A Tchamani

A Tchamani Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from A Tchamani, Newspaper, Matawale, Zomba.
(6)

STINGY MEN ASSOCIATION OF MALAWI

we offer
* ID
* Certificate
* Newspaper
* Graphic and design (birthday cards, wedding cards, posters etc)

0881936529/0996488271

https://youtube.com/?si=-mRj8umQXScblrif

JB iyi yokha imudutse 😂🙌
09/12/2024

JB iyi yokha imudutse 😂🙌

Matchamani koma tu mafanawa abwera ndmatukutuku🙌🤣
09/12/2024

Matchamani koma tu mafanawa abwera ndmatukutuku🙌🤣

09/12/2024

Nde azikukwezelani mitengo yazakumwa utanena kare kuti boma ndi lomweli, ngati ndi December angokhala June
😭😭

08/12/2024

Fanta wakwela mtengo kuchoka pa k650 kufika pa k850 yomwe ili k1000 kale 😭🙌aja ofuna kutamika pomugulira oyipayo fanta akhaula

08/12/2024

Picture of your Landlord 🚶‍♀️ 😎

Kodi matchamani iyi simunayione ? Mafulufute awa 😂
08/12/2024

Kodi matchamani iyi simunayione ? Mafulufute awa 😂

Rofhiwa Calvin Dzimbale eeh 🙄

Professo Phillip Khondowe NDI azinzanu ena omwe munkanyoza SMAM thawi imeneyoo bwenzi pano muli olemera Tcheya alibe tha...
08/12/2024

Professo Phillip Khondowe

NDI azinzanu ena omwe munkanyoza SMAM thawi imeneyoo bwenzi pano muli olemera
Tcheya alibe thawi yofotokoza zambiri km yenwe wawona izi ndikukumbukira ukuyenera kukhala kuti unakwatira pano

Wolemba ~Pj

08/12/2024

Osayiwala kuyenda yenda mu zikwati NDI mapwando kuti musaluze udindo wanu kuno

Wolemba~Pj

Tcheya alire bwanji abale kd ku mzuzu SMAM inalakwa chani 🤣 Wolemba~Pj
08/12/2024

Tcheya alire bwanji abale kd ku mzuzu SMAM inalakwa chani 🤣

Wolemba~Pj

Zifukwa zomwe SMAM headquarters mzuzu tikulephera kumalizira projectWolemba~Pj
08/12/2024

Zifukwa zomwe SMAM headquarters mzuzu tikulephera kumalizira project

Wolemba~Pj

Oyipayoo kuwonongeratu chuma Cha tcheya
08/12/2024

Oyipayoo kuwonongeratu chuma Cha tcheya

Mady P  posted"Mkazi wina ndamukanira chigololo kuseriku ine ndimadana ndi zopusa."
08/12/2024

Mady P posted

"Mkazi wina ndamukanira chigololo kuseriku ine ndimadana ndi zopusa."

Rofhiwa Calvin Dzimbale  eeh 🙄
08/12/2024

Rofhiwa Calvin Dzimbale eeh 🙄

Waneba waneba😂🙌Koma atchamani awa
07/12/2024

Waneba waneba😂🙌
Koma atchamani awa

07/12/2024

Matchamani mwatikhumudwitsa, show iyi mesa ndiya ulere 😭😂🙌

07/12/2024

Anthu 20 ndi amene aponya ndalama ngati gift ya birthday ya atchamani Nokhez, ndipo yonse yakwana k225. Zikuchitika ndithu 🙌✊😂

Happy birthday ENOCK HANDALA (Eno Nokhez) 🎉🎊🎈
07/12/2024

Happy birthday ENOCK HANDALA (Eno Nokhez) 🎉🎊🎈

Address

Matawale
Zomba
TCHAMANI

Website

http://www.atchamani41.com/, https://www.youtube.com/@atchamani

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when A Tchamani posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share

Category