Zest Skits

Zest Skits ๐ŸŽญSkit Maker/Actor.
๐ŸŒInfluencer.
โš™๏ธTech/Media Savvy. DM For Promo.Biz.Ads
(1)

Sindikonda kumvera nyimbo km na iyi yokha Eee "Ndkazakhala ndi ndalama ili si Thupi Langa"  ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ ๐ŸŽถ
21/02/2025

Sindikonda kumvera nyimbo km na iyi yokha Eee "Ndkazakhala ndi ndalama ili si Thupi Langa" ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ ๐ŸŽถ

muzik ProductionAudio: prod.Backstar &Alpha 265 beat by Jan cactus Video: Shot b...

20/02/2025

Kod mawa Lazaro mumufunsa funso lanji ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ tidziwe nawo

20/02/2025

Zafika poti ukagula chinangwa ogulisayo akumakupemphaso kt nditcholeleko ๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ™Œ๐Ÿ’”

18/02/2025

Ndinanenapo mbuyomu k*t panopa tizipanga mix za TV komanso ma comedy Ena... Ndee panopa m***a kuona tayamba maganizo anu ndi otani??? ๐Ÿ˜ฏ ๐Ÿ˜ฏ ๐Ÿ˜ฏ Tyankheni pliz

18/02/2025

Kungot ma Pic wo adyeka mwamva km nafenso timasamba iyaaa ๐Ÿ˜‚ Kungot Ndnatopa ndi chipongwe cha anthunu nkumati sitisamba ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚.. Km or kusamba Kuli apo maluzi ak*tiphwanya heavy
Mohammed Sbs

Camera man opita ku nyanja/party ๐Ÿ–๏ธ ๐Ÿ–๏ธ ndi maluzi ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ Mohammed Sbs musaone ngt tili ND 4n yojambula bwno ayi km adaw...
18/02/2025

Camera man opita ku nyanja/party ๐Ÿ–๏ธ ๐Ÿ–๏ธ ndi maluzi ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ Mohammed Sbs musaone ngt tili ND 4n yojambula bwno ayi km adawa amatha editing... Pic yo ndyodyeka Ndeee ndsamumve wina akt siikuoneka bho๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ

With Mohammed Sbs the camera man and editor [ photographer and videographer] get in touch with him... Mwina Ena simunamv...
18/02/2025

With Mohammed Sbs the camera man and editor [ photographer and videographer] get in touch with him... Mwina Ena simunamve uyo Ali ku manzere nd amene amatijambula komanso editing ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ Zikomo winayo ndiiii....... ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿคช ๐ŸคชPali wina wake amati sitisamba apa bwanj.. Km eeee tili ND maluzi ๐Ÿ’ต

Munthu wamkulu amene angamudziwe nd otitsata  okhaa ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ Mr TV Presenter. Km ati safuna zachibwana ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ akupereka moni ๐Ÿ”ฅ...
18/02/2025

Munthu wamkulu amene angamudziwe nd otitsata okhaa ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ Mr TV Presenter. Km ati safuna zachibwana ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ akupereka moni ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ Zest Skits

11/02/2025

Guys ndaganiza zogula plasma, yakhongo ikundizuza Ndeee timenye tsokhetsokhe. ๐Ÿ˜‚

11/02/2025

Ndee kwabwera ChezaFaya ๐Ÿ˜‚

Mukapeza mpata mupangeko subscribe to my YouTube channel https://www.youtube.com/Zikomo ๐Ÿ™๐Ÿฟ ๐Ÿ™๐Ÿฟ.
08/02/2025

Mukapeza mpata mupangeko subscribe to my YouTube channel https://www.youtube.com/
Zikomo ๐Ÿ™๐Ÿฟ ๐Ÿ™๐Ÿฟ.

ยฎ๏ธZestSkits Official Channelยฎ๏ธ ๐Ÿ“ŒComedian/Actor. ๐Ÿ“ŒInfluencer. ๐Ÿ“ŒTech/Media Savvy. โœ๐Ÿฟ . Please Don't Leave My Channel Without Subscribing. .Your subscription is Much Appreciated. . Am Here to Make Your Day & Show My Creativity.

07/02/2025

Nde pali anthu Ena uwaona alemba 'Kkkkkkkkkk' ngati mu phone mwawo Ma emoji mulibe ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚ ๐Ÿ˜‚

Kutapezeka anthu ngati awa angapo Eee Mellz Kumpanje ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ Thank you
06/02/2025

Kutapezeka anthu ngati awa angapo Eee Mellz Kumpanje ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ Thank you

06/02/2025

Sitonse tagwirizana kt tomato๐Ÿ…๐Ÿ… ali mgulu la ma precious stone๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ

06/02/2025

Ogulitsa tomato ๐Ÿ… ๐Ÿ… pano ndi blesser. ๐Ÿ˜‚

06/02/2025

Kungokhala ndi katundu uyu ๐Ÿ… ๐Ÿ… ๐Ÿ… or lobola akuchepera. ๐Ÿ˜‚

Address

Mangochi

Opening Hours

Monday 05:00 - 00:00
Tuesday 05:00 - 00:00
Wednesday 05:00 - 00:00
Thursday 05:00 - 00:00
Friday 05:00 - 00:00
Saturday 19:00 - 00:00
Sunday 05:00 - 00:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zest Skits posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share