Cuff-B

Cuff-B Malawian Recording Producer @ Big Vision Entertainment
Based in Lilongwe Area 49 Dubai African Music Producer from Malawi Lilongwe Area 49 Dubai.
(3)

25/12/2024

Muli ulemelero mukupemphedwa ndipo muli kugonjera mukupempha...

Pempho lanu ndilotani lero?
Mapemphero anu ndiotani kupempho lanulo? Mumapempha kwandani?

24/12/2024

Oyimba ena sadzatchuka
A mphawi ena sadzalemera
Olimbika ena sadzatukuka

Ena kumangolemerabetu
Ena one song atchukiratu
Business yomweyo ena amanga nyumba
Mulungu yemweyu madalitso osiyana.

Show yomweyo wina Million wina ampatsa tpt yokha...

Ena daily akugona panja pomwe wina wangotuluka kamodzi kokha wabwerako ndi Matenda.

Ngongole yofanana ena business yasintha giya zikuyenda pomwe ena sanabwenzebe ndipo anaduka....

Vuto ndi chani?

24/12/2024

Kuluza award sindekuti ndiwe kape .

Kusapangidwa nominate sindekuti palibe wapangapo chakachimenecho.

Choyambilira mudziyang'ana zomwe munapanga kuti mukwanilitse muchaka chimenecho ,zatheka kapena ayi,ngati award or nomination ili pa list then find out kuti amatengera chani ndipo mungatani to improve...

Award ndiyofunika kwambiri komanso ntchito yanu ija nde yopambana heavy Fada. Kuli anthu ena alibe award koma money akudya from the work they put in pa ground.

Stop looking at someone as a failure akapanda kuwina award. Ndipo opikisana nawo pa category aja si adani anu ayi unless zinalipo ndi kale. This is just entertainment and appreciation.

Kuli madolo kunjaku oti Malawi simawadziwa bhobho koma amadziwa ntchito yawo bwino. No award not famous etc.

Musafere award yokha fada.musafooke chifukwa simunawine Fada.

Big up to Maso Awards, Entertainers of the year Award for the work done this year .

Special Thank you to Story Club Red Carpet Event for Bringing in this thing . I have so much faith in what you are doing.
Tikupitatu forward ndi ngini yathu.

24/12/2024

Appearance of a woman gets a man's attention, personality will make him keep her and her Character will make him fall in Love.

23/12/2024

Kulemberedwa nyimbo is not a weakness,I help almost every artist I work with,sintha that line try this or that.

Chris Brown, Beyonce,Davido etc amalemberedwanso ndipo most professional artists got people who help them write or just write for them.

Udolo uli pokwanitsa kuimba zomwe walembweredwa zija ndikumveka bwino. Most artists Kwathu kuno don't go far because of poor writing skills.
Lyrics yopepukatu ,anali Dolo nthawi inayake koma pano sugar anathamo ndipo salora wina awathandize kulemba.

Anzathu omwe mwayamba kutsatira music coz of social media, dziwani kuti nzotheka ndipo nzofunika kulemberedwa nyimbo. Artist amatha kukhala ndi concept yabwino koma kuti imveke bwino ndi yolongosoka zimafunika writing skills.

Artist yemwe amalora kuti wina amulembere nyimbo ndi Dolo kuposa awo okakamira kulemba ekha ndikumabwatanso pa concept.

Ife timaitana guitarist kudzatiikira Guitar, Pianist adzaike Piano, Vocalist for backings etc kuti nyimbo itheke zomwe ndufuna. Ngati mukuona kuperewera mwainu chonde ask for help. Investing in Audio uja amakhala ndi zinthu ngati zimenezi fada....

Pangani nyimbo zolongosoka ndipo zopanda season....

22/12/2024

Invest more on your Audio first then put more effort in your videos to match Audio.

Video ingakongole bwanji just know ngati audio ili trash basi mwabetsa.
This is not to discourage shooting nice videos. Koma nyimbo ndi Audio ija zinazo nzongothandizira ndikusangalatsa omvera uja.

Audio 30k video 1 million kwacha 😂😂😂😂

Nanga ngati producer okuthayo akulipilitsa 30k ine ndingomupatsa yambiri? Investment yake ndiiti fada?

Mukamvere nyimbo za Diamond za kale nde musiyanitse ndi zapano.

21/12/2024

Off key koma mpaka kumusinzinira poyimba?

Ineyo sinditha kuimba koma at least ndimadziwa kuimba bwino...

Pali kulekana pakudziwa ndikutha kuimba. Ofunika kumazitsatira nginizi fada.

Another one fada from Sife mw called ChipereganyoProd by Cuff-B    Link in the comment section
20/12/2024

Another one fada from Sife mw called Chipereganyo
Prod by Cuff-B





Link in the comment section

Fada tiyeni tiponye Vote ija timalizitse ndipo mukakunga screen shot ya vote ponyani mu comment section Nkhondo tamenya ...
19/12/2024

Fada tiyeni tiponye Vote ija timalizitse ndipo mukakunga screen shot ya vote ponyani mu comment section

Nkhondo tamenya apa tingomalizitsa..

2024 has been great ndipo sitikufooka .

19/12/2024

Next year I will do this
Next year ndikwiya kwambiri ndipo sindifooka.

Next year ija ikafika fada plan yonse balala. Mumachulutsa lapulapu heavy nde mumakanika kuchita Ngini.
Anzanu akapanga zinthu Inu mumayamba kuphweketsa,timangodziwiratu kuti Jealous yavuta heavy.

Next year is coming ndipo mukamadikira kuti mudye money zonse mutapeze December ameneyu ma plan anu a next year adzakuvutani...

December is just like any other month. Samalani money Fada

19/12/2024

Kunali face to face nthawi imeneyo

Kunali kadya ubwelere

Add yours tikumbuke kale.

19/12/2024

Lankhulani chizungu lero Fada.

Chili chonse mumadziwacho

Cuff-B Made It!Aliyense pamalo pake Chete!!!!
17/12/2024

Cuff-B Made It!

Aliyense pamalo pake Chete!!!!

I say thank you to all the fans who voted for Chete as the Best Music Video of the Year @ The MBC Entertainer of the Year Awards. I really appreciate dis!

Special thanks to the whole Team on this project: Zeze Cuff-B Uchie_GangGang Seany Films Halfpast designs and everyone who participated in the Production of Chete! God Bless you all.

As usual I have something for you all this December! Ready up!

17/12/2024

I am ready for collaboration now
2025 will be full of such projects....

I have projects ready and looking for more....
Follow
BIG Vision Entertainment

17/12/2024
17/12/2024

The moment some women knew kuti akalira amamveredwa chisoni basi anayamba kuzipanga abuse heavy.

Nde anthu ambiri timapusitsidwa kwambiri ndikuliraku. I was one them ndipo chisoni sichimachedwa kundimbwandira but nzangozindikira zakuch njera kumeneko ndinasiya kumamngomvera chisoni aliyense olira to get attention.

Azimayi opempha ntowni aja eeeh muli skill. Nanji ankalowa m'bus aja ati andibera transport basitu kuyamba kulira mpaka mamina aaaaah.

Ndinaperekako some of my pocket money to help such a woman. Samalani ndi kulira kwa anthu enawa ndi trap fada....

Area 49 inali konko representing ProVoice Lameck Veda Njucci ELI Njuchi Chikondi Luv-christ Chisale
17/12/2024

Area 49 inali konko representing

ProVoice Lameck Veda Njucci ELI Njuchi Chikondi Luv-christ Chisale

15/12/2024

Growth hurts, it requires a lot of things to change, even if you need to change friends, partners.

Do not waste time guys ,you ain't got enough of it to waste. I was 25yrs old few years ago, now I am 65 samalani nthawi yanu. Use it wisely coz nde ikuthamanga heavy. Taonani za COVID-19 zija zinadutsa pano we are closing 2024.

Make sure whatever you are doing is growing. Business ya madzi ija ikule mpaka kumagulitsa ice blocks fada. Kaya mumagulitsa madzi omanga yambani Siludi aja (sealed)

Artists make sure you are growing numbers. Nyimbo zanu zizimveka kwa anthu oti akusunthani level. Work with producers oti akusunthani pomwe mulipo ndikufika pena.

Chaka chino aliyense ndaweka naye sali chimodzi modzi unless ndiokanika. Tonse Sitingapange ma hit but at least you made a good song with me. This very rewarding to me ndipo takankha Dancehall yanthu fada.

Next year we will do more than this coz we are not sleeping and we are not breathing (sitikupuma 😂😂😂)

Push it to the limit.

Big Vision!
BIGBIG Vision EntertainmentsBIG Vision EntertainmenttBIG Vision Entertainment

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Cuff-B posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Cuff-B:

Videos

Share

Category