14/11/2022
SAD NEWS
Mozy B is no more.
Woyimba yemwe amadziwika kwambiri ndi mayimbidwe ake a Chupa Dance wamwalira.
Ma report akunena k*ti woyimbayi wamwalira pamene amajambula video mdziko la Zambia koma pakadali pano sitidapezebe k*ti chachitika ndichani k*t amwalire.
Mozy b was a Tumbuka artist from Eastern part of Zambia he was based in lundazi as his home town.he plays his on tune called tchupa dance,he formed his on category of music in 2008.
RIP King