04/06/2025
Nkhani yabho guys
choyamba tipepese kwamafans anthu ndi ena onse fukwa chakukhala nthawi yayitali osatulusa content izi zinali chonchi fukwa chamavuto ena omwe anali beyond our control koma chosangalasa ndichoti tabweraso ndipo takonza mavuto onse omwe analipo.
Ngati mbali imodzi yowonesela kuti takonzeka kukupasani zomwe mmakonda zija Saturday (07 june 2025) tikutulusa video (stool session) yathu yoyamba after many months .
tithokoze fukwa chakudekha kwanu ndikutilimbikisa kuti tiyambirenso poti mmakonda chipinda podcast