Asokonezi

Asokonezi Person who likes kucheza

Koma iweyo wati ulibe ndithu
19/11/2024

Koma iweyo wati ulibe ndithu

Nelson Banda yemwe ndi Monitor wa chipani cha Malawi Congress(MCP) waulura kuti ma Monitor a MCP okwana 500 mu chigawo c...
30/10/2024

Nelson Banda yemwe ndi Monitor wa chipani cha Malawi Congress(MCP) waulura kuti ma Monitor a MCP okwana 500 mu chigawo cha pakati adapatsidwa zaunzika za ana osakwana zaka 18 kuti athandize kuwalowetsa mu kaundula wa mavoti kuti adzavote nawo chaka cha mawa.

Ma Monitor 300 a chipani cha MCP mchigawochi akwanitsa kugwira ntchitoyi bwinobwino osagwidwa.

Koma ziliko ziliko hehehe🀣🀣🀣🀣,ndione kae ngati sunavale padπŸ™†πŸ™†
27/10/2024

Koma ziliko ziliko hehehe🀣🀣🀣🀣,ndione kae ngati sunavale padπŸ™†πŸ™†

Haaamayoooo hineeee 🀣🀣🀣🀣😭😭😭
27/10/2024

Haaamayoooo hineeee 🀣🀣🀣🀣😭😭😭

22/10/2024

Ati ma Beans nes asiya kuyanika??πŸ™„πŸ™„ Ayi kungoti nanga ndidziona ndekha?? Auzeni azanuwo apanga like/follow page inoyo

Pomwe afika   pano.ma report akuti bamboyu wathiridwa madzi otentha ndi mkazi wake pa zifukwa za mbanja. : azimai mamuna...
09/10/2024

Pomwe afika pano.ma report akuti bamboyu wathiridwa madzi otentha ndi mkazi wake pa zifukwa za mbanja.
: azimai mamuna simwana wanu,bambo anu kapena mtundu wanu iyayi.amunafe ngati tikupanga zinthu zosakusangalasani koma mwatiuzapo kochuluka sitikusintha,chonde tilekeni, inuyo nyamukani mudzipita kwanu mulinako ndipo makolo ndi azibale anu akakulandirani.koma mukamafika apa ngati munabereka ndinu mmm πŸ€” app ndie mukulakwisa ndipo kungochira apapa straight iweyo chifukwa uli ndi moyo wakwaipa πŸ’”πŸ’”, ndakwiya,😑.

Kodi mukatere mumapindula chani??tell me guysπŸ™„πŸ™„πŸ™„πŸ™„
06/10/2024

Kodi mukatere mumapindula chani??tell me guysπŸ™„πŸ™„πŸ™„πŸ™„

Chonde siyani kutchukisa anzanu pa nkhani  ..kumati   wapakulitsa aaaa   kuonera ka 7 koma sindikuona iyeyo coz nkhope p...
06/10/2024

Chonde siyani kutchukisa anzanu pa nkhani ..kumati wapakulitsa aaaa kuonera ka 7 koma sindikuona iyeyo coz nkhope palibepo.inu munamudziwa bwanji??tiuzeni, ngati ija simunaonerere tiuzeni mu comment box ikupezani.

05/10/2024

Ati azimai kodi Beansnes chomayanikira ndi chani?? kapena ya fresh simafufuma eti??πŸ™„akuti aneba zikuwabowa amati ndiwayankhulire

Address

Kasungu

Telephone

+265991099379

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Asokonezi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Asokonezi:

Share

Category