Mpumulo Services

Mpumulo Services Mpumulo is a Malawian online platform for tributes and dedications to the dearly departed. Ndondomeko zonse zidzatsatidwa. Terms and Conditions Apply.

To submit a memorial profile, simply follow the instructions on our page. Ntchito yathu ndikupereka mwayi komanso malo pa internet pomwe mungaikepo mauthenga a chikumbutso cha abale otisiya, ngati muja amaikira mma newspaper pamtengo wosaboola mnthumba. M***a kutumiza chithunzi komanso uthenga umene mukufuna kuika pokumbukira wachibale kudzera pa ma number athu a WhatsApp motsatira malangizo amene aperekedwa pa tsamba lino. Mpumulo Services- their life, our memories

17/02/2022
A sample of how memorial profiles will look like at mpumulo.com. All you have to do is send us a picture and a text mess...
16/02/2022

A sample of how memorial profiles will look like at mpumulo.com. All you have to do is send us a picture and a text message in the language of your choosing and the Mpumulo team will take care of the rest. Mtengo ndi 1,500 Malawi Kwacha per profile.

In the age of the internet, we offer a digital space for tributes and remembrance away from the traditional newspaper cl...
16/02/2022

In the age of the internet, we offer a digital space for tributes and remembrance away from the traditional newspaper classified ads. Our service will be launched soon, but we have opened the channel for submissions of memorial profiles at a reasonable opening flat fee of 1,500 Kwacha per profile. A sample profile is shown in the picture.

You can submit a picture and the message you would like posted on mpumulo via WhatsApp: 0984665526/ 0886073908
Mpumulo-their life, our memories.

Kale zinkaikidwa mu nyuzipepala, lero tikuyamba kuika pa website kudzera pa mpumulo, website imene ikhazikitsidwe posach...
16/02/2022

Kale zinkaikidwa mu nyuzipepala, lero tikuyamba kuika pa website kudzera pa mpumulo, website imene ikhazikitsidwe posachedwapa.

M***a kutumiza uthenga ndi chithunzi cha abale okondeka amene adatisiya kuti zidzakhale mu gulu loyamba kuikidwa pa website yachikumbutso imeneyi mmene mukuonera mu picture taika apayi. Kwa gulu loyamba lonse, mtengo ndi 1,500 Kwacha pa profile iliyonse.

Ma number omwewa ndiomwenso ali pa WhatsApp.

Airtel Money: 0984665526
Mpamba: 0886073908

Mpumulo- their life, our memories.

14/02/2022

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 07:00 - 17:00
Tuesday 07:00 - 17:00
Wednesday 07:00 - 17:00
Thursday 07:00 - 17:00
Friday 07:00 - 17:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mpumulo Services posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share