Morton Baghaya

Morton Baghaya Morton Baghaya mweneko...everything goes.
(12)

Masteni ena ake ku inbox:"Morton ndigulisileko Tablet (Galaxy Tab A8) iyi. Imagulidwa 500,000 koma ine ndufuna 270 basi....
18/06/2024

Masteni ena ake ku inbox:

"Morton ndigulisileko Tablet (Galaxy Tab A8) iyi. Imagulidwa 500,000 koma ine ndufuna 270 basi. Ndili ku Blantyre pa ma Nambala awa: 0993189330 kapena 0883486905."

A Donia Mw amvekere Chimidzi mwakutimwakuti pa post ya ife nde tinapita kukawapanga stalk. Guys, ngati chitauni ndi ichi...
18/06/2024

A Donia Mw amvekere Chimidzi mwakutimwakuti pa post ya ife nde tinapita kukawapanga stalk. Guys, ngati chitauni ndi ichi ine sindikufuna kubwerako ku tauniko. kabudula alemba kuti chani? Yunis Vithongo?

18/06/2024

Wachema Ng'anga kuti yikakolope muzi, wati wahawi wahauka kweni Boma Likukana vyakuchema ng'anga. Wakomanenge Bina Mhango. Ka Kukuchitikachi? Vikamba uli? Vili Mpha? Nayowoya na: 1. Ng'anga Suzgika, 2. Wa Chikulamayembe, 3. Wa Themba Mwamlowe, 4. Wa Fumu wa Mhango na wanthu wanji kuti nkhani iyi tiyipulikishe makora.

18/06/2024

Anthu akumudzi kwathu anasonkha aliyense 1.5 kuti ayitanise sing'anga kuti ati izachotse ufiti pamudzi, ife titamva tinayimbira a TA, a DC kenako kuyiyimbira sing'angayo kuyiopseza. Move yonse inakanika, anthu anapanga meeting, kutikwiyira ndipo meeting inatha ndi kunena kuti iyeye akazamulodza azakhaula. Osaopa magaye, ine ndimayamba kukangana ndi abale anga omwe ndisanafike kwa ena.

18/06/2024

Tinafunsa izi: "Now that ayika maliro, let's get a few things cleared up: he was in that destructive DPP and left only at the end promising to reveal secrets and to lynch the corrupt. He went to MCP where he stayed silent and only came alive after it was revealed he actually was in cahoots with a very corrupt Indian guy. And yet some want to erect a statue for him and some say he was a Saint and some say anali mfana oganiza bho? Kuwafunsa akungoti anapanga influence ma youths, anasintha kaganizidwe ka anthu."

Anthu ayankha chonchi in summary:

He was better than you
Ukufuna ma likes
He impacted the youths
Mbuli yophunzira iwe
No man is perfect
Iwe wapangapo chani

Can someone talk to me like a standard 5 child and answer the question bho bho?

17/06/2024

Kumudzi kuli Ada ena ake amene anthu amati ndi afiti koopsa. Ironically pamudzipo munthu oyamba kuyika magetsi mnyumba anali adha awowo. Munthu amene amalima mbatata kambiri ndi adha awowo, munthu ameme amatha kuweweza nsomba kwambiri pa mudzi ndi adha awowo in fact abambo awo anali ndi ng'ombe ndipo sing'anga anabwera kuzawachotsa ufiti kenako kuwalanda ng'ombe. Ineyo ndikapita kumuzi ndimapita kwa adha awowo kukadya nsima ndikulipira bill ya magetsi ya mwezi ndipo abale amati: ndalama imene mwawapatsa ija apangira mankhwala ndipo ndalama zanu zonse zipita kwa iwowo. Ndinazindikira kuti ndi nsanje chabe zimene zimapanditsa anthu akumuzi kugwira munthu ufiti.

17/06/2024

Munthu lero kusegula orphanage, mawa kupempha ndalama...kodi mukufuna kuthandiza amasiye kapena kuzithandiza nokha?

17/06/2024

Panali bambo wina wake anayambisa NGO nde amafuna thandizo, ndiwawafunsa, kodi NGO yanuyi zina lake liluti Yehova chakuti chakuti chifukwa chani? Anayankha amvekere: dzinali likuti yehova chakuti chakuti chifukwa amapatsa zonse, amasogolera, amadziwa zonse ndi yehova...ndinangowatsika kuti ngati amapatsa zonse ndi yehova sakuwapasa ndalama zimene akufuna bwanji?

17/06/2024

By the way, ndimathandiza mwana wina wake nde ndinamufunsa kuti amayi ako anamwalira nanga abambo ako ali kuti? Mwanayo anayankha kuti abambo ake analozedwa ndikupenga. Guys ine ndine Morton Baghaya, kaya ndi wachibale kaya ndi family member, amene anena zaufiti ndi ine kamakhala komaliza kuyankhulana. Ufiti kulibe.

There are so many variants of Tumbuka, where I come from we don't even know these here words. We call this thing 'Nkhony...
17/06/2024

There are so many variants of Tumbuka, where I come from we don't even know these here words. We call this thing 'Nkhonyoro.' The Tumbuka that was codified by missionaries is actually just a washed down dialect that is heavily influenced by Ngoni and Chewa. Yewo.

17/06/2024

Pheee AI mu Galimoto.

17/06/2024

JB akuti a Malawi musazavoteronso m'Chewa chifukwa ndale zawo ndizophana. hahaha JB uyuyu ayambana ndigulu.

17/06/2024

Now that ayika maliro, let's get a few things cleared up: he was in that destructive DPP and left only at the end promising to reveal secrets and to lynch the corrupt. He went to MCP where he stayed silent and only came alive after it was revealed he actually was in cahoots with a very corrupt Indian guy. And yet some want to erect a statue for him and some say he was a Saint and some say anali mfana oganiza bho? Kuwafunsa akungoti anapanga influence ma youths, anasintha kaganizidwe ka anthu. Are you fu***ng kidding me?

17/06/2024

I made a whatsapp group for Malawians to buy from China by paying in Kwacha. After two weeks only one person actually wants to buy, enawo akungoyesa zida, wina mpakana kunena kuti kugula ndikudikira ayike kaye maliro a vice president.

Let us do this again: ngati muli ready kugula ngini, go online, make sure you have a link and and or picture or explicit specs of what you want and after that, I will give you the whatsapp link to the group. The people I have will pay suppliers for you and handle shipping. Ask for the group link only if you are ready. 谢谢。

17/06/2024

Munaonapo munthu akunena kuti azodiyaki alemba nkhani chifukwa akufuna ma likes? Pa Times anayitana anthu osiyana siyana kukambapo za Maliro ayikidwawa...alipo wanena kuti a Times amafuna na likes kapena kuti akanadikira kaye? Anthu akuletsana kuyankhula zinthu zokhuza ma public officials? A Zodiak amayika malonda a makampane amene analipira ndikuyika uthenga wa chipepeso. Alipo amene wanena kuti inu mukuphangilaponji ndalama pa malirowa?

17/06/2024

The Bible and Koran both instruct us to love one another, generally.

The K**a Sutra is more specific though.

Oyimba enawa mwina atayamba kuyankhula anthu atha kumawamverako. Ife apa, timatenga mic nkuyankhula anthu nkumamvera opa...
17/06/2024

Oyimba enawa mwina atayamba kuyankhula anthu atha kumawamverako. Ife apa, timatenga mic nkuyankhula anthu nkumamvera opanda kupereka ndalama kwa DJ. Too bad page yaife siyipanga ndalama koma ma views nde alipo. Zikomo amene mukuonera ndi amene mukutukwana nomwe.

17/06/2024

Ma interviews a ma Chinese scholarships ali mawa, congrats to all those who have been shortlisted.

17/06/2024
17/06/2024

Ndisaname, ndimalandira ma messages 200+ a day and kuyankha kumavuta, koma I promise mawa ndikhala pansi ndikuyankha what I can. I only promise to ignore amene atumiza "hi."

Ine ndili bwino, dzikomo, fikilani kungosimba nginiyo kuti message iyankhidwe, osati kungotumiza: hi, bho, how are you, chief, boss, Morton, Axse, muli uli, uli bwanji, akulu, iwe, H, HUD, dolo, captain, Sibweni, imwe, wapapi (okay if you hit me with wapapi I will definitely respond, lol). You get the pic, though...let's go straight to the meat.

Osadandaula ndife ma professional journalists ndithu, award winning ku Malawiko timasunga zinsinsi olo atati a khoti atiopseza kuti tiulule za ku inbox timalolera kukaseva jelo.

17/06/2024

Lekani kuhangayika na chitanda, lekani kufula ma miliyoni pa chakufwa kale.

Almost 10,000 paja titulusa mabomba awiri ukuku anthu akafika 10 sauzande. Pangani subscribe ukoko ndimayamba kuyika ma ...
17/06/2024

Almost 10,000 paja titulusa mabomba awiri ukuku anthu akafika 10 sauzande.

Pangani subscribe ukoko ndimayamba kuyika ma vidiyo ukoko 4 days ndisanawayike panopa.

Protests, Politics and Culture

17/06/2024
Nde wina umumva...mukanagula simenti, puloti, abale anu kumudzi mukuwathandiza koma?  Axse, panga zako. Abale athu kumuz...
16/06/2024

Nde wina umumva...mukanagula simenti, puloti, abale anu kumudzi mukuwathandiza koma? Axse, panga zako. Abale athu kumuzi ngati amakwanitsa kulipira sing'anga kuti izachotse ufiti pamudzi, ali bho amenewo. Komanso wanena kuti za simenti palibe ndani?

Ku Romania bala inayaka moto anthu kufa, Prime Minister anapanga resign. Ma example a ma officer kupanga resign ali mbwe...
15/06/2024

Ku Romania bala inayaka moto anthu kufa, Prime Minister anapanga resign. Ma example a ma officer kupanga resign ali mbweee. Kodi ku MDF ndi ku ma traffic control, ku ma ministry sangapange resign kuti anthu abwere azafufuze bwino?

It was the second crash in three months

Guess where he comes from?
15/06/2024

Guess where he comes from?

15/06/2024

Ali ndi picture ya a Kachaje ya latest atipatse, I want to see something.

Akuti kodi mitengo ya pa alibaba njoona?Yes. Koma muzionesesa ena amafuna mugule at least zinthu 100 komanso muziwe kuti...
15/06/2024

Akuti kodi mitengo ya pa alibaba njoona?

Yes. Koma muzionesesa ena amafuna mugule at least zinthu 100 komanso muziwe kuti palibe shipping ndi duty apopo.

One more thing, onse ogulitsa pa alibaba amaziwa chizungu, chezani nawo ndithu.

Hide my ID: A boyfriend'wa atithandiza koma?"Hie Mr Morton Ndili mu Dilemma munthune Cox always when I tried to give som...
15/06/2024

Hide my ID: A boyfriend'wa atithandiza koma?

"Hie Mr Morton

Ndili mu Dilemma munthune Cox always when I tried to give someone my heart it ended up in tears 😢 😭 for the invalid reasons 😢 So as of now l have boyfriend of which l love him so much ❤️ 😢 but the issue is l don't know if he really loves me but we have stayed almost 7 months. Komano still sikuwona sogolo lililonse cox kamufunsa za ma plan samayakha kalikonse and he never introduced me kwa ma friend ake ,never post me of course l understand kt someone people don't believe in social Komano it's too much for me 🥺🙆 ndye l just need a guide kt should I go for it or zilibe tsogolo? Nsaname zundiwawitsa mutu"

Morton to the rescue : adha awowo akubenefita mwa inuyo basi that is all he wants. Mwamuna amene sapanga introduce anzake akuyenera kupangidwa block unless abwere poyera kuti ali kale ndi kena kake, in that case musayinilana contract ya u MG2 or mugawana zida.

Also, mamuna opanda plan osamusunga, akusiyilani mimba ndikuyikananso.

Try this: mmaneni game for miyezi iwiri muona zimene iye amafunadi mwa inu.

Also, 7 months siyambili. Mwina Sali sure bho bho...khalani naye pansi, muyang'aneni mmaso ndikumuuza zimene mukufuna. Communication ya clear bwino doe the trick sometimes.

Cheers.

Sakuzibisa dzina: kodi ndalama zimene mwaononga kuphunzira simukanapangira business?"Abwana ndimawelengesa makobiri omwe...
15/06/2024

Sakuzibisa dzina: kodi ndalama zimene mwaononga kuphunzira simukanapangira business?

"Abwana ndimawelengesa makobiri omwe mwaononga kuchita udotolo/using'anga omwe mwachita uko ku China, zikuonesa Kuti mwafapo. Kumuzi kuno A2 amachita timitsuso mkumanena Kuti makobiri akhani khani omwe akupita kumaphuziro makamaka aukachenjede ndi ung'anga atati apita kuma business awa2 alutha omwe akusowa kapitolo mwina zitha kusintha maonekedwe a Malawi. Mosachulusa gaga diwa mkutheka mwamba point ya Zomwe Malawi ena akumaona, ine ndimati ndikufunseni inu abwana Kuti Kodi zikafika pomwe mwafikapa zilindi mphindu kwa inu Komaso kudera lanu mwinaso kudziko ?? Kapena mwina inu mumaziona motani zamaphuzira ofika nawo moterewa??"

Morton akuti: nzoona a bwana, bwenzi ndili bwanadi olo nyumba. Koma taonani pano, ndili mbuu olo puloti, olo galimoto, olo munda or phone yabwino.

Ngati muli ndi ndalama pangilani bizinesi, PhD izikhala ya anthu olipilidwa ndalama (scholarship).

Koma... Pali anthu ena samafuna galimoto, ma TV ndi kukhala ndi Chuma. Anthu ena amapanga value mmene akukhalira tsiku ndi tsiku osati sofa imene akhalapo.

Address

Nottingham
NG84JT

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Morton Baghaya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Morton Baghaya:

Videos

Share



You may also like