Malawi social media network xxv

  • Home
  • Malawi social media network xxv

Malawi social media network xxv Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malawi social media network xxv, Digital creator, .

TNM SUPER LEAGUE LOG TABLE # Team P GD Pts1.Silver Strikers 7 15 192. FCB Nyasa Big Bullets 7   6  133. Mzuzu City Hamme...
25/05/2024

TNM SUPER LEAGUE LOG TABLE

# Team P GD Pts

1.Silver Strikers 7 15 19
2. FCB Nyasa Big Bullets 7 6 13
3. Mzuzu City Hammers 7 1 13
4. Mighty Mukuru Wanderers 7 5 12
5.Kamuzu Barracks 7 3 12
6. Civo United 8 1 11
7. Mighty Tigers 7 1 11
8. Moyale Barracks 7 3 10
9. Creck Sporting Club 7 0 10
10. Karonga United 7 -1 9
11. Dedza Dynamos 7 0 8
12. FOMO FC 7 -5 7
13. MAFCO 7 -7 6
14. Chitipa United 8 -6 5
15. Bangwe All Stars 7 -5 3
16.Baka City 7 -8 2

Where is your team?

Chenjelani nao akazi okhala ndi azimzawo achimuna๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
24/05/2024

Chenjelani nao akazi okhala ndi azimzawo achimuna๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

TAMIA JA AM'MANGA KU LILONGWEWofalitsa nkhani pa polisi ya Lingadzi ku Lilongwe, Cassim Manda watsimikizira Timveni Onli...
14/03/2024

TAMIA JA AM'MANGA KU LILONGWE

Wofalitsa nkhani pa polisi ya Lingadzi ku Lilongwe, Cassim Manda watsimikizira Timveni Online kuti apolisi amanga Tamia Ja yemwe dzina lake lenileni ndi Hannah Jabes pankhani yokhudza kuba ndalama yokwana MK8 million.

Manda wati munthu wina wochita malonda kumbuyo-ku adandaula kuti Tamia anazembaitsa ndalamayi pomwe akuti adamutumizira mwangozi.

Malinga ndi Manda, Tamia ja adatsimikiza kuti adalandira ndalamayi ndipo adati amubwezera wamalonda-yo koma mpaka pano sizinachitike

Please follow our page ๐Ÿ™ for more

Eeeeeeeh!!!  Mkhondo yoopsa pakati pa jb nd Abiti yavutila2๐Ÿ™Œ ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
17/02/2024

Eeeeeeeh!!! Mkhondo yoopsa pakati pa jb nd Abiti yavutila2๐Ÿ™Œ ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

God will change your life for good this coming 2024 โค๏ธโค๏ธโค๏ธ
26/12/2023

God will change your life for good this coming 2024 โค๏ธโค๏ธโค๏ธ

24/12/2023

Aneba agula fridge komatu nd nkhuku zomwe zkumwa madz ozizila ๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…

24/12/2023

First born akati alangize amachita kuiwala Zoti nayeso ndi mwanatu๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ

Ayi siyemweyo abaleee ๐Ÿ’”๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
21/12/2023

Ayi siyemweyo abaleee ๐Ÿ’”๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

18/12/2023

Kodi Ku police ndiku saloon amamanga bwino ndikuti?๐Ÿ˜Šndikufuna kumangidwa ine๐Ÿ˜”

She has finally found what she has been searching in my phone ๐Ÿ˜๐Ÿ˜‚๐Ÿคฃ๐Ÿ˜๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜
17/12/2023

She has finally found what she has been searching in my phone ๐Ÿ˜๐Ÿ˜‚๐Ÿคฃ๐Ÿ˜๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜

Moti zikuchitikadi ndithu izizi?  Nduna zanu Amfumu Tay Grin zikufumsa kumudzi kuno๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜Love โค๏ธ in Tokyo ๐Ÿ—ผ
16/12/2023

Moti zikuchitikadi ndithu izizi? Nduna zanu Amfumu Tay Grin zikufumsa kumudzi kuno๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜

Love โค๏ธ in Tokyo ๐Ÿ—ผ

16/12/2023

Kodi ukamapita ku Israel mkazi ukumamusiya konkuno?๐Ÿ˜ณ akufumsa batchala wa mudzi kuno๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚๐Ÿ’”๐Ÿƒ๐Ÿƒ

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi social media network xxv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share