Mpebros TV

Mpebros TV Mpebros TV is Independent media TV which its aim is to proclaim the gospel of our Lord Jesus Christ

05/01/2025

Okondedwa mwa Ambuye, monga tonse tikudziwa kuti tili mu sabata ya mapemphero, tikudzindikira kuti si tonse omwe tili ndi mwayi ochita nawo mapempherowa chifukwa cha ntchito zosiyanasiyana. Choncho pali chikonzero kuti madzulo aliwonse kuyambira 7:30pm mapempherowa azichitikanso online kuzera link yomwe ili m'musiyi.

03/01/2025

Happy follow-versary to my awesome followers. Thanks for all your support! John Mpezeni, Victor EN Banda

03/01/2025

Big shout out to our newest top fans!
Let's keep fire burning John Mpezeni, Shie Faigo, Chimwemwe Napawa, Lc Kakhuta, Pretty Siyo, Victor EN Banda, Matias Mpezeni, Brian Mikweche, Foster Matewere, Verolniccah Montfort, Kavilele Medson Vwenya Mzumara, Victor Ligomeka, Patrick Tupa Nankhonya, Francis Chindiwo Junior, Blessings Blessings, ʚĭɞ Clive ʚĭɞ, Hannah Kamenya, Asimenye Msukwa, Sylvia Mzumara, Robert Waile, Esnart K Sumaili, Esther Chinseu

03/01/2025

Big shout out to our new rising fans! Evangelist Vincent Chakanga

TRANSFORMATION AGENDA (MR JORDAN MALOYA AKUFUNA KUBWERESA KUSINTHA MUMALO ONSE MOMWE MULI ZIPATALA ZA SEVENTH DAY BAPTIS...
27/12/2024

TRANSFORMATION AGENDA (MR JORDAN MALOYA AKUFUNA KUBWERESA KUSINTHA MUMALO ONSE MOMWE MULI ZIPATALA ZA SEVENTH DAY BAPTIST NGAKHALENSO KUKHAZIKISA MALO ENA ZIPATALA)
ZOMWE MPEBROS TV YAPEZA ITACHEZA NDI MR JORDAN MALOWA (MEDICAL ADMINISTRATOR)
Pamene tikupitiliza kukupatsirani za momwe zipatala za Seventh Day Baptist zikuyendereseredwa, lero tinacheza ndi wamkulu woyang’anira zipatalazi Mr Jordan Maloya mu Mzinda wa Mzuzu pomwe anali pa ulendo wawo wobwerera ku Blantyre kuchokera ku Rumphi kumene amakayendera chipatala cha Uzumara.
Mr Maloya, zochepa zokha zomwe anafotokoza momwe ayendera ku Uzumara anati ntchito yothandiza anthu pachipatala cha Uzumara ikuyenda bwino, ndipo anthu akukhutira ndithandizo lomwe akulandira pachipatalachi, Mr Maloya anapitiliza kuyankhulapo kunena kuti panopa akuyembekezera kuti a CHAM ayambe kutenga mbali pachipatalachi muzinthu zofunikira zokhuza zipatala. Ndipo ngwirizano wawo ulimkati kuti nthawi iliyonse a CHAM ayamba kukhuzidwa potengapo mbali pachipatalachi.

Atafunsidwa zamomwe Ntchito yawo ikuyendera komanso chitsogolo cha masomphenya awo, Mr Maloya anayankhula kuti ngakhale kuti mmene amalowa mu ofesi yawo ngati Medical Administrator anapeza mavuto osiyanasiyana koma ngongole, zimene zinapangisa kuti ntchito yawo ayiyambe movuta, komabe anafunisitsa kuti akonze zinthu ndicholinga kuti zitukuko ndi zinthu zina zofunikira kuzipatala ziziyenda bwino.

Kwa zaka ziwiri zokha zinthu zina zomwe amaziyembekezera kuti zichitike zinakwaniritsidwa monga kuonjezera ogwira ntchito ena, kukumbisa mjigo ku chipatala cha ku Chipho komanso kuonesetsa kuti magesi abwera kuzipata komwe kunalibe magesi, kukhazikitsa chipatala cha kuuzumara, kungotchulapo zochepa zokha. Komanso anayankhula kunena kuti kwa nthawi yoyamba kuti zipatala zapeza phindu lochuluka munthawi yomwe iwo akuyendetsa zipatalazi ndi ndalama yokwana MK 37,000,000.

Iwo khumbo lawo ndilofunisitsa kuti zinthu zisinthe komanso kugwira ntchto kwawo kuonese phindu maka poonesetsa kuti akuyendera limodzi ndi akuluakulu a Board ya Mpingo wa Seventh Day Baptist, ngakhale ogwira nawo ntchto kuzipatalazi. Ndipo anayankhulanso kuti kuzipeleka kwawo sakufuna kuonesa ubwana koma zokhumba zawo zikwaniritsidwe mumasomphenya awo ndipo izi zizapangisa kupita malo aliwonse mosavuta ngakhale kuli kovuta kufikirika kumaloko.

Pitilizani kutsatira Mpebros TV kuti mukhale mukumva zambiri za izi ndi zina zomwe tizikupasirani

TV

Wakulu oyang'anira zipatala za  mpingo wa Seventh Day Baptist muno Malawi bambo Jordan Maloya akuyendera chipatala cha K...
25/12/2024

Wakulu oyang'anira zipatala za mpingo wa Seventh Day Baptist muno Malawi bambo Jordan Maloya akuyendera chipatala cha Ku Uzumara m'boma la Rumphi, Iwo anafika kumalowa lachiwiri pa 24 December ndipo akuyembekezeka kubwelera lachisanu pa 27 December.

Malingana ndi uthenga umene Mpebros TV yapeza kuchokera kwa bambo Maloya iwo ati "Cholinga chawo kuyendera chipatalachi chofuna kuonesesa kuti pachipatalachi Pali ukhondo komaso kasatidwe kabwino ka umoyo wathanzi.
Iwo ati "ndi okonzeka kugwira ntchito ndi aliyense cholinga Chokweza Moyo wa ukhondo Komaso nthanzi la aliyense osatengera usikhu potengera kuti moyo ndi Mpamba komaso nthanzi ndi chithu chofunikira pa munthu aliyense." Kupatula kuyendera ntchito zaukhondo kumalowa iwo anayenderaso ogwira ntchito pa malo amenewa kuona mmene akugwirira ntchito yawo komaso anakasiya makhwara osiyanasiyana kuchipatala chimenechi cholinga choonesesa kuti makhwara akupezeka pa chipatalachi.

Anthu ozungulira chipatalachi amene anayamba kupindula ndi thandizo la chipatalachi kuphatikizapo mafumu ati "ndi okondwa kuti wakulu wa zaumoyo wawayenderaso kuonesesa kuti ntchito yaumoyo ikuyenda bwanji, ndipo anaonjezeraso kunena kuti iwo ngati mafumu ayesesa kuona kuti katundu wa pa malo achipatalachi akusamalidwa bwino komaso kutetezedwa."

Chipatala cha ku Uzumala chinakhazikisidwa kumapeto kwamwezi wa August mu chaka chino cha 2024 ndipo chikuthandiza anthu ochuluka kudera limeneli.

Pitilizani kusatira Mpebros TV tikhala tikukupasirani zambiri zammene zikuyendera ku malo amenewa.

TV

20/12/2024

Happy Sabbath to everyone from Zambia
Buchi Seventh Day Baptist church In Copperbelt province

Main service
Preacher: Foster Matewere -Malawi Seventh Day Baptist Youth Music director
Translator : Frey Mukumbo
Zambia Seventh Day Baptist National Youth director

TV

18/12/2024

Big shout out to our newest top fans!
Pretty Siyo, Matias Mpezeni, Verolniccah Montfort, John Mpezeni, Shie Faigo, Lc Kakhuta, Victor EN Banda, Brian Mikweche, Foster Matewere, Kavilele Medson Vwenya Mzumara, Victor Ligomeka, Patrick Tupa Nankhonya, Francis Chindiwo Junior, Blessings Blessings, ʚĭɞ Clive ʚĭɞ, Hannah Kamenya, Asimenye Msukwa, Sylvia Mzumara, Robert Waile, Esnart K Sumaili, Esther Chinseu

16/12/2024

Like and follow the page

Mpebros TV

16/12/2024

TRIP TO ZAMBIA UPDATES

Ma dance pang'ono tivineko

TV

16/12/2024

TRIP TO ZAMBIA UPDATES

TV

16/12/2024

TRIP TO ZAMBIA UPDATES

This song
"Am appreciating God for showing mercy on me"

16/12/2024

TRIP TO ZAMBIA UPDATES

Song is about
"The foolish one says we are tired waiting for Jesus Christ, let's get drunk a bit"

16/12/2024

TRIP TO ZAMBIA UPDATES

History is made as Malawi Seventh Day Baptist Youth visiting Zambia Seventh Day Baptist Youth on 12 December 2024.

According to the information from the one of the representative for this trip says "they were 13 in numbers including Malawi's Acting General Secretary pastor Napier Banda".

The committee would like to appreciate all the youth who use their own money and dedication towards this trip.
They also appreciating everyone prayer towards this journey to Zambia as they went well without any problem encountered on the unforgettable trip like this.

Some other visitors were from Canada who also visit Zambia at Buchi Seventh Day Baptist in Copperbelt province.

Malawi seventh Day Baptist Youth are now back home yesterday on 15 December 2024.

TV

TRIP TO ZAMBIA UPDATES  Malawi Seventh Day Baptist Youth visiting Zambia Seventh Day Baptist Youth in Copperbelt provinc...
15/12/2024

TRIP TO ZAMBIA UPDATES

Malawi Seventh Day Baptist Youth visiting Zambia Seventh Day Baptist Youth in Copperbelt province at Buchi Seventh Day Baptist.

TV

TRIP TO ZAMBIA UPDATES Achinyamata ampingo wa Seventh Day Baptist ochokera mu zigawo zosiyasiyana mu dziko lino la Malaw...
14/12/2024

TRIP TO ZAMBIA UPDATES

Achinyamata ampingo wa Seventh Day Baptist ochokera mu zigawo zosiyasiyana mu dziko lino la Malawi amene ananyamuka pa 12 mwezi uno wa December kupita kukayendera Achinyamata adziko la Zambia afika.

Achinyamatawa afikira Pamalo opephelera otchedwa Buchi Seventh Day Baptist mu province ya Copperbelt mudziko la Zambia

Malingana ndi mtsogoleri wa Achinyamata mdziko la Zambia a Kennedy kodji ati "Ndi osangalala kwambiri kuona Achinyamata azawo akuwayendera komanso kuwalimbikisa moyo wa umzimu"

Mau ake iye watiso Achinyamata adziko la Zambia akuyembekezeka kuzayendera achinyamata a dziko la Malawi chaka cha mawa.

TV

Address

Mbayani
Blantyre
981762775

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mpebros TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mpebros TV:

Videos

Share

Category