MalawiWathu TV

  • Home
  • MalawiWathu TV

MalawiWathu TV Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from MalawiWathu TV, TV Channel, .

10 African countries with the highest cost of living in 20241. Mozambique2. Senegal3. Ivory Coast4. Ethiopia5. Mauritius...
26/01/2024

10 African countries with the highest cost of living in 2024

1. Mozambique
2. Senegal
3. Ivory Coast
4. Ethiopia
5. Mauritius
6. Zambia
7. Cameroon
8. Zimbabwe
9. South Africa
10. Uganda

25/01/2024

Akuba omwe amatsitsa katundu mu magalimoto oyenda mu nsewu wa Mwanza-Zalewa aba katundu waku State House Tent komaso Red Carpet ya President.

Katunduyu watsitsidwa ndakubawa usiku wathawu chama 10pm kuchokera pa bridge ya Vale.

Katunduyu amapita naye ku Mwanza komwe mtsogoleri wa dziko lino akuyembekezera kukachita msonkhano mawa.

Mtsogoleri wa dziko lino, a Lazarus Chakwera, ponyamuka awuza atola nkhani k*t ulendo wawo opita ku maiko a Saudi Arabia...
08/11/2023

Mtsogoleri wa dziko lino, a Lazarus Chakwera, ponyamuka awuza atola nkhani k*t ulendo wawo opita ku maiko a Saudi Arabia ndi Egypt uthandiza dziko la Malawi k*tukula chuma cha dziko lino kudzera m'ntchito za ulimi, migodi komanso zokopa alendo.

A Chakwera anena izi pa bwalo la ndege la Kamuzu ku Lilongwe ponyamuka ulendo wawo opita ku mayiko awiriwa.

Iwo ati ndi khumbo lawo ndik*ti dziko la Malawi komanso m'malawi aliyense akhale otukuka ndipo izi zingathekedi ngati loto la Malawi 2063 lingakwanilitsidwe.

Ku Saudi Arabia, President Chakwera akuyembekezeka kukaonera nawo pa mwambo wosainira ndalama zokwana $20 million (K22 billion) zomangira msewu wa Mangochi-Makanjira.

Ku Egypt, a Chakwera akakhala nawo pa chionetsero cha malonda cha Intra-Africa Trade Fair.

Police in Blantyre are looking for a middle aged man Victor Banda from Bangwe for painting a dog in tiger's colours to s...
25/09/2023

Police in Blantyre are looking for a middle aged man Victor Banda from Bangwe for painting a dog in tiger's colours to scare away NEEF loan recovery officers.

21/09/2023

MBC TO USE NEWLY ACQUIRED BOX LENSES, HD CAMERAS AT KAMUZU STADIUM

The Football fraternity is in for a treat of crystal clear pictures this afternoon as MBC will for the first time use its newly acquired box lenses and new HD camera heads for the TNM Super League game involving FCB Nyasa Big Bullets and Mighty Tigers at Kamuzu Stadium.

Earlier this year, MBC received a donation of box lenses and MBC invested K25 million to buy new HD Camera heads to match the equipment and offer soccer-loving Malawians quality football productions.

MBC Public Relations and Customer Affairs Manager, Chisomo Mwamadi, said the new equipment is a milestone as it amplifies MBC’s commitment to offer football followers quality soccer matches.

“We have tested the equipment and we are certain of beaming crystal clear pictures," Mwamadi said.

The match scheduled for 2:30 pm will be live on MBC TV1, MBC2OntheGo, Radio 2FM, and Airtel TV among other platforms.

Recently when MBC received a donation of some equipment, Director General, George, Kasakula, stressed the need for various organizations to continue supporting the public broadcaster so that it continues to deliver its mandate of informing, educating and entertaining the public better.

Mzibambo wazaka zosachepera 30 wapezeka atafa mugalimoto pa Gogo Jenala ku Area 15 ku Lilongwe.Munthuyu yemwe amagwira n...
20/09/2023

Mzibambo wazaka zosachepera 30 wapezeka atafa mugalimoto pa Gogo Jenala ku Area 15 ku Lilongwe.

Munthuyu yemwe amagwira ntchito yake ku Kampani ya Coca-Cola amuzindikira k*ti ndi Allan Witika.

Malingana ndi wantchito wake, a Witika anachoka pakhomo mawa k*ti akupita kuntchito ndipo anali ali bwino bwino.

Anthu ozungulira malowa, ati anaona mkulu wina ak*tsika Galimotoyi koma anavala chisukumba chofiyira ndi magolovesi oyera.

Anthuwa ati munthuyu atatsika galimotoyi anakhoma zitseko nkuchoka pa malopa.

In Salima a 'stray' police bullet has injured two National Bank-NB customers.According to Police report the victims are ...
06/09/2023

In Salima a 'stray' police bullet has injured two National Bank-NB customers.

According to Police report the victims are Westley Malenga 50, and Gelson Bakali, 43.

A Police report shows that a police officer, Inspector Bannett Cambikwa from Salima Police Station accidentally fired a shot in the air as he was performing rifle safety precaution measures.

Later, the stray bullet fell on the roof of the National Bank, Salima Branch; which is about 150 metres from the office.

As a result, the bullet pierced through the roof and ceiling and hit the following two customers who were on the line inside the bank.

The law enforcers further claim the bullet is yet to be found but have recovered empty cartilage.

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MalawiWathu TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share