Tsopano dziko muno odwala corona virus alipo anayi kutsatira kumwalira kwa modzi waiwo ku brantry
07/04/2020
Munthu modzi yemwe amadwala corona virus wa mwalira mu mzinda wa Brantry munthu ndi zimayi.
14/02/2020
madzi osefukira akuononga nyumba ku dwangwa kamba ka mvula yagwa mowilikiza dzulo ndi lero.
14/02/2020
moni amalawi zikomo kamba konkhala bata mpaka lero kuchokera tsiku lomwe nkhothi linapeleka chigamulo chake pa khani ya chisankho cha 21 may 2019 tiyeni tikondane. ndale zisationongele dziko lathu labwino. pepani nonse amene chigamulo sichinakukomeleni zimachitika pepani!!
Be the first to know and let us send you an email when Malawi News Agency posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.