The Sight

The Sight Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from The Sight, Media/News Company, .
(1)

 Galimoto la mtundu wa minibus lomwe nambala yake ndi DA 4336 layaka moto pa malo omwetsera mafuta a Simso ku Area 25  m...
13/11/2024


Galimoto la mtundu wa minibus lomwe nambala yake ndi DA 4336 layaka moto pa malo omwetsera mafuta a Simso ku Area 25 mu mzinda Lilongwe.

Malingana ndi malipoti omwe The Sight yapeza ati, galimotoli linali pa nzere othiritsa mafuta koma linayamba kuyaka litangothiridwa mafutawa kamba kakutentha kwa engine ndipo dalayivala anatuluka mwachangu m'galimotoli atawona motowu koma palibe yemwe wavulara.

Galimoto zozimitsa moto zili pa malowa kugwira ntchito yake.

Pakanali pano apolisi sanayankhulepo zokhudza nkhaniyi.

Wolemba:Comfort Braziz-Nkhoma



Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati, anthu omwe akukhudzidwa ndi njala m'boma la Mchinji kamba kangamba im...
13/11/2024

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati, anthu omwe akukhudzidwa ndi njala m'boma la Mchinji kamba kangamba imene inalipo m'chaka chino, asadandawure chifukwa boma posachedwapa liyamba kuthandiza mawanja onse anakhudzidwawa

A Chakwera ayankhula izi lero m'bomali m'misonkhano yawo yoyimayima.

Mtsogoleri-yu wati, boma la Mchinji ndi limodzi mwa maboma amene akuchita bwino pa nkhani yotukula chuma cha dziko lino komanso zaulimi kotero wati, boma layika ndalama zomwe zimatchedwa "Constituency Development Funds (CDF)" m'madera onse ndicholinga chopititsa chitukuko pa tsogolo.

A Chakwera ati, achinyamata a m'bomali sanayiwalidwe pomwe ati, akweza mulingo wa ndalama zangongole za National Economic Empowerment Fund (NEEF) kuti achinyamata otenga ngongoleyi akhale ambiri ndicholinga azipanga mabizinezi osiyanasiyana ndi kumadziyimira pa okha.

Powonjezera iwo apempha anthu aku Mchinji kuti akalembetse mwa unyinji mu mkawundula wodzavota pomwe ati nthawi yoponya voti-yi sili patali pomwe anawonjezera kuti voti yawo ili ndi kuthekera kosankha chitukuko chimene boma linayamba kale.

A Chakwera anachititsa misonkhano yawo yoyimayimayi m'malo a Waliranji, Tembwe, Kamwendo, Matutu, Kapiri, Mkanda ndi Mchinji Boma.

Wolemba: Patrick Chilinda - Mchinji



Pali chiopsezo kuti tsiku la lero mwina silingathe bwino ngati ziwonetsero zimene zakonzedwa ndi zipani zina zotsutsa bo...
13/11/2024

Pali chiopsezo kuti tsiku la lero mwina silingathe bwino ngati ziwonetsero zimene zakonzedwa ndi zipani zina zotsutsa boma zingachitike.

Izi zili chomwechi pomwe anyamata azitho onyamula zikwanje akukulabe mphamvu ndi kuthamangitsa anthu ena omwe akukayikiridwa kuti akufuna kutenga nawo mbali kupanga nawo ziwonetsero ngakhale apolisi zikuwonetsa kuti nawonso akhwimitsa chitetenzo pa bwalo la Lilongwe community pamene ziwonetserozi zimafuna kuyambira.

Tikunena pano apolisi ndi mabausa-wa akumawonana ndithu koma sakufikiridwa kuti asiye zimene mabausa-wa akuchita. Mwina tinene kuti nawonso akuwopa kuthiridwa zikwanje.

Komabe Levie Liwemba wati, ziwonetsero-zi zichitika ndithu lero..... Kodi inu mukuganiza kuti zikutha mwa mtendere ndithu izizi?....

The Sight, imangowunikira malingana ndi m'mene zinthu zili pakanali pano komanso kukula mphamvu kumene kulipo ku mbali zonse ziwiri kuti ngati kukula mphamvuku kungapitilire ku mbali zonsezi china chake cha chilendo chikhoza kudza.

Wolemba: Patrick Chilinda




Anthu ena omwe akuoneka kuti anyamula zikwanje akuthamangisa gulu la anthu Lomwe linasonkhana pa bwalo lazamasewero la L...
13/11/2024

Anthu ena omwe akuoneka kuti anyamula zikwanje akuthamangisa gulu la anthu Lomwe linasonkhana pa bwalo lazamasewero la Lilongwe community ground lomwe linakonza kuti lipange ziwonetsero zosonyeza kusakhutira ndi bungwe loyendetsa zisankho mdziko lino la Malawi Electoral Commission (MEC) komanso bungwe loyendetsa kalembera la National Registration Bureua (NRB).

Ziwonetserozi zomwe zinakonzedwa ndi zipani zotsutsa zosiyanasiyana Mdziko muno zimayenera kukhalako lero kuyambira pabwaloli.

Koma mma ripoti omwe The sight media group lawuzidwa, Bwana Nkubwa wa boma la Lilongwe a Lawford Pangani eti anayimitsa ziwonetserozi ponena kuti a Polisi anali otangwanidwa ndi ntchito Zina kotere sakanakwanitsa kupereka chitetezo chokwanira ma ziwonetserozi.

Zipani zotsutsa zosiyanasiyana Mdziko muno lachiwiri sabata ino zinauza atolankhani kuti Zikhale zupangitsa ziwonetserozi ndicholinga chofuna kuwumiriza Wapampando wa bungwe la MEC a Annabel Mtalimanja komanso Akuluakulu ena a bungweli Komanso bungwe la NRB kutula pansi udindo, komanso kuwumiriza bungwe la MEC kuthetsa Mgwirizano wake ndi kampani yomwe yapatsidwa ntchito yoperekera Zipangizo zogwilira ntchito pachisankho Cha Chaka chamawa yotchedwa Smartmatic.

Reported by Benjamin Kafwirangachi Nyirenda, Lilongwe




Pofuna kuchepetsa mtunda kwa ophunzira ena omwe amayenda wapansi kuti akapeze maphunziro awo pa Mbera Community Day Seco...
13/11/2024

Pofuna kuchepetsa mtunda kwa ophunzira ena omwe amayenda wapansi kuti akapeze maphunziro awo pa Mbera Community Day Secondary School m'boma la Balaka, a Toleza Farm’s Sawali Foundation apereka njinga 20 kwa ophunzira apa sukuluyi.

Poyankhula popereka thandizoli ku Toleza Farm a Francis Billiat wati, njingazi zaperekedwa ndicholinga chofuna kuchepetsa mtunda omwe ophunzira-wa amayenda komanso kuwalimbikitsa pa maphunziro awo.

Billiat wati, ali ndichikhulupiriro kuti ophunzira omwe amachedwa chifukwa chakutalika kwa mtundu azipezeka mkalasi mu nthawi yake kotero wapempha ophunzira omwe alandira njingazi kuti azizisamala.

M'mau ake wachiwiri kwa mphunzitsi wa mkulu pa sukuluyi a James Ndlovu ati, ophunzira omwe alandira njingazi atengera mtunda omwe amayenda ndipo ati ali ndichikhulupiriro kuti atsikana omwe anali ndimaganizo ofuna kusiya sukulu chifukwa cha mtunda akhala akupiriza maphunziro awo.

M'modzi mwa ophunzira yemwe walandira nawo thandizoli Alinafe Potani wati, wakhala akuvutika mayendedwe komanso kuchedwa mkalasi pomwe wati ndi thandizoli lipangitsa kuti asamachedwe ndikudzamaliza maphunziro ake aku sekondale mosavuta.

Potani watinso kuti, nthawi zambiri samawerenga ku nyumba chifukwa amakhala watopa ndi mtunda womwe amayenda koma tsopano wati nthawi yowerenga azikhala nayo.

Wolemba: Patrick Chilinda



Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera lero akhala  boma la mchinji ndicholinga chofuna kulimbikitsa anthu kutenga...
13/11/2024

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera lero akhala boma la mchinji ndicholinga chofuna kulimbikitsa anthu kutenga nawo mbali mukalembera wachiwiri wachisankho.

Iye akhalaso akuchita misonkhano yoyimayima malo osiyanasoyiyana monga waliranji, Tembwe, kamwendo, Matutu mwa ena.

Izi zikuchitika pamene Mtsogoleriyu akulimbikitsa anthu kutenga nawo gawo pachisankho cha mchaka chamawa.

Wolemba Shalom Manyozo



CRECK TERMINATES MTETEMERA'S CONTRACTCreck Sporting Club has announced that they have  terminated it's contract with hea...
13/11/2024

CRECK TERMINATES MTETEMERA'S CONTRACT

Creck Sporting Club has announced that they have terminated it's contract with head coach MacDonald Mtetemera on mutual consent due to a series of poor performances that the club has been subjected to.

The club's Chief Executive Officer Muhammad Seleman has confirmed about the development.

According to the club, Mtetemera's remaining 17 month contract has been terminated on performance grounds despite the club calling for Mtetemera to appear before the team's committee to address the issue.

The club has further stated it will calculate every benefit Mtetemera would have collected fr his remaining 17 months including his salary and allowances and will pay Mtetemera in no time.

This development means that Former Flames captain Joseph Kamwendo will assume the top seat at the club as interim head coach.

Reported by Benjamin Kafwirangachi Nyirenda, Lilongwe




ZANYENGO KUTENGERA NTHAMBI YOWONA ZA NYENGO NDIKUSINTHA KWA NYENGOM’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 13 OCTOBE...
12/11/2024

ZANYENGO KUTENGERA NTHAMBI YOWONA ZA NYENGO NDIKUSINTHA KWA NYENGO

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 13 OCTOBER, 2024

Tiyembekezere nyengo ya mphepo, ya mitambo yapatali patali ndi ya mvula ya mabingu usiku uno ndi mawa m’mawa.

MMENE NYENGO IKHALIRE MAWA MASANA, PA
13 OCTOBER , 2024

Mawa masana, kudzatentha, kudzakhala kwa mphepo ndi kwamitambo ndipo mvula ya mabingu ikuyembekezereka m’madera ena akumwera.

CHENJEZO

Nthawi zambiri, mvula ya mabingu imabwera ndi mphenzi komanso mphepo ya mkuntho. Choncho, tipewe kubisala pansi pa mitengo.

KAOMBEDWE KA MPHEPO

Mphepo idziomba kuchokera kumwera chakumvuma...

Samuel Hope Mulima | The Sight Weather






Kusadziwa Nkufa Komwe, Kharani Otsogora, Dziwani Zanyengo .

MEC ANNOUNCES NOMINATION PAPER FEESThe Malawi Electoral Commission (MEC) has announced nomination papers fees to be paid...
12/11/2024

MEC ANNOUNCES NOMINATION PAPER FEES

The Malawi Electoral Commission (MEC) has announced nomination papers fees to be paid by aspiring candidates in the upcoming general elections .

This is according to a general notice released by the commission dated 11th of November 2024 signed by MEC Chairperson Justice Annabel Mtalimanja.

Through the notice MEC has stated that the Presedential candidacy nomination paper has been set at K10 million while the Member of Parliament and the Ward councillor nomination papers have been set at K2.5 million and K500,000 respectively.

Despite this being the case MEC has also said that it has considered reducing the fee for Candidates with disssabilities, Female Candidates as well as Youthful candidates in an effort to encourage them to take part in the elections.

The country is expected to go to polls on the 17th of September 2024 in a bid to elect President, Members of parliament and Ward Councillors.

Reported by Benjamin Kafwirangachi Nyirenda, Lilongwe




MALAWI OPPOSITION PARTIES, CONCERNED CITIZENS TO HOLD PRESSER IN LILONGWEA first ever collaborative press briefing by a ...
12/11/2024

MALAWI OPPOSITION PARTIES, CONCERNED CITIZENS TO HOLD PRESSER IN LILONGWE

A first ever collaborative press briefing by a large grouping of Malawi's opposition parties and concerned citizens after 2020 is slated to take place Tuesday 12 November 2024 at the Alliance for Democracy (AFORD) headquarters in Lilongwe.

According to a flyer making rounds on major social media platforms, the press briefing is expected to involve opposition Democratic Progressive Party (DPP), United Democratic Front (UDF), UTM, AFORD, People's Party (PP), LEF Party, MRP, Economic Freedom Movement, Centre for Democracy Watch and Malawi First movement - and it will dwell on the agenda of demonstrations and vigils against Malawi Electoral Commission (MEC) and National Registration Bureau (NRB) slated for 13 November 2024.

The briefing, which begins at 11:30am, is expected to be aired live on Zodiak Broadcasting Station, Times Television and Radio and Facebook platforms of these major private stations.

Reported by Clement Magombo, Lilongwe




KAMWENDO WATI SATENGA NAWO MBALI MU MPIKISANO WA MASO AWARDSPomwe anthu amuluso osiyanasoyiyana akupitiliza kusawonetsa ...
12/11/2024

KAMWENDO WATI SATENGA NAWO MBALI MU MPIKISANO WA MASO AWARDS

Pomwe anthu amuluso osiyanasoyiyana akupitiliza kusawonetsa chidwi chotenga nawo mbali mu mpikisano wa Maso awards naye katswiri oyimba nyimbo za uzimu Ethel kamwendo wati sapikisana nawo.

Mayi Kamwendo anena izi kudzera pa tsamba lawo la Facebook usiku wangothawu

Iwo awuza mtundu wa a Malawi komaso oyendetsa mpikisanuwu kuti anachiona chopambana kuwayika guluyi koma pakadali pano akufuna amalizitse ma pulojekiti amene anawayamba ndipo akhala akutuluka mchaka chamawa.

Pakadali pano oyimba ena Monga Zeze Kingston, Gwamba komaso ochita zisudzo monga Che mandota ndi Mr jokes sakupikisana nawo pa mphotoyi.

Wolemba Shalom Manyozo




PASUWA AND MPONDA RESUME FLAMES ROLES New Flames interim technical team headed by FCB Nyasa Big Bullets coach Kalisto Pa...
12/11/2024

PASUWA AND MPONDA RESUME FLAMES ROLES

New Flames interim technical team headed by FCB Nyasa Big Bullets coach Kalisto Pasuwa resumed their role in the flames dugouts on Monday this week ahead of a double African Cup of Nations qualifiers fixture against Burundi and Burkina Faso.

The team had their first training session at the Bingu National Stadium in Lilongwe with 13 local based players present for the first session.

But speaking to the media in Lilongwe Pasuwa who is being assisted by Silver Strikers Coach Peter Mponda , has since expressed optimism in the upcoming flames assignments stating that the team is capable of winning these encounters.

Pasuwa has also stated that he and his team are focused on assembling and building a strong team capable of competing with big teams in the continent.

The Flames will travel to Ivory Coast this afternoon ahead of a date with Burundi on the 14th of November in the AFCON qualifiers fixture before they meet Burkina Faso on the 18th of November at the Bingu National Stadium in Lilongwe.

Reported by Benjamin Kafwirangachi Nyirenda, Lilongwe




ZANYENGO KUTENGERA NTHAMBI YOWONA ZA NYENGO NDIKUSINTHA KWA NYENGOM’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 12  OCTOB...
11/11/2024

ZANYENGO KUTENGERA NTHAMBI YOWONA ZA NYENGO NDIKUSINTHA KWA NYENGO

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 12 OCTOBER, 2024

Tiyembekezere nyengo ya mphepo, ya mitambo yapatali patali ndi ya mvula ya mabingu ya apo ndi apo m’madera akumpoto ndi ena akumwera komanso m’mbali mwa nyanja usiku uno ndi mawa m’mawa.

MMENE NYENGO IKHALIRE MAWA MASANA, PA
12 OCTOBER , 2024

Mawa masana, kudzatentha, kudzakhala kwa mphepo ndi kwamitambo ndipo mvula ya mabingu ikuyembekezereka m’madera ena akumwera.

CHENJEZO

Nthawi zambiri, mvula ya mabingu imabwera ndi mphenzi komanso mphepo ya mkuntho. Choncho, tipewe kubisala pansi pa mitengo.

KAOMBEDWE KA MPHEPO

Idziomba kuchokera kumvuma koma pofika mawa masana izidzaomba kuchokera kumwera chakumvuma.

Samuel Hope Mulima | The Sight Weather






Kusadziwa Nkufa Komwe, Kharani Otsogora, Dziwani Zanyengo .

Mtsogoleri wachipani Cha United Transformation Movement (UTM)  Michael Usi walengeza kuti sapikisana nawo ku msonkhano w...
11/11/2024

Mtsogoleri wachipani Cha United Transformation Movement (UTM) Michael Usi walengeza kuti sapikisana nawo ku msonkhano waukulu wachipanichi omwe ukhale ukuchitika loweruka sabata ino.

Mwazina a Usi auza Nyumba zofalitsa Nkhani kuti ganizoli laza kamba koti komiti yayikulu yoyendetsa chipanichi lotchedwa National Executive Committee (NEC) silinatsatse malamulo achipanichi pokonzekera msonkhanowu.

Iwo ati sakufuna kukhuzidwa ndikuphwanya malamulo a chipanichi pofuna kuteteza mbiri yawo ngati wachiwiri kwa Mtsogoleri wadziko lino.

A Usi amayenera kupereka kalata zowayenereza kuyimira pa Udindo was mtsogoleri wachipanichi ku msonkhano waukulu lero potengera kuti lero nditsiku lomaliza lomwe chipanichi chikulandira zikalatazi.

Mene zateremu Mlembi wachipanichi a Patricia Kaliati, Dr Dalitso Kabambe, Dr Mathews Mtumbuka komanso a Newton Kambala ndiwo apereka zikalata zovomereza kukayimira pa udindowu ku msonkhanowu.

Wolemba Benjamin Kafwirangachi Nyirenda, Lilongwe




Renowned good governance activist Undule Mwakasungula has called upon Malawi Electoral Commission (MEC) to collaborate w...
09/11/2024

Renowned good governance activist Undule Mwakasungula has called upon Malawi Electoral Commission (MEC) to collaborate with Civil Society Organizations (CSO's) in the country to reach out to maltitudes in a drive to encourage citizens in the country to actively participate in phase two of the voter registration exercise.

Mwakasungula has made the remarks through a press statement released by him today the 9th of November 2024.

Through his statement Mwakasungula has shown discontent over low turnout of people in voter registration centers during the first phase of the exercise which has seen only 65% of the projected voters in the centers targeted in this phase registering.

Mwakasungula has also stated that the 56.7% male voters and the 72% female registered voters in the first phase clearly shows the gap between Male and Female registrations heading into the second phase of the voter registration exercise.

Mwakasungula has then called upon MEC to join forces with CSO's in the country to ensure that messages reach the mass on the importance of turning out in large numbers to register but also need for these two groups to encourage more Male voters to take part in the registration process for this will ensure that no one is left behind in exercising people's constitutional rights of voting and democracy.

The second phase of voter registration exercise has commenced today the 9th of November 2024 .

Article by Benjamin Kafwirangachi Nyirenda




Khwimbi la anthu likuyembekezereka  kukhamukila kubwalo la za masewero la Bingu masana ano pamene ma timu ampira wamiyen...
09/11/2024

Khwimbi la anthu likuyembekezereka kukhamukila kubwalo la za masewero la Bingu masana ano pamene ma timu ampira wamiyendo a Silver Strikers komanso FCB Nyasa Big Bullets akuyembekezeka kukumana mundime yotsiliza ya chikho cha Airtel top 8.

Kupatula kudzawonelera komanso kuchemelera masewerowa anthu ochita malonda osiyana-siyana monga aziwaya za tchipisi, ogulitsa Mandasi, zakumwa kungotchulapo zochepa afika kale pamalowa ndicholinga chofuna kupeza kangachepe pamaserowa.

Polankhulana ndi The Sight, Modzi mwa ochita malonda pamalowa wati ndiwokondwa kwambiri ndimasewerowa kaamba kakuti lero akuyembekezera kuti bizinezi yake iyenda bwino ndipo apita kunyumba akuyimba lokoma.

Masewerowa akhala amodzi mwamasewero omwe apeleke chikoka kumtundu wa anthu kaamba kakuti Silver Strikers yomwe imadziwika kuti Ma Central Bankers komanso FCB Nyasa Big Bullets yomwe imadziwika kuti Maule ndi amodzi mwamatimu akulu-akulu mdziko muno.

Silver Strikers ikuchita bwino ndipo ikutsogolera ligi yayikulu ya TNM pomwe Bullets ndiyomwe ikuteteza chikhochi.

Wolemba: Comfort Braziz-Nkhoma, (BNS-Lilongwe)




It's the 2024 Airtel Top 8 Finals!!FCB Nyasa Big Bullets vs Silver Strikers at Bingu National Stadium.Who will carry the...
09/11/2024

It's the 2024 Airtel Top 8 Finals!!

FCB Nyasa Big Bullets vs Silver Strikers at Bingu National Stadium.

Who will carry the day?

Drop your predictions.

 Ahead of Today's Airtel Top 8 cup Finals Match between FCB Nyasa Big Bullets and Silver Strikers, 🚦 Stadium Traffic Tip...
09/11/2024



Ahead of Today's Airtel Top 8 cup Finals Match between FCB Nyasa Big Bullets and Silver Strikers,

🚦 Stadium Traffic Tips for Airtel Top 8 Final 🚦

Attention Fans!

As we head towards the thrilling Airtel Top 8 Final, here are the traffic tips to ensure a smooth experience:

🛣️ Main Roads to the Stadium:
- Presidential Way is expected to experience increased traffic. Expect delays and plan your journey early.
- Gateway Mall - Area 49 Road may see rising traffic as we get closer to kick-off time.

🚗 Parking Information:
- Gate 1 (along Presidential Way) is designated for fans with standard tickets.
- Gate 2 (along Gateway Mall - Area 49 Road) is reserved for VIP and Corporate Box ticket holders.

🚨 Important Tips:
- Use carpooling to help reduce traffic congestion.
- Arrive early to avoid last-minute rush and secure your spot.
- Follow the directions from traffic officers for a smooth entry and exit.

Let’s make it a safe and enjoyable match day for everyone!

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Sight posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share