Ku chitipa akuchikazi Alanda mutembo akuti sanayike ng'ombe aku chimuna nde malilo akasunga ku chikazi ayamba dzulo kulimbana mupakana aku chimuna agonja awasiyila ndipo aku chikazi anyamuka okha ntembo kukakweza mugalimoto koma zinazi ngati maloza
Meet Paranza hip-hop up and coming artist from Nzareka. Artist uyuyu amalimbikila osati masewela ndipo ndikhumbo lake atazafika pa Gwamba 🔥🔥
He has just released a new track titled "in Flames" ichichi wapha🔥🔥
Stream and download link in Comment section
Apulo akupeleka uthenga kwa nose ovala Dinda Dinda
Happy hour‼️
Challenge yafikapo iyi.
Mzuzu girls from Mchengautuwa nayo yati zisawaphonye
2025 wayambika, koma kufunika kukhalatu ndi wachikondi? Kodi mulinayo kale?
M Yoxy Mw akutulusa Nyimbo yachikondi mawa title yake Am in Love. Zaonereni limodzi ndi achikondi Anu.
Nyimbo ija Siya Joe Kellz dolo wake ndi uyu Jahmique 265 's latest love song "Serious" is taking the music scene by storm. Listen now⬇️⬇️⬇️
Link in comment section

Link in comment
Nyimbo ija Siya Joe Kellz dolo wake ndi uyu Jahmique 265 's latest love song "Serious" is taking the music scene by storm. Listen now⬇️⬇️⬇️
Amayi kukana 0.5 million yomwe anawapasa Madam Trephornia Mpinganjira
Amayi apa msika wa NJULI ku Chiradzulu kukana 0.5 million yomwe anawapasa Madam Trephornia Mpinganjira
Happy Hour‼️ ma styles akubedi
Happy Hour‼️ ma styles akubedi
Happy Hour‼️ pa 1st January, 2025
Happy Hour‼️ pa 1st January, 2025 kutsogolo kwa church.