Nthawi Mkachitsilu

Nthawi Mkachitsilu Marketing & advertising

My name is.?
07/03/2024

My name is.?

13/02/2024

Good morning friends and family

Ak*telotu
12/02/2024

Ak*telotu

Happy birthday  pastor wayson A K A DJ zimbabwe
12/02/2024

Happy birthday pastor wayson A K A DJ zimbabwe

11/02/2024

Ivory coast vs Nigeria inu mwakwela chani?

11/02/2024

Maganizo anu ndiotani za papa Henry gopan apite ku mental kapena apitize zake zomwezi?

Hello family    kundende anzanu amagona chomchi
11/02/2024

Hello family kundende anzanu amagona chomchi

26/12/2023

Khalizima mandas uja ndi dolo dithu

Christmas πŸŽ„  ikuyenda bwino  kunoπŸ˜€
25/12/2023

Christmas πŸŽ„ ikuyenda bwino kunoπŸ˜€

Rest in peace  ZaharaπŸ’”
12/12/2023

Rest in peace ZaharaπŸ’”

27/09/2023

Saint k*tulusa Album yabwino kuposa asatanic wo πŸ€”πŸ₯±πŸ₯±

19/07/2023

Hay pipo I'm back tiyeni ticheze tithandizane

10/07/2023

Mimba satenga mwangozi pa bedi palibepo nsewu tikuvana atsika

06/07/2023

Good night pipo πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ™

11/04/2023

Dzulo ndi lero sanachokepo i think chatha anthu oyipa mtima apanga alahandulilaπŸ’”πŸ’”πŸ˜«πŸ˜«

10/04/2023

Chikondi ndi mzelu. ngati ulibe mzelu chikondiso palibe πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ‘‡ pangan like page k*t mudziva nkhan zabwino

09/04/2023

Kufuna k*ti bela tikakololaπŸ˜«πŸ˜«πŸ˜«πŸ˜«πŸ˜™

08/04/2023

Pangan like page k*t mudziva nkhan zibwino

07/04/2023

Sakazi ose omwe amafuna ndalama kwamamuna ayi enawa amangofuna chikondi chenichine ndi mtendele wamumtima bas πŸ‘ŒπŸ€žπŸ’¨πŸ”₯πŸ”₯

29/03/2023

Tipexeni tik*thandizan

29/03/2023

Nkhani ndimeni

08/03/2023

R P AYAYA πŸ˜­πŸ’”

05/03/2023

Hi adim ndine mnyamata wazaka 26 ndipo kwathu ndiku mwanza koma pano ndili ku South Africa ndipo ndikufuna mkazi oyambila zaka 18 to 22 wa serious oti ndimange naye banja oro atakhala wamwana mmodzi vuto palibe koma akhale serious

Atsikana nkhani ndimeneyi ndipezeni ku inbox amene angakonde

Osadandaula pano timasunga chisisi kwambir

Ngati muli ndizinthu zofunika kungezedwa tipezeni ku inbox zose zotheka ndipo simudzakhumudwa kose

12/02/2023

Tilipano kulumikizitsa anthu osowana kupeza chibwezi cha seriously banja kulengeza malonda ukwati party ndi zina zambir zomwe mukufuna k*t zichitike tipezeni ku inbox k*t muve zambiri

25/01/2023

DOβ™₯️
YOU β™₯️
LOVE β™₯️
YOUR β™₯️
MOM β™₯️

17/01/2023

Chitsilu mchimene chimagulitsa munda ndalamazo mkulipilila fees chibwezi. mxm mutu wadaziwo gilibata

14/01/2023

Zibwezi 4 koma mkumakhalabe mmaluzi eeee achina memory 😏😏

14/01/2023

Full time

Man U 2

Man city 1

10/01/2023

Ndizomwe timapanga

09/01/2023

Good morning abale wanga mwambuye mukhale ndi tsiku lopambana God bless you πŸ™πŸ™πŸ™

Address

Brown
Durban
HYT

Telephone

+27736730585

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nthawi Mkachitsilu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category