Blessings and Olivia News Desk

  • Home
  • Blessings and Olivia News Desk

Blessings and Olivia News Desk Sharing news ,, mainly current affairs

16/11/2023

Blessings and Olivia News Desk
.
There are a number of potential solutions to address the devaluation of the kwacha. One option is to increase the country's exports, which would help to bring in more foreign currency and stabilize the exchange rate. Another option is to reduce government spending and increase taxes, which would help to reduce the deficit and stabilize the economy. The central bank could also consider increasing interest rates, which would make Malawian assets more attractive to foreign investors and help to bring in more foreign currency.
What do you think would be the most effective solution?

suggestion from Blessings Bakali

11/11/2023




Pamene ndalama yakwacha aichepetsa mphamvu ndi 44.90% malinga ndi bank yaikulu ya reserve, kampani yazamaulendo a m'mulengalenga ya South African Airlines yaimitsa ntchito zake zogulitsa matikiti a ndege m'ziko muno. Kutsatira mavuto azachuma omwe akhudza kwambiri dziko lino kwa masiku ochepa chabe kuyambira pomwe ndalamayi adaichepetsa mphamvu, wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wachipani cha UTM Dr. Saulos Klaus Chilima waudza akatswiri pankhani zachuma kuti apedze njira zothetsera mavuto azachuma amene dziko lino likudutsamo.

(-Reported by Blessings Bakali -Zomba.)

  Kutsatira kutsika mphamvu kwa ndalama ya kwacha ndi 44.90% kwadzetsa mavuto aakulu kunkhani yamayendedwe. Mwazinakhons...
10/11/2023




Kutsatira kutsika mphamvu kwa ndalama ya kwacha ndi 44.90% kwadzetsa mavuto aakulu kunkhani yamayendedwe. Mwazina
khonsolo ya Lilongwe yalengedza zakukwera kwa mitengo yoyendera pa galimoto za mtundu wa minibasi ndi 44% kamba kakukwera kwamitengo yogulira mafuta a galimoto.

(-Reported by Blessings Bakali-Zomba)

10/11/2023




Mphunzitsi watimu ya Mighty Mukuru Wanderers Mark Harrisson wati osewera kutsogolo wa timu ya kamudzu barracks (Olsen Kanjila)ali pa m'ndandanda wa osewera omwe akuwafuna kuti apite ku team ya wanderes nsika ogula ndikugulitsa osewera ukadzatsekulidwa mu chigawo china cha mpikisano wa TNM SUPER LEAGUE wa chaka cha m'mawa . Mark Harrisson wati osewelayu ndi wabwino kwambiri pa zomwe akufuna kupeza mwa osewera akutsogolo kwa timuyi ndipo wati akusaka Saka osewela ena omwe azathe kulimbitsa kutsogolo kwa timuyi potsatira kufooka komwe kukuoneka kutsogolo kwa team yi pokanika kugoletsa zigoli zochuluka mu mpikisano wa chaka chino.

Pamene kwatsala masiku ochepa chabe kuti mpikisano wa (TNM SUPER LEAGUE) ufike kumapeto, Mark Harrisson wati ali ndi ntchito yaikulu yopedza osewera ena amene adzakwanitse kulimbitsa team yi.

(-Reported by Blessings Bakali-Zomba)

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Blessings and Olivia News Desk posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share