06/12/2024
Eeh nde ku Italy akuti amanga Nun (Sistere) pomuganizira kuti ndi member wa Mafia.
Akuti apolisi akhala akufufuza gang yoopsya kwambiri ndipo agwira anthu awiri andale komanso Sistereyu, dzina lake Sister Anna Donelli.
Apolisi alanda ndalama zokwana £1.5 million.
Akuti Sister Anna nde anali mkhalapakati olumikizitsa Mafia ndi gang yoopsyayi. (Allegedly).
Sidenote:
Shaaa nde tidzipempherera kuti ngati mu mpingo muli Mafia