![UNCLE LULU PART 2...Continuation of part 1In my life I have never seen mtolankhani osakonda mabodza. Koma ngati alipo, a...](https://img4.medioq.com/162/266/605246421622669.jpg)
04/04/2023
UNCLE LULU PART 2
...Continuation of part 1
In my life I have never seen mtolankhani osakonda mabodza. Koma ngati alipo, am sure ntchito imawavuta kugwira. Anyways, ntatuluka mu studio muja, nakumana ndi atolankhani amabodzawa omwe anandiphaphalitsa ndi mafunso monga mwa ntchito yawo. Ntangofika, anayambapo modzi, "mwacheza kale ndi ankolo anu?". I was like, "ankolo?". Then another one came in, she was like, "heee!! Timadziwa umanama iwe, Lulu si ankolo ako. Kuteroku nkona wachokamo chothawa mu studio mo eti?". At this point thats when I realized kuti aaahh that guy ndampatsa kagunde uja, was Lulu. Eeeh i was mad at myself. I felt sorry For myself coz I had one chance that I would have utilized to talk to the living legend. Literally I blew it away. Heard the inner voice inside me, "easy, all is not lost". Then i turned to the guys, " kodi Lulu yo wapita ngati? Mesa he is around?, dikilani atuluke muone zoti sindikunama. More over we spoke alot nkatimo koma vuto munalibemo inuyo". Koma eeeh ma guy, munthu ukayankhula chinthu chabodza, its crazy how time flies by to catch up with ur words.
I understand kuti mu studio muja Lulu anakhalamo almost close to an hour. Koma kwa ineyo, it felt like 2 minutes basi. Coz it was like as soon as after I told ma guys kuti Timudikile atuluke will show u kuti he is indeed an uncle, ndipomwenso amatuluka mu studio. Ine ngati ndilowe pansi. Anyways, anthu atuluka mu studio, ma guys are eager to see what am gonna do. Ine am just there thinking what to do coz ndee eeeh zinandikulira. I saw Lulu approaching from where we stood. By that time, I don't know what came over me coz nanyamuka kuti ndikumane naye Lulu kuti asafike kuli anzanga kuopa kuyaluka. Ntamupeza, I said, "Lulu, am a huge fan. Nyimbo zako zimandiwaza heavy. Koma without wasting much of your time, my friends ali apowo, nawanamiza kuti iwe ndi m'bale wanga nde ndizoti they are expecting chinachake". The guy laughed and he asked kuti, "what's your name?" (Ofcoz anafunsa funsoli mu chichewa, ine ndangoganiza kuti ikhale mu chizungu). 2 mins inayake akulu ajanso pena pake amazapangako za Gwamba wezi. Anyways back to my story, I told him my name kenaka anazati, "tiye". Tinafika pomwe panali anzanga aja. He told them kuti we are related blah blah blah.. I wasn't even paying attention. The fact is, the Legend saved me from embarrassment. From that moment Lulu anayamba kundiwaza. Now i understand kuti Ali Ku USA. Am wishing him all the best.AMATHA. Speaking of which, Ku USA kuli mayi anga akulu. I know ena muzitsutsa kumaona ngati ndikunama. Koma na Iyi Yokha, iyiyi, iyiyi nde ndiyoona.
The end.