Shasha pamalawi

Shasha pamalawi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Shasha pamalawi, Digital creator, Lilongwe.

20/08/2024
20/08/2024

Ndipepesee popangaa iziii koma tremor keep rest in peace
Beat imeneyoo tasampulaa
Beat by Jay lubie ngati pali business hit me on 0991900750

Vacation star, JB ready to drop another hit today ๐ŸŽถNdinyimbo itii yomwe imakusangalatsa yabwanawa ?? Osaiwala kupanga li...
19/04/2024

Vacation star, JB ready to drop another hit today ๐ŸŽถ

Ndinyimbo itii yomwe imakusangalatsa yabwanawa ??

Osaiwala kupanga like this page

Confirmed :-  Queen Sheba akubwela kudzakhazikika ku Malawi September ameneyu pamene akuyamba campaign ya mpando wau M.P...
19/04/2024

Confirmed :- Queen Sheba akubwela kudzakhazikika ku Malawi September ameneyu pamene akuyamba campaign ya mpando wau M.P.

Iyeyu akudzayimila ngati independent M.P ku Lunzu mu 2025 moti alipa ndia Shado
Mawu Anu ndiotani kwaashado

Follow page imeneyi madzulo ano 7 o'clock tikhala tikugawa credit thanks

Sad:- Zachitika pompano chapa Kanjedza Assemblies. Minibus yo kaya inaluza ma break nkuphonya nseu kugwa nkugundanso mun...
17/04/2024

Sad:- Zachitika pompano chapa Kanjedza Assemblies. Minibus yo kaya inaluza ma break nkuphonya nseu kugwa nkugundanso munthu amene wamwalila pompo.

Anthu adali mu minibus mo avulala

Lelo gululu ndimamuna aligoneUyu ndi shasha Pamalawi mawu amodzi kwaiyee.
17/04/2024

Lelo gululu ndimamuna aligone
Uyu ndi shasha Pamalawi mawu amodzi kwaiyee.

Ma shasha odzitsataa
17/04/2024

Ma shasha odzitsataa

Compensation ipose apa ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜˜Follow shasha pamalawi
17/04/2024

Compensation ipose apa ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜˜
Follow shasha pamalawi

Shasha wanu uyu ndi Pick Poh. Ameneyu ndimnyamata wadzaka 24 ndipo tinganene kuti ndi half cast tunena izii Malingana nd...
17/04/2024

Shasha wanu uyu ndi Pick Poh. Ameneyu ndimnyamata wadzaka 24 ndipo tinganene kuti ndi half cast tunena izii Malingana ndimaonekedwe ake okopa anyway tamupangeni follow mwanayi mmenemu muli luso kwambi ndipo mayimbidwe ake ndiokoma kwambili mwanyimbo zomwe anaimba ndipo zopatsa mudyo ndi izii

1:Nane
2:Cant be again
3:Nacho
4:Pholoso ft Silence Platinumz
5:Tsoo
6:Wappa ft
7:Yalu ft Tammie
8:Monalisa
9:I don't fear like momy
Etcc.......
Mwa shasha ameneyu simuzakhumudwa
Follow shasha pamalawi

Kodi ndi angat akuidziwa nyimbo iyii!??Like Shasha pamalawi
17/04/2024

Kodi ndi angat akuidziwa nyimbo iyii!??

Like Shasha pamalawi

Monga shasha pamalawi aka timkakati ka hafu mkatii koma mkomwe kamkapengetsa azibambo amma 1984Nanjinanji ka red ๐Ÿ™๐Ÿ˜˜๐Ÿ˜‚
16/04/2024

Monga shasha pamalawi aka timkakati ka hafu mkatii koma mkomwe kamkapengetsa azibambo amma 1984
Nanjinanji ka red ๐Ÿ™๐Ÿ˜˜๐Ÿ˜‚

Onesimus Muzik Muzik Top 40 Songs1- Wayankha2-Ndele3- Miracle Money4- Ndirandileni5- Higher Higher6- Happy Birthday Papa...
16/04/2024

Onesimus Muzik Muzik Top 40 Songs

1- Wayankha
2-Ndele
3- Miracle Money
4- Ndirandileni
5- Higher Higher
6- Happy Birthday Papa
7- Ndamusowa
8- Sinditha Kumvetsa
9- I know
10- My Woman Ft Janta
11- Maria Ft Vusi Nova
12- Looking for somebody
13- Heavily defended
14- Foyu Ft Tekno
15- Easy baby
16- Anelisa
17- Here with me
18- Mr Nobody
19- Panado
20- Sugar
21- Ndilera
22- Ubwera
23- Sounds of peace
24- Solomon
25- Open your heart
26- Shekele
27- Hosanna
28- Testimony
29- Uthando lwakho
30- Superstar
31- Don't pass me by
32- This can only be God
33- Why do me so
34- Tshuku Tshuku (You make me feel)
35- Miracle worker
36- Overdue
37- Baba God
38-Messenger
39- Never beneath
40- Back to sender

1- Allergic
2-Controller
3- Don't pass me
4-Chigoba nkhanga
5- City Of Gold

What's your best song from Onesimus?

Ma juu bwerani Kaye tikambilane mesa phone mwandiswera kale  chifukwa Cha new number ndemukanaso kuzagona zoona ma juuFo...
16/04/2024

Ma juu bwerani Kaye tikambilane mesa phone mwandiswera kale chifukwa Cha new number ndemukanaso kuzagona zoona ma juu
Follow shasha pamalawi

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Shasha pamalawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share