12/12/2023
OSAMA BIN LADEN PART 4
mbiri ya OSAMA BIN LADEN
tipitilize pamene tinalekezera mu part yathu yammbuyo
mu part 3 tinalekezera pamene BALACK OBAMA anasankhidwa kukhala president wa dziko la America ..
BALACK OBAMA analonjeza dziko la America kuti amusaka ndikumupha OSAMA BIN LADEN ๐ฅ
โโmu part ino tiona imfa ya OSAMA BIN LADEN
dziko la America linayesetsa kufufuza malo amene OSAMA BIN LADEN amakhala koma limkanika .
nthawi imenei mkuti osama akukhala malo ena kumalire adziko la Afghanistan ndi Pakistan ku Federally Administered Tribal Areas,
malo amene OSAMA amakhalako samalola anthu ena achilendi kufikako popanda chilolezo
OSAMA ndi amzake a gulu lake anali ndi mawu kapena kuti chiyankhulo chawochawo chimene amagwilitsa ntchito polimikizana
komanso nthawi zambiri amakonda kulankhulana pogwilitsa ntchito makalata ndipo kalata imeneyo ikawerengedwa imaotchedwa pompopompo.
OSAMA amachita zimenezi pofuna kuti adani awo asamadziwe za mamishoni amene ali nawo
OSAMA BIN LADEN anaphwedwa pa 2 mwezi wa may mchaka cha 2011 .
OSAMA anaphwedwa ndi gulu la nkhondo la dziko la America lotchedwa kuti special operation unit ndipo mishoni yokapha osama amaitchula dzina lakuti operation Neptune spear .
IMFA YAKE ๐ฅบ
osaiwala kupanga follow ๐๐ฟ Troy MW
dziko la America linatumiza ndege mdziko la Pakistan zimene zimkajambula chilichose chimene OSAMA akuchita komanso malo enieni amene amkakhala .
kenoko dziko la America linadziwa kuti silingathe kumugwila OSAMA BIN LADEN palokha ndipo linapanga mgwilizano ndi dziko la Pakistan .
mdziko limeneli la Pakistan, anapanga ubale ndi Ahmad Shuja Pasha .
Ahmad Shuja Pasha , anali wakulu wa asilikari amdziko Pakistan mnthawi imeneyo .
ndipo Ahmad Shuja Pasha amkalipilidwa ndalama pafupifupi $25,000 million ndi dziko la America.
Ahmad Shuja Pasha komanso asilikari ena a mdziko la Pakistan anayesera kumusakasaka OSAMA BIN LADEN koma nawoso amkalephera kupeza malo enieni amene amakhalako .
OSAMA BIN LADEN amka