LANAZ Fazili

LANAZ Fazili Anything with sense

16/05/2025

With Maulana Fazili – I just got recognized as one of their top fans!

11/05/2025

Inu kumnamizira   mmmm zosayendat wakukaniran uku...😂😂
11/05/2025

Inu kumnamizira mmmm zosayendat wakukaniran uku...😂😂

24/04/2025

Welengan bwino 🤣🤣👇

AMERICA:
👦::I Saw You Kissing Jonh! 😡.

👧::It Wasn't Me Bbe.

👦::Phaa👋.(slap)

👧::Ouk Bbe😭.. Sorry For Lying It Was Me & I Promise I Won't Cheat On You Again 💔.

👦::Ok Bbe I'm Also Sorry For Slapping You 🙏.

MALAWI:
👦🏾::Phaa 👋 Phaa 👋 Phaa 👋 Dish👊 Dish 👊.

👧🏾::Ndalakwa chaniso?😭.

👦🏾:: Fotsek !! Phaa 👋💥 Phaa 👋💥.

👧🏾:: Sorry Bbe, koma Ndalakwa chani??💔😭.

👦🏾::Umawona ngati sindiziwa!!..Dish 👊💥 Dish 👊💥 Phaa.

👧🏾::🙈😭😭😭😭😭😭

👦🏾::Iwe umati muzinyengana ine osaziwa!!!.. (Spinning Kick😡 phooo wagwera Pasi ..tsiiiiiiiiiiiiiii! Kenako zii). 🚶

🚔...🚑...🏥...🛌...⚰️...

Mwina mumangomva.Lanaz Osman
24/04/2025

Mwina mumangomva.

Lanaz Osman

17/04/2025

*M'doka ndi Lucy...😍 *

M'doka :hie

Lucy :hie, ufuna chani??

M'doka : tadekha ndilongosole

Lucy :panga changu ukundichititsa manyaz

M'doka :mmmhu ,ndukufuna chibwez,ukwati komaso banja

Lucy :khala serious ,sukulu yakukanika olo atati mabanja akusowa ndi inu nomwe ??

M'doka : mayazi sukulu ndinamaliza

Lucy: mmmh bodza tandifusile muchingerezi kape iwe

M'doka : you are mathematically calculated for me.

Lucy : choka apa!!

M'doka :I can't go any where, u are geographically allocated in my heart

Lucy:what ?

M'doka : we can chemically react.

Lucy: kkkk , m'doka are u mad ??

M'doka : when I see you, we are physically fit

Lucy : m'doka usandionjeze kupusa eti !?

M'doka :your nyash is always biologically functioning.

Lucy :choka !wandikwana ndikupita

M'doka : I will historically remember you

Lucy :kkkkk koma malodza ena

M'doka : I was agriculturally planted for you.

Lucy: kkkkkk koma bea! Ndarola basi ,koma ndiye ndiwe ophunziratu ,nde mawa tidzakumane kuti ??

M'doka : m'kati mwa shoprite ndine mulonda kumeneko

Lucy: ???????
Thanks for your attention 😊😊

17/04/2025

Nkazi Ali ngati school pamene iwe ukuyendera ena amachita kugonera konko😂😂😂😂

17/04/2025

Kwatirani muzigona ndiwangongole pa bedi limodzi🤣🤣

17/04/2025

A waterboard mankhwala abomawo muzingothiliratu m'madzimo kuno aliyenset anaola😂

Ambuye kumwambako za ma cartoonzi chonde zindipitilire ine🤣
17/04/2025

Ambuye kumwambako za ma cartoonzi chonde zindipitilire ine🤣

17/04/2025

A Landlord amvekere:
Iwe ukumadya ndiwo zopanda tomato pa plot panga pano?? Bweretsa ndikakataye kutseliku😂🤣😂

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when LANAZ Fazili posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share