House Tv

House Tv Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from House Tv, Newspaper, Box 2115, Blanytre, Blantyre.

27/11/2024

Tikamamva kuti nziko muno muli njara ndizoona ndithu zikafika pazakudya umunthu ukumachoka

Pamene amalawi akhara akudikira mayakho pa nkhani zomwe zakhara zikuchitika mdziko muno  Lero pa 27 November President w...
27/11/2024

Pamene amalawi akhara akudikira mayakho pa nkhani zomwe zakhara zikuchitika mdziko muno Lero pa 27 November President wa dziko lino Dr Lazarus McCarthy Chakwera akhara akuyakhula kwa Mtundu wa a Malawi lero madzuro ano Nthawi ya 8 koloko.

A malawi alindi chidwi ndi khaniyi chifukwa akufuna kunva zomwe Mtsogoleri yu akufuna Kuyankhula madzuro ano.

Once upon a time there was a Zimbabwean ríchest young man called "Genius Ginimbi Kadungure" Mbinga 1 BhuruHe once booked...
25/11/2024

Once upon a time there was a Zimbabwean ríchest young man called "Genius Ginimbi Kadungure" Mbinga 1 Bhuru

He once booked DJ Maphorisa and DJ Tira to Watch him have breakfast with his girlfriend.

Imagine booking two big artistes to watch you have breakfast and paying them millions .

Ku Lilongwe kwavuta ndipo mademo alinkati ngakhare a police akuvunga utsi okhesa misonzi
25/11/2024

Ku Lilongwe kwavuta ndipo mademo alinkati ngakhare a police akuvunga utsi okhesa misonzi

22/11/2024

Hadson Chamasowa and Che Mandota

21/11/2024

zikuonesa kuti ubale wawo uli bwino!

18/11/2024

Ndikuona ngati Flames yayamba kuwina panopa sopano

Celebrating my 1st year on Facebook. Thank you for your continuing support. I could never have made it without you. 🙏🤗🎉
18/11/2024

Celebrating my 1st year on Facebook. Thank you for your continuing support. I could never have made it without you. 🙏🤗🎉

Address

Box 2115, Blanytre
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when House Tv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to House Tv:

Videos

Share

Category