Dr Samson Wasayansi

  • Home
  • Dr Samson Wasayansi

Dr Samson Wasayansi Am The Digital Repairer ( Dr) working to help people understand digital era from 1 to 40 for free.
(1)

25/12/2024

Kodi mmadalira kwambiri network iti

TNM ?
AIRTEL?

25/12/2024

HELLO FAM
Winawake wandipanga tag somewhere alemba zoti WhatsApp will stop supporting older Android devices starting January 1, 2025, specifically those running Android KitKat (4.4) or older. Nde Ma phone omwe apangidwe affected ndi monga awa;
Samsung
- Galaxy S3
- Galaxy Note 2
- Galaxy Ace 3
- Galaxy S4 Mini
Motorola Devices
- Moto G (1st Gen)
- Razr HD
- Moto E (2014)
HTC Devices
- One X
- One X+
- Desire 500
- Desire 601
LG Devices
- Optimus G
- Nexus 4
- G2 Mini
- L90
Sony Devices
- Xperia Z
- Xperia SP
- Xperia T
- Xperia V

Apapatu chofunika ndikumenya magobo a serious kugula 4n ya android version yoyambira 7. So chifukwa chachikulu apangira izi chak*ti ku Whatsapp kuja ayamba kuonjezera ma features ena nde ma phone omwe Ali ndima android version yochepa sangagwire so izizi zikhoza kupangisa k*t privacy ya anthu omwe Ali ndima 4n awowo ikhale pa mbalambanda Kuma hackers nde ndibwino ma phone awawa asamalowe Whatsapp. In fact zili ngat kumpasa nsima ya m'memo mwana wakhanda.

15/12/2024

Mafunso akuchuluka

Mabwana, foni yanu ikasowa musadalire google kapena k*ti muli Email basi ipedzeka.

Zimatheka mwa apo ndi apo ndipo matsiku ano kupanga bypass phone kunaphweka.
Komanso foni yanu yobedwayo ikasowa , akaizimitsa, nkusintha location basi zonse zabalalikamo. Pajatu phone timaisintha nkuiikira ma configurations ena. Ndipo or mukuifufuza pa google imaonetsa information yaboza.

Ndiye nkhani yaikulu ndi kusunga serial number ya phone kapena IP address imene mmaipedza ku Bluetooth kuja kenako muzipanga trace phone kugwiritsa ntchito Frequency. Zili ngati k*tuma ma text ... Kodi kumafuna Data kapena google? Ayi. Nanga kuimba foni Nako kumadalira google? Ayi, foni Ili ndi zinthu zoti zizithandiza kuziwa k*ti phone Ili k*ti osati google yodalira mayunisi a network zovuta kalezi.

Za Email ndi 30% chabe

22/11/2024

GOOD MORNING 🌞

Hello Team Ngati Computer yanu imalemba zili pa chithuzipo mukafuna kupanga connect ku wifi or through hotspot yamu phon...
29/10/2024

Hello Team
Ngati Computer yanu imalemba zili pa chithuzipo mukafuna kupanga connect ku wifi or through hotspot yamu phone.Pali njira yoti mukhoza kupanga connect computer yanu ku phone kopanda Hotspot kumagwilisa ntchito internet ya phone yanu. Tiying'alule??
Let this post hit 1k likes tiyike video yake


Hello TeamPhoto ndaikayi ndi uthenga omwe ma scammers akumagwilisa ntchito kupanga hack ma Facebook account ambiri so pl...
28/10/2024

Hello Team
Photo ndaikayi ndi uthenga omwe ma scammers akumagwilisa ntchito kupanga hack ma Facebook account ambiri so please don't be deceived with these guys ndi akuba koopsa ndipo musapange click ma link awo akubelani ma account whenever you see this post kaya ndipa account ya nzanu just know amupangira hack account so please stay safe from being hacked


Hello FamAmene tili ndima luso osiyanasiyana oti tikhoza kumagwira ntchito online pali ka link apa muzidya Dolla online ...
18/10/2024

Hello Fam

Amene tili ndima luso osiyanasiyana oti tikhoza kumagwira ntchito online pali ka link apa muzidya Dolla online koma zimafunika effort yanu ineso ndawonera kwa wina wake nde am new to it koma yesani mwayi wanu nanu Mwina kudya nawo ma kobidi kuzapezeka k*t mukuwagaila a DR anuu😂😂
https://www.fiverr.com/pe/YR47YzK

One marketplace, millions of professional services. Browse. Buy. Done.

29/09/2024

MAFUNSO AMBIRI KU INBOX akungofunsa zoti
" BWANJI SIMUKUMAPANGANSO POST PAFUPIPAFUPI MONGA MUJA MMACHITIRA KALE?"

TEAM 🔥🔥
ifeyo maganyu amene timagwira samatipatsa nthawi kwambiri ndipo padera pa izi , ndimaonjedzeranso pepala lina ku university ya kunja k*ti ndidzaloledwe k*tsegula zinthu zina mtsogolomu

Ena akufunsa za ma Online class.
Ndinene k*ti zizatheka, nanga tingopangitsa Class popanda kukonzekera ngati ? Ulendo unowo class yake izizakhala ndi Certificate, so tikufuna zizikhalabe za serious zija. Zimene sizifuna Certificate zo tizizipanganso komano paja nkhani ndi k*thandizana hustle pa town.

But from today , ma post ndi kathithi

28/09/2024

UBWINO WA MA PHONE A POP 7

Choyamba mtengo wake umakhalako witsikirapo , paja a Tecno cholinga chawo ndi choti muno mu Africa anthu ambiri akhale ndi ma smartphone

2. Ambiri samasweka touch chisawawa makamaka mukawagonera , mukawagwetsa komano ngati afika poipa amatha kusweka kulibe cha muyaya.
3. Battery limayetserako kulimba ndipo Kwa amene amayenda maulendo aataliatali atha kukafika ulendo wawo isanathimebe. Komano simachedwa k*tha mukamalowetsamo magemu ndi zina.

4. Imazaza mukafikitsa ma GB amene analemba ku ma settings a storage or ku file manager ko, si mazaza ndi zinthu zochepa monga mmene mafoni ena amapangira.

Komano osaiwalanso zimene TINANENA MU post yoyamba ija, Mafoni alinso kufooka kwawo

26/09/2024

TEAM 🔥
1111? 1212?

26/09/2024

Big shout out to my newest top fans! Precious Jones Ndeule, Matious Vincent, Anderson Bakali, Patrick Kuwana Wa Chimtali, Cathy Panky J Mpate, Bwax Bamusi, Kondwan Kho Milanzi, PRØMISE MASØÑGØLÄ, Hezekiah Bikoko Edwin, Noel Nana, Dento Kenneth Dalion, Moises Francisco Pedro Candrinho, Auze Mboba, Emmanuel Nkhoma, Stevie Thimbula, George Maluwa, Moffat Nkhonjera, Jonathan Chingwandu, Ada Aku Kingston, 全彼成績, Jacco Chima, Manizo Wa Lesten, Alexander Chatuwa, Kelvin Saga Matupa, Henry Iziah David, Timothy Z J Loyce, Jussu James, Petro Nkakasi, Starford Asitho Mankhokwe, Emmanuel Julius, William George Junior, Tita Kachotsa, Kapyola Amos, Mphatso Grant, Evance Richard, Thank Thank, Anthony K Chakondwa, Erijah Jere, Joseph L Milosi, Đęñťøz Dëññiš Mšíwâ Çhûñğã, Maggie Magona, Mlongoti Happy Solomon, Fophwe Juzzy, Rodwell Buliana, Petro Hita, Slams DE King, Blessings Peter, Alinafe Malisiza, Msekanawana Chiwozga Gondwe, Thomas Ephraim Galelo

22/09/2024

Team 🔥

POP 7 ndi SPARK ALIYENSE
MMAKONDA ITI?

15/09/2024

TEAM 🔥

LERO NDI YA 1111 KAPENA 1212?

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dr Samson Wasayansi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share