Charxy Bandry

Charxy Bandry Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Charxy Bandry, Music Producer, Lilongwe.

Luso la manja, ngati mukufuna zithunzi zojambulidwa pamanja ndi pensulu ngati chimenechi. Link G Posh Art pa number iyi ...
16/11/2024

Luso la manja, ngati mukufuna zithunzi zojambulidwa pamanja ndi pensulu ngati chimenechi. Link G Posh Art pa number iyi 0987094255.

01/07/2024

One thing about Soldier Lucius Banda kwa ine chomwe ndizamukumbukile nacho, ndichoti, he was the first artist kumuone maso ndi maso ataima pa Jenda (a trading center I grew up). Adatsika mgalimoto yake nkutiyankhula, kutiweva nkutiimbila acapela song yake. Nthawi imeneyi nkuti ndili wachichepele. Ndidasangalara kwambili, chinali chinthu chachilendo komaso chosangalatsa.

20/02/2024
01/01/2024
The track you produced has been nominated ,click to vote. Araj pa Ntaj: BEST NASHEED 2023 You Can Vote Here : https://mu...
15/11/2023

The track you produced has been nominated ,click to vote.

Araj pa Ntaj: BEST NASHEED 2023 You Can Vote Here : https://muslimartsawards.com/contest/best-nasheed-2023/

year inawina ndakatulo ya Musa Ngwira, ya Alikuti adaphula dziko pamoto, yopangidwa produce ndi ine amene and this year yapangidwa nominate nyimbo ya Araj Pa ntaj, yochokelaso ku studio yomweyi. Tiyeni timuvotele

05/08/2023

Today with Afana Ceez in the studio, kuweka on a track titled Aku Naku,

Muli ma artist awa, Black Don, Papa Juxy, Afana Ceez, Brighto, Wiz A3ka & Lome98.

Charxy Bandry pa machine kulongosola ngini.

!

Coming soon
04/08/2023

Coming soon

Address

Lilongwe

Telephone

+265884765090

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Charxy Bandry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Charxy Bandry:

Share

Category