MBC TV 2

MBC TV 2 MBCTV 2on the Go...THE ONLY Entertaining Television IN Malawi🇲🇼
(2)

REST IN PEACE DR SAULOS KLAUS CHILIMA👑
11/06/2024

REST IN PEACE DR SAULOS KLAUS CHILIMA👑

18/03/2024

Good Morning 🌞🌝

10/03/2024

HAPPY SUNDAY🤝🇲🇼

08/03/2024

FRIDAY LANU LIli Bwa Ndipo Mukuonelela Kanema Kuti🇲🇼🤝🤝🎯❓

Beanca Is Back Catch Her live today on 2ONtheGo live   with deh Baddest Drew JESSIE🇲🇼💯✨🌟⭐   Starts at 1:30Pm
27/02/2024

Beanca Is Back Catch Her live today on 2ONtheGo live with deh Baddest Drew JESSIE🇲🇼💯✨🌟⭐ Starts at 1:30Pm

19/02/2024

Its Another Beatiful Monday ......🤝🇲🇼Good Morning🧡

16/02/2024

GOOD MORNING🇲🇼🤝

13/02/2024

🇲🇼MWASWELA BWANJI❓🗼 Tichezeko Masana Uno🤝

⚽  🇲🇼🔥🔥🔥 Kodi Atayiphule Ndani❓
10/02/2024

⚽ 🇲🇼🔥🔥🔥 Kodi Atayiphule Ndani❓

10/02/2024

HAPPY SABBATH🇲🇼🗣️♥️

KUMVETSERA MWACHIDWIKhwimbi la anthu limatsatira mwachidwi  zomwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera amayaankh...
09/02/2024

KUMVETSERA MWACHIDWI

Khwimbi la anthu limatsatira mwachidwi zomwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera amayaankhula mu uthenga wake ku mtundu wa a Malawi kudzera mu nyumba ya malamulo.

Panja pa nyumbayi aikapo zinkuzamau zomwe anthuwa amamvetsera mwa chidwi.

Dr Chakwera wafotokoza mapulani aboma mundondomeko ya chaka chino mpaka chaka chamawa, pachingerezi SONA.

Wolemba: Mayeso Chikhadzula

Industry captains have welcomed Government's decision to remove visa entry restrictions for 48 countries including the U...
08/02/2024

Industry captains have welcomed Government's decision to remove visa entry restrictions for 48 countries including the USA, United Kingdom, Germany, France, Australia, China and Russia.

The visa exemptions also apply to all SADC and COMESA member states, including some multilateral institutions that do business with the Malawi Government.

Standard Bank Plc, Chief Executive Officer, Phillip Madinga says it will help the country increase inflows of foreign currency.


Afcon Semi Finals Begin Today ⚽ 🏆 7Pm:- Nigeria Vs South Africa10pm :- Ivory Coast vs Dr Congo  ⚽
07/02/2024

Afcon Semi Finals Begin Today ⚽ 🏆
7Pm:- Nigeria Vs South Africa
10pm :- Ivory Coast vs Dr Congo ⚽

Afcon Quarter Finals Begin Today 🏆  🇲🇼🔥⚽⚽7pm :- 🇳🇬 Nigeria vs Angola 🇦🇴 10pm :- 🇨🇩 Dr Congo vs Guinea 🇬🇳
02/02/2024

Afcon Quarter Finals Begin Today 🏆
🇲🇼🔥⚽⚽

7pm :- 🇳🇬 Nigeria vs Angola 🇦🇴

10pm :- 🇨🇩 Dr Congo vs Guinea 🇬🇳

31/01/2024



AFCON QUARTER FINALS FIXTURES 🏆

Friday

7pm: 🇳🇬Nigeria vs Angola 🇦🇴

10pm :- 🇨🇩 Dr Congo vs Guinea 🇬🇳

Saturday

7pm:🇲🇱 Mali vs Ivory Coast 🇨🇮

10pm : 🇨🇻 Cape Verde vs South Africa 🇿🇦

29/01/2024

🇲🇼 ON Fire 🔥🔥🔥

27/01/2024

Goodmorning ☀️
Happy Sabbath 🙏

26/01/2024

Segulani MBC2 TV .. NOW muonele Jetu ..... Interview

10pm :- ZAMBIA🇿🇲 vs Morocco 🇲🇦 MWAKWELA ITI‼️
24/01/2024

10pm :- ZAMBIA🇿🇲 vs Morocco 🇲🇦 MWAKWELA ITI‼️

24/01/2024

MWADZUKA BWANJI AMALAWI ❓🇲🇼📌

21/01/2024

ZAMBIA 🇿🇲vs TANZANIA
🇹🇿 MWAKWELA Iti❓⚽⚽

21/01/2024

CHAKWERA ARRIVES FROM DR CONGO

President Dr Lazarus Chakwera has arrived home from the Democratic Republic of Congo (DRC) through Chileka International Airport in Blantyre.

Dr Chakwera was welcomed by Vice President Dr Saulos Chilima, government ministers, First Lady Madam Monica Chakwera, members of the Tonse Alliance and traditional leaders, among others.





21/01/2024

SUNDAY LANU LIKUYENDA 🏃BWANJI❓🇲🇼📌

19/01/2024



Team awards:

1. The most improved team- Chitipa United (K2 million prize)

2. Third placed team- Mighty Wanderers (K7 million prize)

3. Runners up - Silver Strikers (K15 million prize)

4. Champions- Bullets (K40 million prize)

 Akubanja la Katelele Ching'oma, ati mwambo oyika m'manda thupi la oyimbayu uchitika mawa kwawo ku Chididi m'boma la Nsa...
18/01/2024



Akubanja la Katelele Ching'oma, ati mwambo oyika m'manda thupi la oyimbayu uchitika mawa kwawo ku Chididi m'boma la Nsanje.

Oyimbayu wamwalira m'bandakucha wa lero ku chipatala cha Kamuzu Central ku Lilongwe atadwala nthenda yokhudza chiwindi. Malinga ndi a Elvis Ching'oma Katelele wamwalira ali ndi zaka 36 ndipo wasiya mkazi ndi ana atatu.

Padakalipano Dy Seva yemwe amayimba m'gulu la Sena Universe wati imfa ya Katelele ndiyodandaulitsa ponena kuti anali katswiri yemwe anathandizira kupitisa patsogolo mayimbidwe ku Nsanje.

Dy Seva wauza MBCtv2 kuti anayimba nyimbo ndi katswiriyu kumapeto a chaka chathachi, 'Makhaliro a Asena' yomwe sinatuluke ndipo akukhulupilira kuti mzimu wake udzakhala osangalala nyimboyo ikatuluka.

16/01/2024

Dominant FCB Nyasa Big Bullets have received a vote of confidence from their sponsors after the team completed a domestic quadruple, barely a year after partnering First Capital Bank (FCB).

15/01/2024

HAPPY JOHN CHILEMBWE DAY ✔️🇲🇼

07/01/2024

HAPPY SUNDAY NIGHT MALAWIANS‼️ VIBES on VIBES 🇲🇼

Catch us live‼️‼️ Radio 2fm New Frequencies 2024 vibes🇲🇼
04/01/2024

Catch us live‼️‼️ Radio 2fm New Frequencies 2024 vibes🇲🇼

04/01/2024

Bwalo la Malomo First Grade Magistrate ku Ntchisi lero lalamula a Shupo Lekodi azaka 46 kuti akakhale ku ndende kwa zaka ziwiri pa mlandu omwetsa mowa mwana wa zaka zisanu ndi ziwiri.

Mboni ya boma pa mlanduwu a Dalitso N'goma idauza bwaloli kuti mkuluyu adapaluma mlanduwu usiku wa pa 26 December chaka chatha pomwe adatenga mwanayo yemwe ndi wa mlongo wake cha m'ma 7 koloko ndikukabwera naye cha m'ma 11 koloko usiku omweo.

Malinga ndi a N'goma, pa nthawiyo a Lekodi adatsazika kuti amakagula tomato koma atafika ku msika adalowa ku malo ena azisangalalalo komwe adamwetsa mwanayo mowa wa mtundu wa Nyasa Gin Spirit mokakamiza.

Koma oweruza milandu ku Malomo a Damiano Banda adati ngakhale mulanduwu chilango chake ndikukakhala ku ndende zaka khumi, iwo apeleka zaka ziwirizi kambakoti a Lekodi ndikoyamba kupalamula.

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MBC TV 2 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to MBC TV 2:

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share