02/07/2023
Phungu wa dera la chigawo cha pakati m'boma la Mulanje yemweso ñdi mtsogoleri wotsutsa boma mnyumba ya malamuro , Wolemekezeka Kondwani Nakhumwa lero ali nawo pa mwambo wopeza ndalama zothandizira tchalichi cha Nsanje Catholic m'boma la Nsanje.
Nankhumwa pofika pa malowo,walandilidwa ñdi aphungu a chipani cha DPP m'boma la Nsanje mayi Gladys Ganda komanso Eurita Mtiza.
Mmodzi mwa akuluakulu a chipani cha DPP mchigawo cha ku mwera bambo Kondwani Chiutsi alinawoso pa mwambowo.