Amayi awa tiwatengere ku khoti akafotokoze zikuoneka ngati ali ndi umboni😂. Nanga inu nanu a Brian Banda masten mwawafunsa funso nokha nanga chowakanizilanso kuyankha ndi chani?😂
Anthu ena akuti Sho Madjozi anachita kulembeledwa free style yapa Made On Monday. Chifukwa nde sizoonatu. Kuchita kumposa Charisma 😭
Anthu ena akuti Bakili Muluzi Tv ndi uyuyu akamunyamule ndipo asachedwechedwe. Koma akangomunyamula ma audios ena samachedwatu. Amakhala ma audios akutuluka munthu ali ku selo😂.
Nde muli intelligence eeh nde chikadzati "akulu akulu! Thomas Sankala anatha 3 days"? Nde nde nde Bakili Muluzi TV 😂😂
#Chinsapo
Anthu atanyamula bokosi akukuwa kuti mwana wathu mutibwenzere
Wanjinga iwe watiswa mtima😭😭
Anthu 26 onse apita. Zovetsa chisoni. Zomwe zachitika ku Kasungu!!!😭😭😭💔💔💔💔
Lulu kutenga microphone 🎤 mkuika mu boxer ku show ya Yo Maps. Kenako oyimba amzake anatenga mkuika kukamwa ayi zikomo😭
Mau osaiwalika omwe anayankhula Dr Saulos Klaus Chilima! May God be with his family.
Rip 😭💔😭😭
Akutitu anthu ndi asilikali akungoyenda mu nseu alibe zinthu zopangira Search. UTM team has joined the search. Why Malawi olo ndika drone komwe?
Ma video opatsa mantha ayamba kutuluka💔💔😟😟. Ati kumene ndege yagwera. #Chilima #Ndege #flight #Malawi #vicepresedent #chikangawa
Jetu analira mokweza atamuwona mwana wake patadutsa zaka 14 ali ku joni 🙆♀️🙆♀️🙆♀️. Kuyesa kumuchemelera kuti asalire kwambiri
ipondeni fadah.. thamangisa iwe ..ukuopa Chan kodi? uku akutukwana anthu oyenda pansi. Tithokoze Mulungu onse opulumuka palibe wafa. Pali turn pali turn kumalowelanso turn yolakwika osati yaku Chanco