Malawi Zama boma news

  • Home
  • Malawi Zama boma news

Malawi Zama boma news Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malawi Zama boma news, Media/News Company, .

Jam Kaunda ndiye mwini wa Vision2020 (Tonse Solutions 2009-2012)I was the one whp invetes the 5G spectrum with ubiquit b...
26/07/2020

Jam Kaunda ndiye mwini wa Vision2020 (Tonse Solutions 2009-2012)

I was the one whp invetes the 5G spectrum with ubiquit base station foe data offload. Only cliwnt device has to tap the signal by (ICU and twp finger follow for peace).

Noq its Tonse Alliance of Tonse wiMax 4G now last mile connectiviry (LTE)

Ask Paido paso and Anold Soko to locate Ligomeka to )


Lawyer wakale wa late Bingu says Dr Dan Namarika was foeced to poison the HE ask Z Allan Ntata is my witness thats why akuti APM atule pansi udindo ija inali treason iye ndiye mboniyo nchifukwa anamugwetsa Ben Phiri the pupet Master. Afuse Randera Hardware and Plusten od Chunrahs who have villas in Zambia, Abdul Azizi of blocl buater ndi mwini wake wa poundstretcher Zambia

24/07/2020

Breaking! Ligomeka the IT wizard, says He can trace the albino bones on dark internet where 80% of real dirty deals occur, if Chance is given with help of Chinsapo community of children he trained.

Breaking! Mzukwa wauka ku area 24 Ngwenya kuseli kwa phiri la mwala muchigayo Cha "Living Christ".Iye akuti Mayankho a y...
23/07/2020

Breaking! Mzukwa wauka ku area 24 Ngwenya kuseli kwa phiri la mwala muchigayo Cha "Living Christ".

Iye akuti Mayankho a yemwe amagula mafupa Ali Munyimbo ija ya ndizaulura ndi Nsambi. Akuti Mutharika amagula mafupawo kumupatsa Bushiri kuti Azungu azilengela moyo wina monga anailura Yohane kuchubvumbulutso kuti akafa azausidwa ndi mphabvu ya aneneri amafumu onyenga kwa Mulungu ya mafupa. Ndipo APM uja ndi mzukwa wa alubino anaumuutsa ndi Bushiri yemweyo. Munthuyu akufanana ndi nyani ndipo akuti wabwera kuzayankha a Malawi kuti makiyi a Boma Ali ndi JB ndi GCK cameras spy wake uja akuziwana ndi Chisale. Anthuwa ndi amodzi ndi kusataniki ndi grace Chinga anamuika muchigayo ku Zambia walumbilanso mudzina la Mulungu kuti mudikire imfa ya Munthu wamkulu yemwe JB anamupatsa makiyi aboma la Malawi omwe amathandauza pa makaka a chipani chake. A Malawi mwawoloka kamba ka imfa ya Grace, Munthuyu, ndi Mwazi wa alubino. Padali pano msinganga wa pa Chigayo Living Christ wabera kuzamuchiza Munthuyu. Ati computer munayamba ndinu nzeru zabawo ndipo Covid ndi Malungu adzinyama mankhala ake ndi mchere wambili ndi madzi mwachikulupiliro ngakhale a science akudziwa fufuzani. Mukanika mumvere bwino Mayankho anakupatsani kale Prophets Matafale (Mumamunyoza & Time mark), Gift Fumulani (Moto), Grace Chinga ndi Antony Makondetsa mbendera. Ati Bingu uja anamupha dala chifukwa anapupuluma kusintha dzuwa ndipo anamulande ndege yomwe Mulungu anamugulira ndikugawana ndalama kunamizila asilikali. Ndege ili ndi Bushiri. Mukumbuke Kelvin Sulugwe atayambana ndi Bushiri anangoti Depeco nayi koma zandege sindikuziwa kanthu, amatanthauza chani

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Zama boma news posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share