Mikozi

Mikozi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mikozi, Digital creator, .

15/10/2024

Potulutsa nyimbo chonde kumaonetsetsa kuti ili bwinodi chifukwa anthu afika potopa akumangokamba chilungamo 🙏
Bundle yadhula🙏

Lawyer wa gulu uja wayankha. Paja amamuopseza kuti asiye kuyankhula pomuwuza kuti amusumira ndipo apereke chindapusa cha...
11/10/2024

Lawyer wa gulu uja wayankha. Paja amamuopseza kuti asiye kuyankhula pomuwuza kuti amusumira ndipo apereke chindapusa cha K250 Million. Wangowayankha mawu awili: PLEASE SUE.

Alexious Kamangila 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

Anthu sakulankhula bwinoyi
10/10/2024

Anthu sakulankhula bwinoyi

Ma preparations ayambika :- Mawa Bwaku Mlakho
05/10/2024

Ma preparations ayambika :- Mawa Bwaku Mlakho

Pa Dyeratu ku Chikwawa, Friday li kukubwela Ma Blacks
02/10/2024

Pa Dyeratu ku Chikwawa, Friday li kukubwela Ma Blacks

Kwachuluka Mkangano, Ma Comedian ena akufuna aziti Haye Haye si comedian pamene anthu akuti mchikulireyu atha kukhala co...
02/10/2024

Kwachuluka Mkangano, Ma Comedian ena akufuna aziti Haye Haye si comedian pamene anthu akuti mchikulireyu atha kukhala comedian of the year

25/09/2024

Timangoyesa

25/09/2024

Kodi amati tasowayo ndindani

Matengelatengela. Phiyee Puleshaa
18/08/2024

Matengelatengela. Phiyee Puleshaa

04/08/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Omega Chidzala, Rich D Cow, Elick Ndaona

Koma zikuchitikadi izizi? Mpaka ma pulasitiki ?
04/08/2024

Koma zikuchitikadi izizi? Mpaka ma pulasitiki ?

Ku Chigumula chapa viphya boys ina yapha nkuphika galu  wa mtundu wa Maltese wa neighbor wawo poyesa ndi Kalulu.Boys yo ...
29/07/2024

Ku Chigumula chapa viphya boys ina yapha nkuphika galu wa mtundu wa Maltese wa neighbor wawo poyesa ndi Kalulu.

Boys yo imaweta akalulu ndikale ndiye usiku wu inabwela italedzela nkulakwitsa kugwila galu wa neba m'malo mwa kalulu mpaka kuyamba kumuphika.

Panopa Neba wavuta.
Boys ilile bwanji

Apolisi ya Lingadzi ku Lilongwe amanga bambo wa zaka 45  pomuganizira kuti ananamizira kuti wauka kwa akufa n'kukwatira ...
15/07/2024

Apolisi ya Lingadzi ku Lilongwe amanga bambo wa zaka 45 pomuganizira kuti ananamizira kuti wauka kwa akufa n'kukwatira mkazi wa malemu omwe anali mfumu, kenaka kukwatiranso akazi ena awiri.

Mneneri wa polisi ya Lingadzi a Cassim Manda wati chaka chatha mkulu yemwe amadzitcha kuti ndi mneneri wa Mulungu, adanyengerera abale a malemu ku Mtandire kuti atha kudzutsa mfumuyo kwa akufa.

Apa ati anapita kukatenga a Chipiliro Mbewe, kuwameta tsitsi ndi kuwaveka zovala zabwino. Kenaka ati adauza anamalira kuti mfumuyo yauka koma asadandaule za kusiyana maonekedwe popeza nthawi ikamapita nkhope idzabwerera adzayamba kuoneka ngati malemu.

A Manda apitiriza kuti a Mbewe adayamba kuonetsa khalidwe la chilendo kuphatikizapo kuledzera ndi kusuta zomwe zinadabwitsa a kubanja mpaka kukanena kwa mfumu ina.

Apa ndi pomwe ati woganiziridwayo anaulula kuti mneneriyo ndi yemwe anamupempha kuti anamizire kuti wauka kwa akufa.

A Mbewe, ochokera m'mudzi wa Zuze ku Dedza, akayankha mlandu wonamizira komanso kugwiririra pamene apolisi ali mkati kusaka mneneri wabodzayo.

Charisma and Tuno 👀😂
18/03/2024

Charisma and Tuno 👀😂

Awawa nde adayesetsa ndithu, koma ngati kuli kusamva ayi ndithu nkusamva kwanu komwe anthuni.
18/03/2024

Awawa nde adayesetsa ndithu, koma ngati kuli kusamva ayi ndithu nkusamva kwanu komwe anthuni.

19/01/2024

ANTHU OMWE AMAZIMVA NGATI ALOWA KALE KUMWAMBA NDIPO AKUNJOYA NDI JESUS
( Compiled by Kazembe Woo Jin Mateso )

1. Ma mechanic a ma German Car. Eeeh amakhala ngati tu anawapatsa dzina ndi Abraham or Mose. Kuona muvu yokhayo komanso malankhulidwe kuti mukagule "DSG Transmission oil."

2. Amene sanapangeko ngozi on the roads of Malawi. They will be like been driving since 2000 but zero accident record;

3. Those families with two cars. Abambo yawo. Mkazinso yake. Akati azipope: "Ine ndimangowaona anthu akamapita ku bridal shower ndi akazi awo."

4. Mfana amene wayenda BT - LL less than 3 hours. "Ndikuti ndakhazika ma TX, ma Vee Wee." Honda Fit mpaliro;

5. Anthu amene sanaguleko fuel mu chigubu. Matama akewo. "Ine mugalimoto mwanga simungapezeke chigubu."

6. Amene amagwiritsa ntchito oil wa 5W40. Oil uyuyu ndi odula kuposa bulangete la mu PEP. mmmmmm

7. Anthu amene amayima pa Chikondi Stopover kugula nyama. Umo agwilira takeaway box uku atapanila phone ndi mutu, zokuti nyama agulayo ndi ya 3000 one would think ndiyaK1 million. Muli demeti kwambiri;

8. Amene sanagule galimoto pa ngongole. Amalankhulatu motumbwa. "Ndimangowona anthu akutenga loan kugula galimoto. Galimoto kuwonongeka koma ngongole kumabwenzabe."

9. Anthu oyendetsa galimoto za manual. M'mene amakwinyila kunkhopemo akamva kuti sumatha. Anthuwa ndiovuta amwene.

10. Anthu amene galimoto zawo zili ndi ma leather seats. Umva mu galimoto mwanga olo utayile madzi pa mpando;

11. Anthu amene ali ndi comprehensive Insurance. Umva iwe tatiye ku police, all I need is police report andikhonzetsera a insurance. Komatu wangowapanga scratch

12. Ma guys omwe anagula galimoto kenaka plot, busy kuzipopa akuti "Plot umayenela uziloza ndi ma key a galimoto."

13. Anthu oyendera galimoto ya Push to Start. mmmmm zoti ndi Ractis ya Push to Start yo kuletsa tu.

14. Anthu oliza galimoto mogulula. Busy kukambirana kuti yakuti timalizila mu 2; yakuti timalizila mu 3. Za ziii

15. Anthu oyenda ndi tissue mu galimoto mwawo

22/08/2021

I was sleeping next to my wife when I got a notification from Facebook. I stood up to check; it was a friend request from a lady. I decided to go through her profile to know who she is. Finally, I found out that it was my old time school mate.

I accepted her friend request and I sent her a massage "Hello" since she was still online. She replied "Hi, I heard you are married with kids" I responded, "Yes". she said, I really love you and I'm willing to do whatever it takes just to be part of your life"

Hmmm, I quickly closed the chat to make sure my wife was sleeping.

I left the bed and sat on the chair that is in my bedroom.

I looked at my wife, she was deeply sleeping after the busy and exhausted day from work and house chores.

As I was still looking at her, something came into my mind. "This woman doesn't deserve to be cheated on, look at how safe and comfortable she's sleeping in our bedroom. She really trusted me so much that I can't hurt her" I started thinking, " she left her family, her caring mother, her Dad who at all times was providing almost everything she needs and her siblings who always brighten her day and joined me in my one bedroom apartment leaving her dad's mansion.

All these thoughts and more was driving me crazy. Then I asked myself, "how can I do this wickedness to this innocent woman?" So I hurriedly picked up my phone and hit the "BLOCK" button.

I turned to my wife and I walked straight to the bed and cuddled her and she adjusted herself to accommodate me.

I can't afford to loose her trust or make her cry. NEVER!

I was able to do that because I am a "Real" man. Real men don't cheat on their wives. Real men don't make their wives cry. Real men don't make their wives regret Marrying them. Real men value their wives more than any other woman.

Be the "Man" the "Real Man"

Love your wife
Never cheat.

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mikozi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share