Madolo

Madolo 𝑴𝒂𝒅𝒐𝒍𝒐 π‘΄π’–π’π’•π’Šπ’Žπ’†π’…π’Šπ’‚ π‘·π’“π’π’…π’–π’„π’•π’Šπ’π’
(2)

Akutitu pang'onong'ono akanaphana ku Chiradzulu kokumbukila John Chilembwe pomwe ma sapota a UTM amatherana mau ndima sa...
15/01/2025

Akutitu pang'onong'ono akanaphana ku Chiradzulu kokumbukila John Chilembwe pomwe ma sapota a UTM amatherana mau ndima sapota a MCP.

Mmodzi wavulala pa chiwawazi ndipo amgoneka ku chipatala cha PIM Mission ndipo dzina lake ndi Geoffrey Kokana.

Ngakhale zimathero, akulu akulu azipani ziwiri amasekelelana Ali mweeeeee.

Fakani caption?Caption yomwe ikhale ndima likes ambiri pali ka bundle
15/01/2025

Fakani caption?

Caption yomwe ikhale ndima likes ambiri pali ka bundle

15/01/2025

Zokudya zabwino zikudibwa ndi apumbwa ku America

Happy Chilembwe Day from Madolo Multimedia. Uyu anali dolo
15/01/2025

Happy Chilembwe Day from Madolo Multimedia.

Uyu anali dolo

Cover the boss mu Blantyre, a police kuchuluka kuposa anthuπŸ™Œ
15/01/2025

Cover the boss mu Blantyre, a police kuchuluka kuposa anthuπŸ™Œ

Kwatuluka mundandanda wa maina uku.Alexious Kamangila akuti kaya kuli achina Wapona Kita, Khumbo Bonzo Soko, Prophet Bus...
15/01/2025

Kwatuluka mundandanda wa maina uku.

Alexious Kamangila akuti kaya kuli achina Wapona Kita, Khumbo Bonzo Soko, Prophet Bushiri, Triephornia Mpinganjira ndi hane wache, akuti onse mbamvaπŸ™Œ

Nde mma comment akuti ya Prophet Shepherd Bushiri siimuthera bwino, akuti ana apapa salora kuti dzina lao litchulidwe pa chabe.πŸ™Œ

Ife ku stand tiibekelele

Kwacha tiyeni ku Street Food tidzikacheza ndi 10May
15/01/2025

Kwacha tiyeni ku Street Food tidzikacheza ndi 10May

14/01/2025

Zana aboma anagundika kutionesa zithunzi zama thankala kuti mafuta akubwera through Tanzania.

Zulo mwati mathankala akukanika kudusa ku Mozambique.
Mkutitenga uchikape Eti?

Mongokumbusana, Molare The Rapper ndiwa Seventh Day Adventist. Ndi mesa ndithu.I come in peace ✌️
13/01/2025

Mongokumbusana, Molare The Rapper ndiwa Seventh Day Adventist. Ndi mesa ndithu.

I come in peace ✌️

PUBLIC AFFAIRS COMMITTEE YATI BOMA ILI LAKANIKAConclusion ikutiπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒA pulezisenti, tikudziwa kuti mbuzi Zina zibwera ku...
13/01/2025

PUBLIC AFFAIRS COMMITTEE YATI BOMA ILI LAKANIKA

Conclusion ikutiπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒ

A pulezisenti, tikudziwa kuti mbuzi Zina zibwera kudzakunamizani kuti zomwe takambilanazi msachite, komatikuwuzeni moopa mulungu, boma Ili mwalephera kuyendesaπŸ™Œ

Chasala ndi mabonya okha okhaπŸ˜„πŸ˜„ PAC 2025

13/01/2025

Kuli challenge uku, muilowa kapena za uhule simmapanga nao

A shadow MP a ku Lunzu awa nawonso akufunika ku Truth or Drink, adzatiuze kuti opempha ndi angati, ndipo ma celebrity an...
13/01/2025

A shadow MP a ku Lunzu awa nawonso akufunika ku Truth or Drink, adzatiuze kuti opempha ndi angati, ndipo ma celebrity anadyamo ndangati.

Wangomvala t shirt no pant I mean no skirt. Koma ichi nvhooneka bwino

Ichi nde chasandukatu chakudya chagulu, akuti 2 days akhalira mu industry mu, anthu otchuka 8 ampemphapi kuti adye, koma...
13/01/2025

Ichi nde chasandukatu chakudya chagulu, akuti 2 days akhalira mu industry mu, anthu otchuka 8 ampemphapi kuti adye, koma 3 ndamene adya kale Moti. Ndekuti athe chaka?

Welcome to chopwizo

13/01/2025

Arsenal ndi nchabwa wa team.

NDE MWATI MAN UNITED SIIWINA LERO?MATCHDAY: Arsenal vs Manchester United πŸ†FA CUP⌚5PMπŸ₯…Emirates Stadium
12/01/2025

NDE MWATI MAN UNITED SIIWINA LERO?

MATCHDAY: Arsenal vs Manchester United
πŸ†FA CUP
⌚5PM
πŸ₯…Emirates Stadium

Inu a Mellz Kumpanje tamangolembani zichewa zomwezi nzomwe munatchukila, zizungu mtichedwetsa nazo fotseki.Good morning ...
12/01/2025

Inu a Mellz Kumpanje tamangolembani zichewa zomwezi nzomwe munatchukila, zizungu mtichedwetsa nazo fotseki.

Good morning madolo

Kwambiri timthokoze mulamu Sangie povomeleza kuti wathuyi Malinga Mafia akajambule video ya "You and I" yomwe anayimba n...
11/01/2025

Kwambiri timthokoze mulamu Sangie povomeleza kuti wathuyi Malinga Mafia akajambule video ya "You and I" yomwe anayimba ndi Jahmiel.

Mlamu mkaladi uja, sakanalora kuti Malinga apite ku Ghana kukajambulitsa nyimboyi, akanakadyera Pizza iyi.

Lero, Malinga walengeza kuti ajaambula video ya nyimbo ya 'You and I' ndipo itukuka posachedwapa.

Mpaseni like wake Sangie

Third Eye ndi ovuta kulera aaaa
11/01/2025

Third Eye ndi ovuta kulera aaaa

Address

Lilongwe

Telephone

+27786221611

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Madolo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Madolo:

Videos

Share

Category