwedzi😞💔

14/01/2024

Akungi.....mulikuti?

30/12/2023

Muli kuti?...

27/12/2023

Koma amalawi tipuma? Kuchedza kwanji uku?🤣🤣

25/12/2023

Nde nkumazati chan kufotokoza kwake mawa lino?

24/12/2023

Lero tigawe airtime yochuluka motan....?

22/12/2023

Munthu Wataya Mimba ndikumavalaso Zoonesa Mchombo ife Tiziona Chilizacho😇😭

21/12/2023

Dzuwa lake limeneli, kuti uyambe kusisita mwendo wa mwamuna mzako, mpaka unyowe ndi lero?

21/12/2023

Kodi ndi bwino m'silamu kuika manyowa a Nkhumba munda mwake??

As we promised Akungi....Airtel TNMTag your  friends  to follow Akungi nawoso adzidya nawo bwino🔥🔥
20/12/2023

As we promised Akungi....

Airtel
TNM

Tag your friends to follow Akungi nawoso adzidya nawo bwino🔥🔥

789DA94,63FEA50...20 legs....tip-ov 1.5 goals...19+ odds...Akungi tiyeni tikungeni... komaso tipepese dzulo tinakanika k...
20/12/2023

789DA94,63FEA50...20 legs....tip-ov 1.5 goals...19+ odds...

Akungi tiyeni tikungeni... komaso tipepese dzulo tinakanika kugawa ya stake ndi airtime tikhala tikugawa lero at 7pm lero sitikunamiza palibeso cholephelesa dzulo tinatanganikwa🤝..

Follow our page for more updates Akungi

20/12/2023

Apapa we can confirm kuti Queen Sheba uja amangodyesera pamene Mai Dan Lu anali oyembekezera🤝😂

20/12/2023

Tchulani woyimba amene m'mamuteteza olo atalakwitsa motani koma mumakhalabe ku Mbali yake ngati Kuti amakulipirani.

Kodi Transport Yochoka Ku Mzuzu Kupita ku Btz Ili pa Bwanji Pano??
20/12/2023

Kodi Transport Yochoka Ku Mzuzu Kupita ku Btz Ili pa Bwanji Pano??

20/12/2023

Nde Kwatulukaso Ma N**e Aku Mpingo Omwewo

20/12/2023

Pangen TAG mzanu modzi wa CATHOLIC adziwe kuti mumakonda.🤣

19/12/2023

tiyeni tikunge..

Game ya Chelsea - Yellow cards Under 6.5
Everton Double Chance
Dortmund ✅
Napoli ✅
Leipzig ✅
Man City ✅
Al Hilah double chance
Hoffenheim ✅
Atletico Madrid double chance

Komano key ndi Betway Malawi, ma odds abho.

Betway Malawi

Penaso timadzaona ngati uyuyu mumati 6th  mwana yi amangofuna azimu user to build  his brand.. Basopu🫵
19/12/2023

Penaso timadzaona ngati uyuyu mumati 6th mwana yi amangofuna azimu user to build his brand.. Basopu🫵

19/12/2023

Ife tinkadabwatu ma school a girls and boys okhaokha aja😂🙌

19/12/2023

Tiyen titchule mayina amahule ndayamba ine 🙌Memory🙌😂

19/12/2023

Akungi tiudzeileni a betwapa kuti deposit ku TNM ikuvuta '...

19/12/2023

Nde paja amalawi muli ndikupanga accuse zili zonse Gwamba za catholic zii simumupangaso? Mxiew

Za Catholic  sizatiwalise kuti Temwah  amatiimilira malawi muno🔥🤏
19/12/2023

Za Catholic sizatiwalise kuti Temwah amatiimilira malawi muno🔥🤏

19/12/2023

Apa sibasi mpingo watsala opemphera choonadi ndi Chisilamu bas
😁🙂

19/12/2023

Tingoti a Catholic wa ndi a satanic basi🤣🤣

19/12/2023

The first 700 pple to follow Mfumu Jalifu mulandila bundle direct ku inbox ...let go first come first serve ...7PM

19/12/2023

If you recognize the doctor then you won't see heaven 🤣🤣

Address

Molhalaletsi
Polokwane

Telephone

+27648243222

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Akungi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Akungi:

Videos

Share

Nearby media companies