04/10/2024
Mwezi watha ndinayesa kupanga create YouTube channel k*t ndidziponyako tizinthu tanga monga producer kma zikomo kwa Yehova wa Mphanvu zonse channel chomwe ndimati ndikuyesa chija kwa mwezi umodzi ndapeza 17 subscribers ndima total views 1k,kwaine ndi chinthu chapamwamba coz sinagwilise ntchito zomwe zapanga trend kma zomwe ineyo ndimapanga 🙌