Nkhalango Multimedia

Nkhalango Multimedia We are Professionals in TV/Radio Adverts, Documentaries, Film Production, TV/Radio Programs, Graphic Designing, HD Photography, Screen Printing and many more.
(2)

We are Affordable with Best Quality.

Happy John Chilembwe Day
15/01/2025

Happy John Chilembwe Day

TONDE WADULA EPISODE 137
14/01/2025

TONDE WADULA EPISODE 137

TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 137

13/01/2025

TONDE WADULA EPISODE 137
KOMA CHIMENE ANAYAMBANA GAGA NDI MAYI PHIRI NDICHACHIKULU - Wonerani Episode yonse pa YouTube kudzera ku Link iyi: https://youtu.be/K_JJv7c8Bfs

13/01/2025

Komatu Episode ya lero mukanaguliratu bundle. Chifukwa ndie kuli zinthu.

11/01/2025

MWAYI WOKHALA ACTRESS/ACTOR MU TONDE WADULA.

Kwa amene amaziimba kuti atha kuchita Zisudzo za pa Kanema, kuli mwayi wa munthu m'modzi weniweni.

Tikufuna msungwana wa zaka zapakati pa 24 ndi 30 komanso anyamata awiri a zaka za pakati pa 27 ndi 35 kuti azizajambula nawo sewero la Tonde Wadula koma akhale okhala madela ozungulira Bangwe monga ku BCA, Namiyango, Bangwe, Chigumula, Kachere, Mpingwe ndi Nachamba.

Tumizani uthenga wanu osonyeza chidwi chofuna kupanga nawo zisudzozi ku number iyi: 0881467765.

Asikana 5 komanso anyamata 10 a mphumi azasankhidwa kuzachita ma Auditions ku office ya Nkhalango Multimedia ku Bangwe.

Wishing you all the Best.

10/01/2025

NKHANI ZATHU M'MAWA UNO;

1. Bambo wina yemwe akuti sakudziwika kwawo, wapezeka atafa m'mbali mwa nsewu ku Makwasa m'Boma la Thyolo.
Bamboyu yemwe akuwoneka kuti wapangidwa chiwembu ndi achifwamba, wapezeka kucha kwa lero, ali ndi mabala achikwanje m'mutu komanso kunsana. Koma chodabwitsa ndi chakuti, bamboyu wapezeka ndi ndalama zokwana 46,500 m'thumba la buluku lomwe anavala komanso foni ya mtundu wa Nokia 3610 koma yothima ndipo munalibe sim card.

Ena akuganiza kuti bamboyu mwina watemedwa ku Chibwenzi kapena kokuba, ngakhale kuti chanicheni sichinadziwike.

2. Gogo wina wa zaka 66 zakubadwa, wapha Mayi ake omubereka omwe akuti ndi a zaka 84 powagogoda ndi nyundo pa liwombo.

Gogoyu yemwe akuti amakhala limodzi ndi Mayi akewo, anayamba wakautunga Kaye mowa kuti achotse chisoni ndipo atafika usiku anangofukira kudzwanya mutu wa Mayi akewo omwe anali mtulo pa nthawiyo.

Malingana ndi omwe atipatsira nkhaniyi, anthuwa akhala akutsemphana kwa kanthawi. Anthu okwiya a m'mudzi nawo amafuna angopheratu gogoyu koma achisoni anayimba phone ku Police ndipo apolisi anathamanga kuzapulumutsa gogo wakuphayu.

3. Mnyamata wina wa zaka 14 zakubadwa, ali mu ululu waukulu kumalo obibila pomwe bambo wina wa zaka 34 wamuchita chipongwe pomugwililira.

Mnyamatayu yemwe amakhala moyandikana ndi kunyumba kwa mkulu wachipongweyu akuti anatsemphana maganizo ndi makolo ake ndipo apa mkuluyu anatengerapo mwayi popempha makolo a mnyamatayu kuti amutenge akamulangizire kwawo ndipo mphuno salota, makolo a mnyamatayu anavomera. Uko ndi komwe chilangizo chinadzambatuka komatu choopsa chifukwa tikunena pano mnyamata akukanika kukhala pansi.

Atazindikira kuti nkhaniyi ivuta, bambo wachipongweyu anathawa ndipo a polisi akumudakasaka.

Nkhani zathe m'mawa buno ndi zomwezi.

Bye Bye!

10/01/2025

Good morning from Mpanje

LA 40 DRAMA SERIES Starting on 30th of January, 2025 and Every Thursday from 8:30pm, repeat on Saturday at 2pm on TIMES ...
09/01/2025

LA 40 DRAMA SERIES
Starting on 30th of January, 2025 and Every Thursday from 8:30pm, repeat on Saturday at 2pm on TIMES TELEVISION and Nkhalango Multimedia YouTube Channel.

Get Ready.

LA 40 DRAMA Series Kuyambira pa 30 January, 2025.Iziwonetsedwa Lachinayi lililonse nthawi ya 8:30pm komanso kubwelezedwa...
09/01/2025

LA 40 DRAMA Series
Kuyambira pa 30 January, 2025.
Iziwonetsedwa Lachinayi lililonse nthawi ya 8:30pm komanso kubwelezedwa Loweluka 2 koloko Masana pa TIMES TELEVISION

Something you can not afford to miss.

Amuna tsopano pa Mtondo,Writer |  Producer | Cinematographer |  Director and  Editor of TONDE WADULA.Muyankhuleni mkuluy...
09/01/2025

Amuna tsopano pa Mtondo,
Writer | Producer | Cinematographer | Director and Editor of TONDE WADULA.

Muyankhuleni mkuluyu!

09/01/2025

Amene muli ku Mozambique tiyankhuleni, Zikuti bwanji kumeneko?

Muthinda Wangoona kukhala bwana koma akazi akumuthawa, mukuganiza kuti vuto lake ndi chani?
09/01/2025

Muthinda Wangoona kukhala bwana koma akazi akumuthawa, mukuganiza kuti vuto lake ndi chani?

Muli naye mawu ngati?This is Mollen Chinaga ndipo mu Tonde Wadula amadziwika ndi dzina lake "MOLLEN". Munayamba mwawoner...
09/01/2025

Muli naye mawu ngati?
This is Mollen Chinaga ndipo mu Tonde Wadula amadziwika ndi dzina lake "MOLLEN". Munayamba mwawonerapo Tonde Wadula? Yambani kulitsata lero, ndi Sewero labwino kwambiri.

08/01/2025

Big shout out to my newest top fans! Kenneth Gomiwa, Gomonda Yankho, Willard P Manyozo, Moses Elemia, Sanji Rex, Bright Yesaya, Graciano Kaliwo, Magret Mkotola, Nachi Majawa, Chidothe Blessed Angella, Andrew Martin Namakupula, Gaven Nandolo, Reubeb Ngwata, Annie Katangwe, Ibrahim Khalifah, Ben Banda, Praise Pempho, Fatima Saidi, Adam Kiaz Kiambo, Diamond O'Brien Nazombe, Chikondi Leonard, Asile Kalimba, Fanuel Boston Kapalamula Chunga, Tee Kay, Chris Friday Hector Jani, Kcee Alick, Panganani Alufandika, Fragson Chimpanda, Yassin Anubi, Fiester Wokonderedwa Bandah, Zeck Msukwa, Ester Nambindo, Amfumu Mira, Tricia Moses, Stêvêñ P Dêlêx, Precious Chifundo Chakwana, Wezboy PC Mw, Zeke Zeke, Cephas Chapamba, McDonald Makawa Jnr, Gibson Wyson, Meta Inbox, Prince Daniel Malimelo, Taís Sestae Bile Angulete, Jack B Clarpton, Madalitso Chauluma Kumwenda, Lenato Katunga, Nganga Mwamuna Mkapolo, Red Moon Musiq, Oscar Jonathan

08/01/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chicco Gift, William Chimwaza, Goba Harawa, Chiko Temwa Naminga, Pempho Favoured William Masina, Fahad Bilali, Clever Manyong'onya, Geocry Y Qamban, Anthone Mkwamba, Peter Leonard Nkhata, Charles Piksy Malingamoyo, Patricia Chiotcha, Râmzÿ Àrsêñâl Hârrÿ Jñr, Benson Zefeniah Magodi, Stevens Paul January, Dumisan C Saka, C Banda Banda, Langisi Omega Chimowa, Celina G. Chisaleh, Limson Makuteyah, Gift Machemba, Elizah Saidi, Lungiswa Majola, Luqumqn Spatar, Tadala Jamer Hassan, Rabson Mumba, Jafali Khalid, Stuart Bestings, Mars Chitungo Ruth, Leki Leki, Jones Maxx Majawa, Bendita Alberto, Gloria Kanjaula, Arthur Toto, Shannon Spt, Dale's Mupacho, Ellen L Tchaluwa, Bernard Chiomba, Amin Mtambo, Filimon Suppli, Martha Likhomo, Jonathan Christopher, Gerson Zacarias, Rodrick Kaudzu, Ma Monalisa, Rose Matchado, Roy B Mw, Michael Mayeso, Stella Mtambo, Ramsey Wa Milanzie

Tonde Wadula 2024 - Most Punctual and Hard Worker - Masiku (Esmey)
07/01/2025

Tonde Wadula 2024 - Most Punctual and Hard Worker - Masiku (Esmey)

Representing Junnie Mulazie Tonde Wadula 2024 - The most Disciplined Actress.
07/01/2025

Representing Junnie Mulazie
Tonde Wadula 2024 - The most Disciplined Actress.

Tonde Wadula 2024 - Outstanding Performer (Gaga)
07/01/2025

Tonde Wadula 2024 - Outstanding Performer (Gaga)

Address

Limbe
Blantyre
MW

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhalango Multimedia posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nkhalango Multimedia:

Videos

Share