DPP ndi chipani chobalalika. DPP ndi masanje enieni. Chonchi Mkumati DPP ingalowenso muboma?? Zosatheka.
FIFA President meets Chakwera
BREAKING NEWS CHITHYOLA BANDA TO WIN WITH 80% ELECTORAL SURVEYS SHOW
Despite all the propaganda against him, Poll Surveys still give Hon Chithyola Banda the highly favoured candidate to win with 80% of the delegates so far reached
His umunthu and level headedness is one of the unique features that are earning him trust and confidence amongst voters
Uyu basi Mipando Watenga Kale
Nduna yowona zamaboma aang'ono ang'ono Wolemekezeka a Richard Chimwendo Banda MP ati, anthu aku Mwanza West Constituency asalole kuti asinthe Phungu Wa kunyumba yamalamulo. A Chimwendo adati ku Mwanza West Constituency anthu tili naye kale phungu wawutsogoleri wabwino yemwe ndi Joyce Chitsulo . A Chimwendo adalankhula izi pamsonkhano wachitukuko womwe adachititsa muboma la Mwanza.Achimwendo adawuzanso anthu okhala muboma la Mwanza kuti asalole ndale zogawana. Achimwendo adatinso ndi Pulezidenti Chakwera yekha yemwe angathandize kuti moyo wa anthu aku Mwanza komanso chitukuko zipite patsogolo. Achimwendo apemphanso anthu kuti asamanyoze mafumu.
JOYCE CHITSULO: THE EPITOME OF DEVELOPMENT - RICHARD CHIMWENDO BANDA
Minister of Local Government, Civic Education, and Unity, Richard Chimwendo Banda, has praised Joyce Chitsulo, Independent legislator for Mwanza West, for her outstanding development initiatives in the constituency. Speaking at Chiwembu Community Ground in Mwanza West, following an inspection of various ongoing projects, Chimwendo commended Chitsulo's exemplary dedication to the betterment of her constituents.
Emphasizing Chitsulo's remarkable commitment to development, Chimwendo Banda highlighted her exceptional role as one of the few female MPs transcending conventional boundaries in both Parliament and their constituencies.
Chimwendo lauded Chitsulo for her unwavering focus on the people's welfare, declaring government support to ensure her re-election in the upcoming term.
"I can personally attest that Joyce Chitsulo is an industrious representative in Parliament, tirelessly advocating for the interests of Mwanza West Constituency. She actively contributes to parliamentary debates and steadfastly defends the rights of women and her constituents," stated Chimwendo Banda.
He underscored President Lazarus Chakwera's commitment to equitable development nationwide, citing projects such as the Mwanza Community Stadium as evidence of this dedication. Chimwendo expressed confidence that Chakwera's government would secure victory in the next election, driven by its nationwide pursuit of development.
In her remarks, Chitsulo expressed heartfelt gratitude to Chimwendo Banda for his visit to her constituency and for spearheading the development rally. She particularly appreciated the various projects initiated in her constituency through the Ministry of Local Government and other ministries, under President Lazarus Chakwera"s leadership.
Assuring the minister of the constituents' deep appreciation for the developments, Chitsulo pledged their commitment to maintaining these initiatives.
Before the r
*MSONKHANO WACHITUKUKO WAKU MWANZA HIGHLIGHTS*
Poyankhula pa Msonkhano wachitukukowu, Wolemekezeka a Joyce Chitsulo MP adawuza Nduna yowona zamaboma aang'ono a Richard Chimwendo Banda MP kuti akawaperekere uthenga wothokoza kwa Pulezidenti wadziko lino His Excellency Dr Lazarus McCarthy Chakwera. A Chitsulo adati anthu aku Mwanza West akuyamika kwambiri Pulezidenti Chakwera kaamba ka zitukuko zomwe a wapatsa muboma la Mwanza. A Chitsulo adati wina asakunamizeni kuti ku Mwanza ndikuchipinda kwawo. A Chitsulo adati kumwanza ndi kwa a Nicholas Dausi MP, a Joyce Chitsulo MP komanso a Senior Chief Govati, Senior Chief Nthache ndi a Senior Chief Katuli . A Chitsulo adati zitukuko zimene a Chakwera akuwapangira ndi zambiri. Ndipo apempha Pulezidenti Chakwera kuti apitilize. Kenako a Joyce Chitsulo adapempha achimwendo kuti akawapemphere kwa mayi wafuku lino Her Excellency Madam Monica Chakwera kuti alole azimayi a Chakwera Muboma (Azimayi) omwe amagwira ntchito muboma kuti akacheze ndi mayi wafuko lino. A Chitsulo apemphanso boma kuti limalize kumapanga msewu omwe ukumangidwa ku Mwanza.
The Northern Region has spoken
Hon Simplex Chithyola Banda MP is Loved and Favoured in all Regions.
Truly truly, Hon Simplex Chithyola Banda MP is the Incoming MCP Secretary General.
*Malawi Congress Party Women Advocate for Hon Esther Kathumba MP During Kamuzu Day Commemoration*
Today, during the 𝗞𝗮𝗺𝘂𝘇𝘂 𝗗𝗮𝘆 𝗖𝗼𝗺𝗺𝗲𝗺𝗼𝗿𝗮𝘁𝗶𝗼𝗻 ,Malawi Congress Party women from across the country have passionately put forth a challenge to the delegates tasked with voting authority to rally behind and vote for 𝗛𝗼𝗻 𝗘𝘀𝘁𝗵𝗲𝗿 𝗞𝗮𝘁𝗵𝘂𝗺𝗯𝗮 𝗠𝗣 as their preferred candidate 𝗳𝗼𝗿 𝘁𝗵𝗲 𝗽𝗼𝘀𝗶𝘁𝗶𝗼𝗻 𝗼𝗳 𝗗𝗶𝗿𝗲𝗰𝘁𝗼𝗿 𝗢𝗳 𝗪𝗼𝗺𝗲𝗻.This endorsement comes as a result of Hon. Esther Kathumba's unwavering commitment to bolstering women's representation and support within the party.
In an emotional display of solidarity while uttering songs of praise the women within the party have highlighted Hon. Esther Kathumba's exceptional dedication to serving and uplifting the female members of the Malawi Congress Party. Their rallying cry echoes the sentiment that she is the most fitting candidate to advance the interests of women and propel the party forward.
𝗸𝘂𝗻𝗮𝗹𝗶𝘁𝘂 *𝗸𝘂fuwula kuyankhula mokweza mawu* 𝗸𝘂 𝗸𝗮𝗺𝘂𝘇𝘂 𝘀𝘁𝗮𝗱𝗶𝘂𝗺 𝗹𝗲𝗿𝗼 𝗮𝘇𝗶𝗺𝗮𝘆𝗶 𝗮𝗸𝘂𝗻𝗲𝗻𝗮 𝗸𝘂𝘁𝗶 𝘁𝗶𝗸𝘂𝗳𝘂𝗻𝗮 𝗛𝗼𝗻 𝗞𝗮𝘁𝗵𝘂𝗺𝗯𝗮 𝗼𝘀𝗮𝘁𝗶 𝘄𝗶𝗻𝗮 𝗮𝘆𝗶 𝗻𝗱𝗲 𝗶𝗻𝘂𝘆𝗼 𝗻𝘁𝗵𝘂𝗺𝘄𝗶 𝗺𝘂𝘀𝗮𝗱𝘇𝗮𝗹𝗮𝗸𝘄𝗶𝘁𝘀𝗲.✅✅✅✅✅✅☑️☑️☑️🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥✅✅✅✅✅
*DPP Njamba Rally Highlights*
MFUNDO ZOMWE ADAYANKHULA HON NOEL LIPIPA MP PAMSONKHANO WA DPP PA NJAMBA FREEDOM PARK
#1.Phungu wa kunyumba yamalamulo wadela Blantyre City South Constituency, Wolemekezeka a Hon Noel Lipipa adayamba ndikuyamika Mulungu ponena kuti Mulungu ndiwabwino nthawi zonse.
#2.Lipipa adati, Mulungu ndiwabwino watisungira ndi moyo Pulezidenti wathu Professor Arthur Peter Mutharika Kuchokera Panthawi yomwe tidavota mu 2020 kufikila lero
#3.A Noel Lipipa MP adati chipani cha DPP chimayimilira zinthu zingapo zomwe timangoziyankhula koma ndi zamu Bayibulo (Bible).
#4.Noel Lipipa adatchula mawu amubuku lopatulika mu Bayibulo (Bible) pa buku la Miyambo 31 :8 - 9 pamene mawu akuti yankhulirani iwo amene sangadziyankhulire okha, tetezani ufulu wa anthu osauka komanso anthu ovutika (osowa).
#5.A Lipipa adanenanso vesi (verse) ina yomwe ndi Masalimo 41 :1 pomwe mawu akuti " Odala ndi amene amasamala anthu ofowooka pakuti Mulungu amamuwombola pa nthawi yamavuto.
#6.A Lipipa adatinso, lachisanu lapitali pa 10 May 2024, Bungwe la UNICEF latulutsa lipoti limene likunena kuti kuno ku Malawi, muchaka chino cha 2024, umphawi wakula koposa momwe udalili muchaka cha 2020. Pano umphawi wanyanya.
#7.A Lipipa adati kuno ku Malawi, chiloweleni muboma awa a Tonse Alliance, chilichonse Chakwera Mtengo. Chimanga Chakwera Mtengo. Sopo, shuga, mchere , feteleza nazo zakwera mtengo.
#8.Lipipa adati wagwada pansi kuwagwadira a Polofesa Mutharika kuwapempha kuti awombole dziko la Malawi.
#9.A Lipipa adati amalawi akufuna kuti Polofesa Mutharika abwererenso mu chaka cha 2025 kuti adzakonzenso dziko la Malawi.
#10.Dziko la Malawi lomwe Polofesa Mutharika adalisiya mu 2020, si dziko momwe lirili pano.
#11.A Lipipa adatinso a Polofesa Mutharika adapeleka msewu wa Manja kuti awuyika tala (phula). Koma mpaka pano boma ili lilipo pano likulephera kuwuyika tala.
Ku Nancholi, ku Village House misewu idakali momwe idalili mu 2020.
#12. A Lipipa adati panthawi yomwe a Noel L
*DPP Njamba Rally Highlights*
Malo a Njamba Freedom Park ali mudera (Constituency) ya Blantyre City South Constituency yomwe MP wake ndi Wolemekezeka a Hon Noel Lipipa MP. Msonkhano usadayambe, Mtolankhani Wotchuka wa Times TV, Mr Brian Banda adacheza ndi a Lipipa.Brian Banda adanena kuti kwabwera anthu ambiri ku msonkhano ndipo a Lipipa popherapo Mphongo adati apa mpang'ono chabe chifukwa anthu ambiri apita kokalandira bwana H. E. Professor Arthur Peter Mutharika. A Lipipa adauzanso Brian Banda kuti kuno ku Malawi, anthu akuvutika kwambiri. Njara yavuta kwambiri ndipo chilichonse Chakwera Mtengo. A Lipipa adati Professor Mutharika mu chaka cha 2020 dziko adalisiya pabwino. Ndiye chonde akupempha a Mutharika kuti chonde mu 2025, Professor Arthur Peter Mutharika alibwezeretse dziko pamene adalisiyila. A Lipipa adati anthu ambiri adabwera ku msonkhano wa DPP kuti adzamve momwe zikukhalila. Lipipa adatinso Denge samangoyendetsa wina aliyense.
Lipipa adati pano dziko la Malawi lilibe oyendetsa ndege (Payiloti /Pilot). Dziko lili pa auto Pilot. Dziko lili pa auto pilot ndichifukwa chake mitengo ya zinthu ikungokwera.
Lipipa adatinso mu cha cha 2020, aMalawi adanamizidwa. Lero Banki yayikulu mudziko muno ya Reserve Bank yapanganso loss.
Mu 2020 aMalawi adanamizidwa. Panopa mu 2024 anyamata ambiri opanga bizinesi yogulitsa magalimo aduka. Anthu ambiri opanga bizinesi aduka. Lipipa adafunsa kuti lero ndi ndani amene angakwanitse kudya katatu monga a Chakwera ndi boma la Tonse Alliance amatilonjezera??
Lipipa adati mu 2025 tikufuna Professor Arthur Peter Mutharika abwererenso pampando ndipo adzakonze zinthu momwe zidalili mu 2020.
Anthu oposa 100,000 ndiwo adabwera ku Msonkhano wa DPP omwe udachitika pa Njamba Freedom Park dzulo mumzinda wa Blantyre.
*PART 2 OF BRIAN BANDA'S TIMES EXCLUSIVE INTERVIEW WITH HON NOEL LIPIPA MP.*
👉Mfundo Zikuluzikulu zomwe adayankhula a Lipipa.
1. Wolemekezeka a Noel Lipipa akukhulupilira kuti muzisankho zomwe zichitike chaka chamawachi, iwo adzawina ngati Phungu Wa kunyumba yamalamulo wadela la Chilomoni - Kabula - Nancholi Constituency
2. A Lipipa akuti iwo ndi Phungu yemwe amakhala bwino ndi anthu
3. Constituency yatsopano ya Chilomoni - Kabula - Nancholi ndi Constituency yomwe yapangidwa kumene pophatikiza ward ya Chilomoni ndi ma ward ena atatu omwe adali ku Constituency ya Blantyre City South Constituency.
4. Mwazifukwa zina zomwe Wolemekezeka a Hon Noel Lipipa MP asankha kukayimila ku Constituency ya Chilomoni - Kabula - Nancholi Constituency ndi zoti, pamene amadula dela la Blantyre City South Constituency kukhala ma Constituency angapo, zapezeka kuti Nyumba ya a Lipipa yapezeka ku Constituency yatsopano ya Chilomoni - Kabula - Nancholi Constituency.
5. Mwazitukuko zina zomwe adachita ku Constituency ya Blantyre City South Constituency, Wolemekezeka a Hon Noel Lipipa MP adamangisa chipatala cha Mtonda Clinic. Pomwe amadula Constituency ya Blantyre City South Constituency, papezeka kuti Mtonda Clinic yakhalila ku Blantyre City South Constituency.
6. Noel Lipipa adagula ambulance pa Mtonda Clinic kugwilitsa ntchito ndalama zake zamthumba mwake.
7. Noel Lipipa satenga /salanda ambulance yomwe adagulira chipatala cha Mtonda Clinic
8. A Noel Lipipa anenetsa kuti iwo sangalande galimoto yomwe adagulira dera (Community) chifukwa iwowa ali ndi umunthu komanso mtima othandiza anthu
9. A Lipipa ati anthu tisamangowafuna nthawi yovota yokha
10. Ambulance ya pa Mtonda clinic, mafuta ake amathila ndi iwo a Noel Lipipa
11. A Noel Lipipa akuthoza azimayi agulu la Mtonda Women wome adapeleka mchenga, komanso kugula Cement ndicholinga chothandiza MP wawo kuti amange Mtonda Clinic
12. A Lipipa akuti iwo ataluza u MP sangalande Ambulance kapena kuchotsa zitukuko zomwe adachita iwo chifukwa
President Dr. Lazarus McCarthy Chakwera is bringing home a staggering US$350 million from United States of America for Millennium Challenge Compact which is going to foster economic growth and reduce poverty in the country.
Millennium Challenge Corporation (MCC) hosted President Dr Chakwera and his delegation to dinner last night Dallas, Texas, the US, putting into force Malawi’s second Millennium Challenge Compact.
Minister of Finance Honourable Simplex Chithyola Banda explains to journalists accompanying President Dr Chakwera the significance of the Compact to Malawi:
President Dr. Lazarus McCarthy Chakwera is bringing home a staggering US$350 million from United States of America for Millennium Challenge Compact which is going to foster economic growth and reduce poverty in the country.
Millennium Challenge Corporation (MCC) hosted President Dr Chakwera and his delegation to dinner last night Dallas, Texas, the US, putting into force Malawi’s second Millennium Challenge Compact.
Minister of Finance Honourable Simplex Chithyola Banda explains to journalists accompanying President Dr Chakwera the significance of the Compact to Malawi:
#Times360Malawi
Mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera wati boma lithandiza kampani zimene zikufuna kukulitsa ntchito zawo mdziko muno.
A Chakwera ayankhula izi ku Dallas, Texas ku America pamkumano ndi akuluakulu ochokera ku kampani ya Coca-Cola Corporation Limited.
Mwazina, akuluakuluwa anafotokozera a Chakwera za mapulani awo okuza ntchito zawo ku Malawi.
A Simplex Chithyola Banda ndi nduna ya zachuma ndipo akulankhula ndi mtolankhani wathu Taonga Sabola Ku Dallas, Texas.