Troy MW

Troy MW Artist Musician
(2)

Ma phone ADula Cash Simungakwanitsé Kupeleka, Komaso Kusungila Ndalama Kukuvuta ! Osaopa Ife Ma Phone Opeleka Pa Ngongol...
04/09/2024

Ma phone ADula Cash Simungakwanitsé Kupeleka, Komaso Kusungila Ndalama Kukuvuta ! Osaopa Ife Ma Phone Opeleka Pa Ngongolé Nde Tikupitilizabe Kukutulutsilani !

Pali Ka
Spark 20
128.GB Spaces

Tipezeni Kuma Shop Athu Mudzatenge Pa Ngongolé!

Timapezekaso Ndima Itel 👍🏿💥

# 0994468474
# 0883252620. Whatsapp Or Calls 📞

Ndi Momwe A Dulila Ma phone Panopa Si Aliyense Amene Akukwanitsa Kukatenga Pa Counter Mwa Cash ! Ena Akupeza Mwayi Pa Ng...
29/08/2024

Ndi Momwe A Dulila Ma phone Panopa Si Aliyense Amene Akukwanitsa Kukatenga Pa Counter Mwa Cash ! Ena Akupeza Mwayi Pa Ngongolé!

Itel S23
128 GB space

Ti Haleni Pa Whatsapp Mumve Ndondomeko Zake Osaopela Kutali💥

# 0994468474
# 0883252620

Kwa Omwe Ali Ofunisitsa Kukhala Ndi Phone Ya Bwino Pa Ngongole Atenge Nawo Katundu Wabwino Uyu...Itel A7012.GB Ram128.GB...
28/08/2024

Kwa Omwe Ali Ofunisitsa Kukhala Ndi Phone Ya Bwino Pa Ngongole Atenge Nawo Katundu Wabwino Uyu...

Itel A70
12.GB Ram
128.GB Space

Halla Me On Whatsapp Timvane Business Yosabelana

# 0994468474
# 0883252620

Ngati Dollar Zokatengéla Phone Ya bho pa Cash Mulibe Koma Mukufuna Kupeza Phone Ya New ! Pali Mwayi Oti M***a Kupeza Pho...
27/08/2024

Ngati Dollar Zokatengéla Phone Ya bho pa Cash Mulibe Koma Mukufuna Kupeza Phone Ya New ! Pali Mwayi Oti M***a Kupeza Phone Pa Ngongole Nkumapeleka Wezi Wezi Kwinako Muku Gwilitsa Ntchito Phone Yanu !
Timapezeka Ndima phone mitundundu Yonse Yomwe Mukuyidziwayo

Ndiyimbileni Ngati Mukufuna Kupeza Yanu :

0994468474
0883252620

26/08/2024

KUIPA KOKWATIRA / KUKWATIWA:
- kulibe ufulu ometa mavuzi ku banja. Siungamete mavuzi popanda kumuuza mzako.😂🏃

Timafuna Tingoku Dziwitsani Kuti Kunja Kuno Kwabuka Chi Nyimbo Cha Huster Waiting For Your 👋🔥
24/07/2024

Timafuna Tingoku Dziwitsani Kuti Kunja Kuno Kwabuka Chi Nyimbo Cha Huster Waiting For Your 👋🔥

19/07/2024

Ati Dzikhede Khede 😀

28/06/2024

Mercy akazanga atenga number yako akakuyimbila unenekuti ndiwe Ogulitsa ma tissue wava..🙈

17/06/2024

Bola Iweo Mwana Wa Chilima Bambo Ako Akusiyira Chuma Koma Ife Adati Siyira Dzikombole....😭😭

14/06/2024

Kunjaku nde kwatapidwa ma Screenshot,
Bola ikafika nthawi yopelekera umboni tisazamalankhule chibwibwi.🙌🙌😀

08/06/2024

Azimayi Thawi Zina kumaselewunarako Ndamunanu Tayesani Kuwauza Kuti Dad Mwana Oyamba Siwanu..😅

04/06/2024

Dzulo ndinagwira ntchito yaulele 🙄🙄Komanso kubetsa 2pin 🙇🙇

Ndinali phee Ku barbershop kwanga kudikilira ma customer, mwamwayi ndinaona bambo wina atabwera ndi mwana wake.

Ndinameta bamboyo style imene amayifuna, kenako anati bwana tamamumetani mwanayo ndikubwera Kaye,mundipatse 2pin ndiperekera limodz ndikamamutenga mwanayu.

Ine ndinatenga 2 pin kumupatsa m'bamboyo kenako kumamumeta mwana uja.

Chodabwitsa panadutsa 2 hours bambo uja asanatulukire, mwana uja nditamumaliza Kale Kale, ine mtaona kuchedwa ndinamufunsa mwana uja kuti bambo ako aja atalikira eti?

Mwana anayankha amvekere SI BAMBO ANGA AMENE AJA.

ndimafunsa ndiye ndi ndani ako?

Mwana anati....ANANGONDITENGA PA MSEU NDIKUSEWERA NDI ANZANGA KUNDIUUZA KUTI TIYE UKU TIKAMETESE ULELE KOMA SINDIKUWADZIWA..

🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄Abale mwanayu mtani naye😭😭

03/06/2024

Ouma ❤💥

Ndinali M'nyamata osam'dziwa mkazi chikhalire ndipo pa nkhani ya akazi sindimakambapo Chifukwa sindimadziwa kuti ndingamatani naye mkaziyo.

Nditafika zaka 34 opanda mbiri iliyonse makolo anga ndi abale anali nane nkhawa kuti kapena wathuyu kalulu anamudutsa m'phechepeche? Mwaicho anandisakira mkazi kuti ndikwatirane naye.

Usiku wathu oyamba kugonera limodzi ndinaona ngati malodza🙄, mmene ndimafika ku bedroom, ndinapeza mkazi wavula ali buno bwachoncho🙈🙈 ndinali wamantha Chifukwa kunali kuyamba kuona munthu wamkazi asanavale.

Mkazi anandiyang'ana mwachilendo ndipo anati, ukudziwa chomwe ndikufuna? Ine ndinati mmm ayi sindikudziwa. Mkazi anandihaga kenako anandifunsa ukudziwa chimene ndikufuna? Ine ndinati mmmm ayi.

Mkazi anagona pa bed ndipo anafunsa ukudziwa chimene ndikufuna? Ine ndinati mmmm ayi ....mkazi anatambasula mendo yake wina ukooo wina ukoooo kudzadza pa bed ponse ndipo anati ndikukhulupira wadziwano chimene ndikufuna eti? Ine ndinamwetulira😄😄ndipo ndinati eya eya ndadxiwano chimene ukufuna ....ukufuna ugonepo wekha pa bed po osadanda ndikagona chipinda china🙈🙈🙈

03/06/2024

Anangoti Muvuleni Boxer Apitidwe Mphepo , Ine KudzidziMuka Kunali Komweko..🤕

03/06/2024

MINYAMA😂😂

Ndinaweruka ku ntchito ndinafikira kukhala pansi, kenako ndinaitanitsa madzi okumwa, madzi asanabwere mwana wanga anabweretsa school report ine kuona🙆

Biology 17%
Chemistry 26%
Geography 12%
Economics 20%
English 30%
Mathematics 7%
Chichewa 41%
Bible knowledge 2%

Sinapitilize kuona zotsatira zonse mopsa mtima ndinayamba kukalipira mwa m'nanu mwana wangayo

Mayi ake anayesera kundidekhetsa koma ndinawadzadzira mwamkwiyo ndipo ndinati....mwanayi mukumulekelera ndichifukwa sakuchita bwino ku sukulu taonani tsopano zotsatira zomwe akubweretsa pakhomo pano? Ndindani ku mtundu wanu kapena ku mtundu wathu anabweretsapo zotsatira zochititsa manyazi chotere?

Mwana wanga uja anati...adad taonetsetsani school report lo bwino bwino......si zotsatira zangatu koma ndi zotsatira zanu za mu chaka cha 1993 kungoti ndaipeza mu drower ndikukonzamo ndiye ndimafuna ndikufunseni kuti ndiyitsungebe izifunikira?

Ine.😳😳🙆🙆

😅

Address

Area 41
Lilongwe

Telephone

+265993748592

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Troy MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Troy MW:

Videos

Share