Zathu zomwe Mwi

Zathu zomwe Mwi In this group do not writte venacular language because many pple are elders here

02/11/2024
FAMU YOGULITSA iyi ndifamu yomwe ikugulitsidwa pamtengo wokambilana 13.5 On map +7yekazi .failo yafamuyi ilipo 4n 098553...
23/02/2024

FAMU YOGULITSA iyi ndifamu yomwe ikugulitsidwa pamtengo wokambilana 13.5 On map +7yekazi .failo yafamuyi ilipo 4n 0985533557

Unlocking Abundant Harvests: Unconventional Gardening Tricks RevealedFull article in the first comment πŸ’¬πŸ‘€
23/02/2024

Unlocking Abundant Harvests: Unconventional Gardening Tricks Revealed
Full article in the first comment πŸ’¬πŸ‘€

03/06/2022

Kayoyo ndiyankhuleni

21/05/2022

Mawa Trip yopita kukampala ground linga transport K2000 yokha bas tiyeni tipite kumeneko

28/11/2021

Tidya ochepa Xmas

28/11/2021

Mnyamata wina wanyongedwa atamenya alandrod amzake panopa Ali mchitokosi cha a police 😭😭😭😭😭😭 like it mumve zambiri

28/11/2021

Welcome πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘

28/11/2021

Kayoyo oyeeeee !!!!!! Zodabwisa sizizatha muu B13 today (lero) bar man wa Mr mwiniwake bala wapandidwa ndi ogula mowa wina now like it kuti mumve zambiriπŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…ndayimika manja mmwambaπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

06/09/2021

Zikomo nonse muno sitinakuyiwaleni ma post akubwer

30/03/2021

B 13 ON FIRE

24/03/2020

Koma corona virus wathetsa nzeru anthu anzeru zawo.. Pakadali pano President wa Ku south Africa Lamaphosa walamula kuti kuyambira pa 26 March mpaka pa 17 April pasapezeke munthu otuluka mnyumba kaya komwe amakhala mkumangoyenda kuja, kupatula achipatata omwa asankhidwe ndi boma.Iwo ati opezeka akuphwanya lamulo ili amangidwa. Nako Ku Tanzania President Magufuli wakanitsitsa kuti satseka ma church chifukwa akukhulupilira kt muliliwu ukutsogozedwa ndimphamvu ya mdyelekezi.President yu wanenetsa kuti ndipemphero lokha lingagonjetse muliliwu..Mulili wavuta uwu!!chonde

09/03/2020
30/01/2020

Guys kwainu amene muli muno tmasukirane zomwe aliyese amakonda,inee ndeee ni maaaabe

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zathu zomwe Mwi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Zathu zomwe Mwi:

Videos

Share

Category