Luntha television

Luntha television Luntha TV A Catholic Television located in Malawi. Promoting Spiritual and Integral development of the viewers.
(2)

17/01/2025

LUNTHA TV | LIKUNI GIRLS SECONDARY SCHOOL STUDENT SOCIAL WELFARE | 17 JANUARY 2025

17/01/2025

LUNTHA TV | NEWS UPDATES | 17 JANUARY 2025

Apolisi amanga mkulu waimodzi mwakampani zomwe unduna wazantchito unatseka lachinayi kamba konyalanyaza zomwe undunawu u...
17/01/2025

Apolisi amanga mkulu waimodzi mwakampani zomwe unduna wazantchito unatseka lachinayi kamba konyalanyaza zomwe undunawu unalamula. m'kuluyu ndi a Zhouh Youn Fei omwe ndimkulu wakampani ya NT plastics yomwe ili m'dera la Njewa.

M'mawa wa lachisanu nduna yazantchitoyi a Vitumbiko Mumba anapitaso kukampaniyo komwe anakapeza kuti kampaniyi imagwilabe ntchito zomwe kunali kunyozela pazomwe unduna wawo unalamula.

Ndunayi dzulo inatsekaso kampani ya Central Poultry ku Kanengo kaamba kosasamalila bwino malo ogwilila ntchito mwazina zomwe zimapeleka chiopsezo kwaogwila ntchito.

Wolemba Robert Edward.

17/01/2025

LUNTHA TV | PRESS REVIEW | 17 JANUARY 2025

17/01/2025

LUNTHA TV | KUGAWA MAU | 17 JANUARY 2025

17/01/2025

LUNTHA TV | DAILY MASS | 17 JANUARY 2025

 Tiwafunira zabwino Zonse Sr Tekla DzikoAchipani cha Tereza Oyera wa mwana yesu omwe akwanitsa Zaka 106 zakubadwa Lero.S...
16/01/2025



Tiwafunira zabwino Zonse Sr Tekla Dziko
Achipani cha Tereza Oyera wa mwana yesu omwe akwanitsa Zaka 106 zakubadwa Lero.

Sr Tekla anachita malumbiro awo oyamba Mchaka cha 1944, Ndipo anali mphunzitsi.

Iwo anaphunzitsako ku Bembeke, Likuni, chiphaso, Mpherere ndi Nambuma.

Pakadali pano Sr Tekla a kukhala ku Mlale ku Nurşing house Komwe kumakhala a sisteli achikulire

HAPPY BIRTHDAY Sr.

[Wolemba Bridgette Mwanoka]

16/01/2025

LUNTHA TV | ADORATION :Theme: "Oh woman, great is your faith. Let it be done for you as you wish." Mat. 15: 28 | 16 JANUARY 2025

16/01/2025

LUNTHA TV | NEWS | 16 JANUARY 2025

16/01/2025

LUNTHA TV | CHIDZULO | 16 JANUARY 2025

16/01/2025

LUNTHA TV | NKHANI MWACHIDULE | 16 JANUARY 2025

Mboni yachiwiri yambali yomwe ikuyankha milandu pa nkhani yokhudza wothandizira mtsogoleri wakale wa dziko lino, Mama Ci...
16/01/2025

Mboni yachiwiri yambali yomwe ikuyankha milandu pa nkhani yokhudza wothandizira mtsogoleri wakale wa dziko lino, Mama Cicilia Kadzamira womwe akulimbirana malo a Tichitenji Estate ndi banja la a Elias Kamphwiti Banda, ikupitila kupelekera umboni kubwalo la High Court ku Lilongwe pomwe oyimila a Kadzamira Khumbo Soko akuthambitsa mafuso mboniyi.

Mboniyi a Falles Kaphwiti Banda omwe ndi mkazi wa malemu Kaphwiti, mwazina ikunfusidwa ngati akudziwa zaka zomwe Mai Kadzamira anatenga umwini wa Tichitenji Estate.

Mfumu yaikulu Kawere ya ku Mchinji ndiyo inali mboni yoyamba lachinayi ndipo Kumbali yake Mfumuyi inati mkuvetsetsa kwake, zikalata zapamalo amafumu kapena amudzi (customary land) zimakatengedwa kuunduna wazamalo mafumu akapeleka malowo kwamunthu, koma mkudabwa kwake mama Cicilia Kadzamira anakatenga zikalata zamalowa pomwe T/A Kawele siidapatse malowo.

Apa Mfumuyi inati iyo mchaka cha 1966 inapeleka malowa kubanja la a Kaphwiti ndipo malowa ndi a banja la a Kaphwiti osati Mama Cecilia Kadzamira.

Wolemba Robert Edward

16/01/2025

LUNTHA TV | NEWS UPDATES | 16 JANUARY 2025

16/01/2025

LUNTHA TV | NEWS UPDATES | 16 JANUARY 2025

  The Government of Malawi, in partnership with the Presidential Taskforce on Public Health Emergencies, the Ministries ...
16/01/2025




The Government of Malawi, in partnership with the Presidential Taskforce on Public Health Emergencies, the Ministries of Health and Water and Sanitation, the World Health Organization (WHO), UNICEF, and other stakeholders, is set to launch the Malawi Multi-Sectoral Cholera Control Plan.

The launch, will be presided over by the Minister of Health, Honourable Khumbize Kandodo Chiponda, MP, and the Deputy Minister of Water and Sanitation, Honourable Liana Kakhobwe Munthali, MP.

Under the theme “Healthy Communities, Cholera-Free Lives: Let’s Work Together,” the initiative seeks to eradicate cholera in Malawi by 2030. The plan highlights a collaborative, multi-sectoral approach to addressing this persistent public health challenge, focusing on clean water access, improved sanitation, and community involvement.

[Reported by Bridgette Mwanoka]

Address

Luntha Tv, Area 2
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Luntha television posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Luntha television:

Videos

Share

Category