Story Club FM

  • Home
  • Story Club FM

Story Club FM A revolutionary Radio Station in Malawi devoted to the Arts
(12)

Mmodzi mwa anthu odziwika bwino pa masamba amchezo pa nkhani za msangulutso komanso kuthandiza anthu munjira zosiyanasiy...
09/09/2024

Mmodzi mwa anthu odziwika bwino pa masamba amchezo pa nkhani za msangulutso komanso kuthandiza anthu munjira zosiyanasiyana, Pemphero Mphande, walandila ndalama zoyendetsera mpikisano wake. Pemphero amachititsa mpikisano wa olemba nkhani omwe ndi achinyamata komanso ophunzira ochokera msukulu zosiyanasiyana. Ndalamazi zomwe ndi zokwana 15 million kwacha, apereka ndi a sukulu za King's Foundation Limited.

Poyankhula pa mwambo omwe unachitikira ku King's Foundation Rose Academy ku Lilongwe, mkulu wa sukulu za King's foundation a Chitsanzo Hiwa, ati sukulu zawo zili ndi chidwi ndi mpikisanowu chifukwa ndi njira imodzi yotukulila luso la malembedwe komanso kulimbikitsa khalidwe lowerenga. Iwo anati ndizovetsa chisonii kuti chidwi chowerenga chikulowa pansi pakati pa a Malawi makamaka ana a Sukulu ndipo ndicholinga chawo kuthandizilapo kukonza vutoli.
M'mawu ake Pemphero Mphande anayamikila Sukulu za kings foundation chifukwa cha thandizoli ponena kuti lithandiza ntchito zoyendetsa mpikisanowu.

Aka ndikachiwiri tsopano kuti a King's foundation athandizire mpikisanowu womwe udayamba mu chaka cha 2021.


Olemba: Frank Likaomba

Gulu la Free worship Malawi lakoza phwando la mapemphero opembedzera ku BICC Amphitheater.  Mapemphero ndi mapembedzerow...
08/09/2024

Gulu la Free worship Malawi lakoza phwando la mapemphero opembedzera ku BICC Amphitheater. Mapemphero ndi mapembedzerowa ali mkati ndipo kuli anthu ochuluka.

Anthu akuoneka okhudzika ndi miyoyo yawo, palipano aliyense akumapemphera muchiyankhulo chakechake ena muChichewa, Chitumbuka, Chingerezi ndi zina, nyimbo zamapembedzo zili mkati.



Sailes Phiri

Malawi Under-20 National Team coach Bob Mpinganjira has released a 30-man provisional squad for the AFCON Under-20 Cosaf...
08/09/2024

Malawi Under-20 National Team coach Bob Mpinganjira has released a 30-man provisional squad for the AFCON Under-20 Cosafa Qualifier, which will be held in Mozambique later this month.

The majority of the players who led the junior Flames to victory in the Four Nations Under-20 tournament earlier this year are included in the squad.

GOALKEEPERS
Amos Sande
(Ekhaya FC)
Julius Banda
(FCB Nyasa big Bullets Rsv)
Vincent Mdoka
(Mighty Mukuru Wanderers Rsv)
Innocent Kamwambe
(L**e Masters)

DEFENDERS
Washali Jaziya
(Silver Strikers Rsv)
Edward Thengo
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Helmas Masinja
(Ascent Academy )
Kondwani Tebulo
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Anold Jumbe
(Luanar Fc)
Happy Mphepo
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Andrew Lameck
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv )
Yohane Jimu
(Ekhaya Fc)

MIDFIELDERS
Dan Kudonto
(Mighty Mukuru Wanderers)
Oscar Petro
( FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Francis Malikebu
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Mwisho Mhango
(Ascent academy)
Chifuniro Kamenya
(Mighty Mukuru Wanderers)
Blessings Kanowa
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Maxwell Tsakanamba
(TDS)
Steve Palemeza
(Mighty Mukuru Wanderers Youth)
Chrispine Mapemba
(FCB Nyasa Big Bullets)
Wyson Msuka
(Agumbala Fc)
Hadji Steven
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Felix Jalasi (TDS)

STRIKERS
Madalitso Safuli
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Misheck Billiat
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Emmanuel Saviel
(Mufulira Wanderers)
Masambelo Kalua
(Mighty Tigers)
Zannil Jussab
(FCB Nyasa Big Bullets Rsv)
Benard Mpoto
(NRC Academy)

An empowering women artists conversation at the Lake of Stars : Temwa,Hazel and Chmba
08/09/2024

An empowering women artists conversation at the Lake of Stars : Temwa,Hazel and Chmba

08/09/2024

An exclusive interview with Mtameni in our Media Van at the Lake Of Stars.

07/09/2024

Performing now at the Lake Of Stars, Sho Madjozi 🔥🔥

07/09/2024

Chipani cha Peoples (PP) pa msonkhano wake waukulu, chasankha atsogoleri ake a National Executive Committee (NEC) omwe akhale akuyendetsa chipani kuchoka pano kufika chaka cha 2029. Mndanda wa atsogoleriwa uli motere:
1. President ndi a Dr. Joyce Banda
2. Vice President South ndi a Ephraim Chivunde
3. Vice President East ndi a Lawrence Bisika
4. Vice President North ndi a Duncan Kawonga
5. Vice President Centre ndi a Peter Kamange
6. Secretary General ndi a Ben Chakhame
7. Deputy Secretary General ndi a Flony Maliro
8. Treasurer General ndi a Noah Chimpeni
9. Deputy Treasurer General ndi a Njaliwa
10. Deputy National Organising Secretary ndi a Gadi Thyangathyanga
11. Director of Women ndi a Beatrice Mwale
12. Deputy Director of Women ndi a Mable Masangano
13. Director of Youth ndi a Aubrey Harare
14. Deputy Director of Youth ndi a Cecilia Kumwenda
15. Director of Economic Affairs ndi a Vincent Chirwa
16. Director of Strategy ndi a Dr James Munthali
17. Deputy Director of Strategy ndi a Dr. Makala
18. Director of Elections ndi a Andekuche Chanthunya
19. Deputy Director of Elections ndi a Frank Kagone
20. Director of Legal Affairs ndi a Aaron Kisebe
21. Director of Campaign ndi a Cliffa Kondowe
22. Deputy Director of Campaign ndi a Rosten Chawinga
23. Director of Recruitment ndi a Edrissa Kazembe
24. Director of International Relations ndi a Edith Banda
25. Deputy Director of International Relations ndi a Yusuf Mmatila
26. Director of Research and Development ndi a Lemani Chapitapansi
27. Deputy Director of Research and Development ndi a Alefa Chisokeza
28. National Publicity Secretary ndi a Ackson Kalaile Banda
29. Deputy National Publicity Secretary ndi a Wellington Kuntaja
30. Director of Political Affairs ndi a Alex Solanke
31. Deputy Director of Political Affairs ndi a Cecilia Imani
32. Director of Religious Affairs ndi a Pastor Webster Kameme
33. Deputy Director of Religious Affairs ndi a Pastor Leonard Kafunsira


Sailes Phiri

07/09/2024

Afana Ceez kuyakitsa pa stage🔥🔥

07/09/2024

Wanga the poet performing at the Kweza stage

New day, new songs to listen to, new artists to explore.Mverani Mphanje za Luso 7pm ndi Prominent Yegama pamene akhale a...
07/09/2024

New day, new songs to listen to, new artists to explore.
Mverani Mphanje za Luso 7pm ndi Prominent Yegama pamene akhale akusewela nyimbo izi

1. Wanga - Mophy
2. Jay kiddo - Light skin Girl
3. Star Killers - Sitivana
4. Plot Lap D Ft Mwanache
5. NRendo - Benefit
6. Pay Zee - Ndioneseni
7. Mwenye Gamba – Mwina - Ngwaine
8. Zuku'Zama ft SomaBeatz - Altitude
9. Modern Squd - Rise up
10. Smadah Alcapone - Bredda
11. Kuwala ft Somabeatz - Gong
12. Lil Dash ft Shack D - My Lover
13. Eddicai NL - Follow
14. Mawiz viva - Zilimtsogolo
15. Crest x Boi Kid - Moyo Uli Bwino
16. Luda ft Stefact - Nthawi
17. Jaji Mw – Dear Jah
18. Baxton x Bebinah - Katswiri
19. Prefix - Adisababa
20. Betho - Sekelera

Catch Fashionista today with the host Mary Chitsonga at 12 pm!
07/09/2024

Catch Fashionista today with the host Mary Chitsonga at 12 pm!

Zeze Kingston is chilling after an amazing performance at the Lake of Stars yesterday.
07/09/2024

Zeze Kingston is chilling after an amazing performance at the Lake of Stars yesterday.

06/09/2024

Zeze Kingston performing

The  British high commissioner to Malawi highlighted the friendship that our cultures share, we need to interact more an...
06/09/2024

The British high commissioner to Malawi highlighted the friendship that our cultures share, we need to interact more and learn from each other in her opening remarks
Lake of stars started 20 years ago and we as a country are celebrating 60 years of having freedom and with this freedom we have such events as lake of stars with is a Flagship tourism marketing event that is done with various partners.
Zilanie Gondwe lauded the partners for investing in the arts, because it helps to tell the stories about different aspects of our beautiful culture.

The opening speeches where concluded by an exciting fireworks show to mark the official start of this years Lake of Stars.

06/09/2024

Tamba Africa performance

06/09/2024

Fireworks celebrating the launch of 2024 Lake of Stars!

06/09/2024

Rachel Dadd, folksinger from the UK and one of the main headliners for LOS2024, warming up for her performance.

The Party just got started!!!Patrons of the beloved festival have started flocking in to the venue, Fish Eagle Bay in Nk...
06/09/2024

The Party just got started!!!
Patrons of the beloved festival have started flocking in to the venue, Fish Eagle Bay in Nkhotakota ready to have intense fun. Stay locked in for more.

Catch Mphanje za Luso at 7pm with Prominent Yegama and explore the following Artists and there songs:1. Gazel Wagonjetsa...
06/09/2024

Catch Mphanje za Luso at 7pm with Prominent Yegama and explore the following Artists and there songs:

1. Gazel Wagonjetsa

2. Nazarite Chiwaya - My beloved

3. Z-Square Ndampeza

4. chastarapa Wine

5. Ed ft Clempo Sugar

6. Vystar interlude

7. Ulex B Ft Blaz B- Osafooka

8. Teck Tays Ft Bes Park Undisainire

9. Love Star Boss Pena

10. KayStevo x Tupo Apite(Finesse Cover

11. Jizo Ndinu nokha

12. Chris Andres - Entertainer

13. Skypree X Toompex X Chagoz Tambourine

14. Prestar & Jae- Awiri

15. Asodzi tidzaiwala bwanji

17. Iplus

16. Kyle_&_Tsoxy Bwoyree Pempho

18. Chisomo Somebody

19. The Bigger Brain 50 Man Zobisanabisana

20. Sauce Mate - Joker

Lake of Stars here we are!!
06/09/2024

Lake of Stars here we are!!

Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya anyamata  yagonja ndi timu ya dziko la Burundi 2-3 pomwe amakumana mu Africa C...
05/09/2024

Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya anyamata yagonja ndi timu ya dziko la Burundi 2-3 pomwe amakumana mu Africa Cup of Nations Qualifies lero pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe.

Malawi inapeza zigoli kudzera kwa Chawanangwa Kawonga pa mphindi 30 komanso Lanjes Nkhoma pa mphindi 71 pamene timu ya Burundi inapeza chigoli choyamba kudzera mwa Chimwemwe Idana yemwe anadzigoletsa yekha pa mphindi 22 asanabwere Jean Claude Girumugisha pa mphindi 33 komanso Jordi Baininwa Liongol pa mphindi 88.

Pakali pano timu ya Burundi ndi yomwe ikutsogola mu gulu "L" ndi ma points atatu.

Flames ikuyembekezeka kukumana ndi timu ya Burkina Faso la chiwiri ku Bamako dziko la Mali.

Wolemba: Killion Sambo

05/09/2024

Mphindi zokwana 88 zatha pa Bingu.

Malawi 2-3 Burundi

05/09/2024

Mphindi zokwana 76 zatha pa bwalo la Bingu.

Malawi 2-2 Burundi

Chigawo chachiwiri chayamba pa bwalo la Bingu. Malawi 1-2 Burundi
05/09/2024

Chigawo chachiwiri chayamba pa bwalo la Bingu.

Malawi 1-2 Burundi

05/09/2024

Chigawo choyamba chatha pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe pomwe timu ya Flames ikukumana ndi Burundi mu Africa Cup Qualifies.

45' + 3'
Malawi 1-2 Burundi

05/09/2024

Mphindi zokwana 33 zatha pa bwalo la Bingu.

Malawi 1-2 Burundi

05/09/2024

Mphindi zokwana 30 zatha pa bwalo la Bingu pomwe Chawanangwa Kaonga wagoletsa chigoli.

Malawi 1-1 Burundi

05/09/2024

Mphindi zokwana 26 zathapo pa bwalo la Bingu.

Malawi 0-1 Burundi

05/09/2024

Masewera ayamba pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe pomwe timu ya mpira wa miyendo adziko lino ya Flames ikukumana ndi timu ya Burundi.

Malawi 0-0 Burundi

Anthu  akulowa mosisitika kuno kubwalo la masewero la Bingu munzinda wa Lilongwe pomwe Timu yathu ya mpira wa miyendo ya...
05/09/2024

Anthu akulowa mosisitika kuno kubwalo la masewero la Bingu munzinda wa Lilongwe pomwe Timu yathu ya mpira wa miyendo ya dziko lino "The flames" 🇲🇼 ikuyembekezeka kusewera ndi Burundi 🇧🇮 mu ndime yodzigulira malo mu Africa Cup of Nations lero nthawi ya 3 koloko masana ano.

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Story Club FM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Story Club FM:

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share