Malawi-wa-luso

  • Home
  • Malawi-wa-luso

Malawi-wa-luso THIS PAGE AIMS AT CEREBRATING, PROMOTING & QUESTIONING ALL SORTS OF TALENTED PEOPLE IN MALAWI, GETTING THEM TO BE UNDERSTOOD SO THEY COULD BE APPRECIATED

23/06/2024

Kodi Zaka Zanzanuwo ndimaonekedwe awo chachikululu nchani?

23/06/2024

Luso lanu ndilotani

01/12/2022

MALAWI WA LUSO

13/11/2022

*KUTSEGULA MALUSO OBANIKA*

Malawi ndi dziko lodzadza ndi anthu anthana zamaluso osiyanasiya. Malusowa sabwera poyera kamba kosowa upangiri, kuvuta kwazachuma komanso njira zoti ena amanja achinyontho ndimtima opanda njiru angatidziwire.
Galamuka Malawi, kwacha, Tenga khasu laluso lako no ligwire molimba tiswe ndime. Papita khasu sipanama, ubongo sudzadza.
Pukuta mnsozi wakusathandizidwa munjira zingapo pa lako luso,.

Tikuyenderani, tidzakufunsani, tidzakuthandidzani kufikira lanu luso litadziwa ubwino osamila kutchuka. Osalema paluso lako, nthawi yakwana Malawi .
Matsiku alimkuzawa, tidzicheza ndi amaluso ngati Inu anthu nkumakuonerani, yomweyo nkukhaka pasipoti yanu yakuzimuka.
MALAWI WA LUSO : kutambasula nkhani zamaluso Malawi

10/11/2022

Hallo Che Mandota squad,

Without wasting much of your time I would like to go back and explain in detail pa zinthu zomwe ndinalemba dzulo pa page pano komanso kuphatikizilapo nkhani yonkhudza depression.

Dzulo nditalemba post ija ndinachoka pa line chifukwa zinali zikundipweteka kuti ma fans anga sindikuyenera ndiapatse chiphinjo ngati chimenecho ndiponso ndimadziwa kuti pali anthu ambiri omwe angayankhule zosiyanasiyana komabe ndinalibe option ina but to just post and stay offline kwinaku ndikuyesa njila zina zothetsela vuto lomwe linalipo.

Ndikudziwa aliyense anali ndi mafunso mu mtima koma lero ndati ndikutsimikizileni kuti inde nkhani yomwe ndinalemba dzulo ija ndiyoona ndithu komaso si ya masewela koma tiyamike mulungu kuti yatha bwino!.

I been into an online importation business for some time koma ulendo uno siinathe bwino as i was scammed.
The bad side of it was that i had collected some advance payments from customers omwe ataona kuti katundu wao sanabwele after the promised days of delivery, lomwe linali lachisanu, anandipatsa 48hrs to give them their products or i refund ndalama yao yomwe anapeleka amounting to $1300=Mk1,820,000(osawelengela yanga yomweso nnalowetsa pa katunduyese) kapeta athana nane!.

Being in a confused state, i thought of making a request to my fans to bail me out of this; as that was the only hope i had since i used my monthly earnings on settling my bills this side.
I would not contact my work place here in Uganda or INNOBUILD (where I am their ambassador) as i thought it would be inconviniencing since i already got my monthly payment in full kumayambiliro kwa mwezi uno.

Mwa mwai anthu munaonetsa mtima wachikondi ndikusonkha ndalama yoposela mk320,000 komaso a INNOBUILD anandiyimbira phone lero kundifusa zomwe zachitika ndipo nditawalongosolela anafunsa kuti ndiwaonetse umboni wa ndalama zomwe ndinatumiza kunja zo kudzela mu Email komaso ndiwaonetse Telegraphic Transfer (TT) slip, ndipo nditawatumizila a Innobuild Limited Comp

04/06/2022

A cloud of uncertainty hangs over the scheduled performance of South African dancer and socialite Zodwa Wabantu in Malawi. This follows the withholding of issuance of a permit for her performance in the country by the Censorship Board. The South African has been lined up to host a musical event on J...

Today's headline. Shammah's fans react over his idea of terming his hair...
20/05/2022

Today's headline. Shammah's fans react over his idea of terming his hair...

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi-wa-luso posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi-wa-luso:

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share