NSIPE MEDIA

NSIPE MEDIA God.

Know who you're and know what you're doing
what ever is hard...... success is not in easy way whether you come from rich or pool family .try to avoid trableling a peace
Understand situation and be comfortable with negative thoughts and feelings.

16/01/2025

Koma guys vuto la fuel β›½ lidzatha liti ?

15/01/2025

John chilembwe
Anawona azungu kuti ndi akhadza, ndi okupha komanso Kuba
Inu mumayiwona bwanji legacy ya John chilembwe

15/01/2025

Makolo amatipusisa amvekere
Akazi amaotcha nde tinkaopa
Lero ndamva kukoma ndi akazi akutipakulira nyemba kuchita kuzithawa

15/01/2025

Pa Malawi πŸ‡²πŸ‡Ό chilichonse tilinacho
Good water πŸ’¦in with spatial fish 🐠, good land for agriculture and with natural resources, good people highly recommend education PhDs ,degrees,
Koma mavuto ndi omweaja from 1840s
John chilembwe ankalimbqna ndi azungu kuti chilichinse tizipanga tokha mwaufulu

15/01/2025

Chikumbukiro choyambilira pacha chilichonse kwa siku 15 ndi cha John chilembwe munthu yemwe anathangitsa azungu oononga akupha koma atsogo alero akuyanjanawo azungu akuba ndi kusokoneza malawi wanthuyu
R.l.p chilembwe

Nkazi amafuna moyo wofewa azimva kukoma    Wikise1992  holding her in his arms zosangalasa
15/01/2025

Nkazi amafuna moyo wofewa azimva kukoma
Wikise1992 holding her in his arms zosangalasa

15/01/2025

HAPPY CHILIMBWE DAY

Aida analira 😭😭😭 ataona kuti azungu akufuna kupha John chilembe
Koma sikazi amasiku ano kumva kuti amuna amwalira kuthamangira pomwe pali iPhone, nyumba kapena galimoto

15/01/2025

GOOD MORNING
M. Munapha
C. Chilima
P. Pandenge

14/01/2025

Anangowadyetsa khuzumule πŸ› amuna awo iwo amakhala pa social πŸ“±πŸ“žbusy ndi amuna ena
Akaweleka mamuna afike panyumba 🏘aphike achapenso akazi amafika mochedwa amayamba Kaye amwe uwiri 🍾🍾
Weekend aliyenso amayendera yake amai amabwera pakati pa usiku sometimes amabwera Monday pochokera kuntchito
Mamuna zimamunyasa koma m'mtima amangoti ndi akazanga ndi my family
Munakuna kuti ?
Munkafunamo chani ?
Anafusira ndani ?
Nkhuku yoweta 🐀sitigura pansika
Mudzagula nazo njoka πŸ¦žπŸ¦‚πŸ’πŸ¦ŽπŸ

14/01/2025

🫘SEEDπŸ˜…

What's is your life seed 🌱 ?

Do you know what is a seed ?

Know your life seed and germinate it into lifetime to produce flowers and fruits

Without seeds no harvest !
Without time on seedlings no more food progression and food programs like Food marketing EVEN FARMERS BELIEVE in that area of seed
Seed can be your goal πŸ₯…, achievements ,potentials and also your powers but a seed would be first as first thing in life
If you're good seed then produce good qualities
If you put on wrong germinate land, poor results or die on
If in a seed there's no life, it would not be grown and bear something
What is relationship bteen a seed and life
Know what si your seed of your life today ...........seed.........life........

14/01/2025

Kungothetsa chibwezi popanda reason lero January wafika mwakumbukira KFC akakugulirani njara ikakugwirani
Asika muzimukonda boyfriend wanu nthawi zonse

14/01/2025

Kulibe manda ambeta inu mupeza boyfriend πŸ€“ wa galimoto chaka chino

14/01/2025

First of murch tiyamba kugawa airtime AIRTELL/TNM
keep in touch 2025 tikufuna muzinva kukoma

14/01/2025

January Samanama eti x wanga kundihara ine kumuimbira amvekere tibwelelane πŸ˜†πŸ€”

14/01/2025

Alili malawi πŸ‡²πŸ‡Ό ku John kukanakhara pafupi ndikanayenda wapansi koma mmm zafika povuta ntchito zikusowa chilichonse chakwera

14/01/2025

Moyo ndikusililana wina ali ndi chinkazi chambina ❀️ wina Ford ranger πŸ›» wina masion 🏘 inu musawofooke limbikirani kwa mulungu kulibe umphawi

14/01/2025

Amakana kukwatiwa adakali fresh pano ana atatu abambo awo osiyana πŸ˜…πŸ€”
Azimai chonde tazikhazikikani muchikondi nthawi imathatu yothamangayi
Liwiro lingakulere bwanji limakaima basi
Amuna akufuna azimai ozichepetsa osati odziwa kugulitsa nyemba pansika

14/01/2025

ANA ISRAEL ANANYAMURA NJERWA ZAMOTO KU IGUPUTO
NDE IWE NDINANU PUSHA KUTI ZAKO ZITHEKE

SUCCESS

Address

650 South Coast Road , Clairwod
Durban
7100

Telephone

+27678080278

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NSIPE MEDIA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share