Mzebede

Mzebede Notícias, vídeos & Serviços

14/01/2026

Oque tens agora é muito important.

14/01/2026

Um agradecimento especial aos meus maiores fãs mais recentes! Bernaldinho Alberto Bessitala, Teslaeffect Bwanalisauteni, Cláudia Manuel Gabriel, Marcelino Lidane Chicapa, Pedro Manuel Nunes

14/01/2026

Um obrigado especial aos meus novos seguidores! Que entusiasmo poder contar convosco! José Thomo, Nanda Erique, Atanaziyo Lusiyano welcome. Be free here

13/01/2026

SAMALANI AKUPUYANI PA FACEBOOK PANO

Nthambi yoona za information (Institute Nacional de Comunicação de Moçambique)(INCM) iyamba kukhoma onse omwe adzipereka mauthenga omwe angadzetse kapena kupereka Chiopsezo kudziko.

Uthengawu waperekedwa Lero lachiwiri 13.01.26 pansonkhano wa atolankhani, omwe makosana a nthambiyi anachititsa.
Nthambiyi yati, ganizoli silatsopano, koma likungounikidwanso, pakuti liankhazikitsidwa koyamba mu 2014, koma analiunikanso mu 2023. Paichi zinafunikira kuti akozenso mwina ndi mwina pofuna kuligwirizanitsa ndi nyengo zino.

INCM yati pakhala njira zozindikirira anthu amene adzikhala iyamba kufalitsa mauthenga opereka chiopsezowa, ndiponso ndondomeko zake mpaka kufika powakhomera masamba awo anchezo .

Mwa njira Ina, zikuoneka kuti, pankumanowu zadziwikanso kuti, pa anthu omwe adziwatsekerawa adziwatsekuliranso mulandu.

____________________________________
Note: Pakufunika kusamala mabwebwetedwe, apo biii upezeka uli kuseli kwa mabagala baaaa.
__________________________________

INFORMATION NDI CHINTHU CHOFUNIKA KWAMBIRI PADZIKO LAPANSI.

Follow us here 👉 Mzebede
Titsatireni apa 👉 Mzebede
Siga nos here 👉 Mzebede

13/01/2026

BOMA LAGANIZA ZOLIPIRA 40% YA 13⁰ SALARY

Lero 13.02.26 mum'Ma hours apitawa pansonkhano wa olemba Nkhani, boma lalengeza kuti lilipira 40% ya 13⁰ Salary kwa ogwira ntchito m'boma, ndalaMayi yatsika ndi 10% polinganiza ndi yomwe inalipiridwa mu 2025.

Mlembi muundu wa zachuma bambo Amílcar Tivane ati, Mavuto azachuma omwe dziko lino likuyandamamo ndi omwe akudzetsa ntsetekowu.

ndalaMayi igwera mumaakaunti a ogwira ntchito m'bomawa mkatikati mwa miyezi ya January ndi February.

________________________________

Ogwira ntchito m'bomawa mwemweterani, zilowa ndithu.
____________________________________

Follow 👉 Mzebede
Kuti zofunikazi zidzikupezani mosavuta.

13/01/2026

Anthu ambiri atakuyang'ana, amaganiza kuti iweyo ndiwe pwepwete.
Unamadya kukutuwo ukugwere ndithu.

good morning

13/01/2026

A liberdade começa quando você corta a corrente.

(aqueles actos que TE deixam refém)

NGATI ULI MOYO NZOTHEKANTHAWI INAYAKE NDINAONAKO MPHONGO ITALUZA ZONSE :•Ntchito•Ndalama•Nkazi analongedza nkumapita.Cho...
13/01/2026

NGATI ULI MOYO NZOTHEKA

NTHAWI INAYAKE NDINAONAKO MPHONGO ITALUZA ZONSE :

•Ntchito
•Ndalama
•Nkazi analongedza nkumapita.

Chomwe chinandikhudza sikunali kuluza zinthu ayi koma:

_Uchete wake.
_Sanadandaule.
_Sanalozepo chala winawake.

Anangodzambatuka, zinthu nkuyambanso kutheka, inde mdima kusowa, kuwala nkudza.

Panopa alinso pathodzo:
-Ntchito yatsopano,
-Business yovaya
-Nkazi watsopano,
-Galeta latsopano

•Mwamuna weniweni sanyoka pa masamba anchezo.
•Mwamuna amakozanso moyo wake mwakachetechete.
•Amadzipanga kukhala Tonde omveka fungo.

Ambwana,Kaya ukudutsa munzotani, gobola, babada mitundayo, ndiponso phukira mwachimunu.

Kenako, tulukira Mwadzidzi.

Follow us here 👉 Mzebede
Siga nos aqui 👉 Mzebede
Titsatireni apa 👉 Mzebede

13/01/2026

no blood for lazy vampire...

12/01/2026

Kuchokera kwa Mphongo kupita kwa Mphongo

"Tisamamenyerane akazi iwe, AKAZI sanyamula Bokosi".

11/01/2026

Já está aí

🇪🇸 Barcelona XI: Joan García; Balde, Eric García, Cubarsí, Koundé; De Jong, Pedri, Fermín López; Raphinha, Lewandowski, Lamine Yamal

🇪🇸 Real Madrid XI: Courtois; Álvaro Carreras, Huijsen, Asencio, Valverde; Tchouameni, Camavinga, Arda Güler; Vinicius, Bellingham, Rodrygo

11/01/2026

ENTREGA TOTAL

"Uma coisa que muitos homens não sabem, é que, as mulheres mantêm as suas opções abertas mesmo estando em relacionamentos “sérios”.
Isso significa que, as mulheres continuam conversando com homens mesmo comprometidas ou casadas.
Os tais amigos, colegas, vizinhos são teus potenciais substitutos".
_______________________________________

Siganos aqui 👉 Mzebede

Endereço

Tete EN7
Tete
230

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Mzebede publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Compartilhar